Khoti laling’ono la Chisenjere mu mzinda wa Blantyre lagamula mayi wina oyendayenda kuti akagwile ukaidi wa zaka ziwiri atapezeka olakwa pa mlandu otentha nyumba ya bambo wina.
Khotili linamva kuti mayiyu, wa zaka makumi awiri ndi mphambu imodzi (21) anatentha nyumba ya bambo wina, bamboyu atalephera kumulipira iye atamusangalatsa.
Khotili linamva kuti pa 27 Sepitambala chaka chino, mmayiyu amene dzina lake ndi Ellen James amamwa mowa limodzi ndi bambo wina pa malo ena otchedwa Soul City mu dera la Chileka.
Akuti awiriwa atamwa mowa anazindikira kuti akukondana ndipo anaganiza zopititsa chikondi chawo patali. Iwo anakachita za chisembwere ndipo atamaliza bamboyo anakanika kulipila. Iye anapempha kuti azalipile mtsogolo.
Akuti mayi oyendayendayo anamuvomela koma bamboyo anayamba u kavuwevuwe ndi kumangozemba ndi ndalama ya mayiyo.
A James pokupsa mtima ati anakatentha nyumba ya bamboyo ndi kuononga katundu okwanila K400,000.00.
Poweluza mulandu umenewu, oweluza anawalamula mayi James kuti akakhale kundende kwa zaka ziwiri ati chifukwa chotentha nyumba.
A James amachokela ku Balaka, mmudzi mwa a Matola. Bambo amene wawapititsa ku ndende uyu, a Polisi akana kumuulula ku gulu.
Kumpanje kwavuta eti.. Pausilu panu agalu nose …asuntche ampaka ziboda akalulu inu
Hule wachabe chabe
Kodi nkuruyo saripabanja? nanga nkazi wake aribe bwetete? ndisachedwe ndimafuso apa chigamuro changa ndiichi bambo iwe m’chira wako hure kundendeko mzimu wako uwuse muntendere kkkkkkk?
Akanangomupha basi huleyo iyaaa
Kkkkkkkk
Kodi uhule ndi business eeeti ofunikaso MRA igwirepo ntchito
Bamboyoso akamange chifukwa sanampase ndalama
If interested all cute ladies available in this group who needs a guy to give them good sex and this includes all sugar mummies or just older ladies but should be smart and ready to spoil with money inbox or call on 0882926882 same line hit me on whatsapp, love you
kodi amakhalaso ndi makastomala eti?
Haaaaaaaaaaaaa kkkkkkkkkkkkkk koma inu inu ohooo zosakhala bwino ma guys tiyeni tizikwanilisa zomwe tagwilizana osamango chinda amkaziwa mulibe cash njala yathuyi simuyiona nanutso amakhoti samakondela pogamula mlandu mdalayutu nanaye ndiolakwa akanapeleka dollar zikanathela kumjangokoko izi ndipo sitikanaziziwa izi ok
nthawi yantha tembenukirani kwa yesu
Milandu ya anthu osauka nde imakuphwekerani.Ya ma cashgate mumavutikanabayo kugamula.
Kkkkkkkkkkkk zabooka yapakanayopeleka pang’opang’ono ndikubwela naneso ndizangole
Kunsika supita opanda cash ikakhala ngongole mumakambiranatu Chile usanakazitereke nyembazo
kkk akuopa udindo@ Chri
Zofuna izooooo!!!
amuchit bwino akaziwon
koma azimayiwa akuonjeza. tangoganizani mnthuy mwnanso anamupasanso zokandakand ndy kumuotcheranso nyumbA? aaaaa! two yrs yachepa kwambr
Mamunayo chisilu sunganyamuke kupita ku Shop Uribe drama banva akanamudulA chonyengelacho khani yakha
hule ndimamuna aliyese wachilendo amalandiliratu ndalama koma m’mene ndikuvera apa kusonyeza kuti anali kasitomala amavesesana amatha kumukwera pa ngongole..koma chomwe chinavuta bambo ameneyi zikuoneka anajaira anayamba kumutenga hule ngati chibwez chake kuti azimukwera ulele asanakambilane ndi huleyo..pomwe hule sazaloweleka alibe zoti wamukwera nthawi yayitali wakhala ukumulipira umayenera ulipire basi..pokhapokha mwina ngati amakufila iyeyo zimatheka kumakuitana ulele mwinaso kupita ku room yake kukutulutsila ndalama zomwe wakweletsa tsiku limenelo kukugaira zina mpaka kutenga kukamwera mowa ndiiweyo…kwaine ndikuona bamboyu ndiye olakwa ali ndi vuto amafuna kumaonetsa ushasha kwa hule pomwe hule safuna uzimuonetsera ushasha
Muziti hule wamangidwa chifukwa chotetha nyumba yahule mzake.
Malonda opanda oda.mahule ena amachita kudzitama akuti ali ndi zokoma (kadya ubwelere) aliso ndi ma style awo step iliyose ili ndi kam’tengo kake.utafuna ugone pompho ADMIT koma ya prain pakatipa inakwela inafika 5pin.koma panopo chifukwa chakugwa mphava ya kwacha zatsikako ma 2.5 pena ma 2
Amuchepetsera kma achikhala mamuna ndiye zaka 6 aaaaaa mahule alibe ulemu
Amuchepetsera kma achikhala mamuna ndiye zaka 6 aaaaaa mahule alibe ulemu
akanyengedwe ndanyapala nd overstay kundendeko kkkkkkkkkk
Kkkkk koma abale
Zili bwino chibwana chimakanda opusa, wina kundende pamene wina nyumba katundu zidapsya, ulangidwilatu pasi pompano muyambepo kumdziwa mulungu muluona bwa!!!
Ameneyo amangidwe basi
Ndie mukuti hule wamangidwa chifukwa chotentha nyumba ya bambo wina? Hule wamangidwa chifukwa chotentha nyumba ya hule mzake, period. Mwamunayonso ndi galu wa munthu, osangokwatira bwanji???
Show
Anamukwela ulele
zachepa bola 5!!!
Mayi siwo lakwa olakwa ndi bambo yo kodi mayi yu akana patsidwa ndalama yake akana ka otcha nyumbayo kungoti anthu oweluza mrandu aku malawi zimakukanikani imeneyi sinkhani zili ngati ufiti zogonanazi öne mkazi sangango fikila kuti tiye tikanyengane kumuuza mamuna anayambitsaso nkhani yoka vulana ndi bambo khothi lakanika kuzenga mrandu mwinaso mayi yu poti analibe ndalama yokadisa ku khothiko kwaoweluza mutayeni mayi siwolakwa olo kuli n.dalayo akudziwa bwino kuli ieko kuti sanapange bwino apolice akana bwanji kumu ulula pamenepa akudziwa bwino bwino chilungamo zandi nyasa bwanji chifukwa munthu ali ese amadziwa kuti galu ukanponda nchila amakuluma iwe ndiku kanponda dala nde unga mayankhule kuti galuyu ndiwa chiwewe pomwe chiwewe chita choka kwaiwe sibwino pofuna ku gamula mrandu prz ku malawi osama ona kuti aujeni wa poti ana chenjela munthumba ndetika wakumbukile kukhoti ndiza pathako izi ndi ufiti chigololo sapangila pagulu pofikana kuti zitheke sizikhala zamasewela ayi ndi bamboyo olakwa pamenepo nkaziyo ndiwa bwino bwino ma hule samalola amafuna upelekeletu ndalama osana pange chili chose nde mayi wa kunali kutopa olo ndili ine ali ndi mwayi galu ameneyo olo akana mudikila amu otchele ku modzi zobayo apolice so aku malawi ndinu zitsilu kuphatikizaso ndi akhothi mwina kapena chifukwa choti ntchito zama siku ano mumango patsana kuntundu ndimbuli zomwe zoti ku maphuzilo sizinapite uzi ona zili ku police akuti zikugwila ntchito mukungo tipaka manyi simukumatha zokha zokha zama buzi anla
Samadanda azikagulisa kundende komweko ndimamudziwa bwino
Kkkk Azikagulisa Chani?Unena Bwinot Iwe
Iwe ndi huletu uyo kkkkkkkkkkkkk
Kk
Azikagulisa konko kumasinthanisa ndi sima kkk
Zaunsiru ma beach akuonjeza
vuto onse mahule khololao ndi kaliat nde sakuopaso mumuona atuluka ameneyo
Shashashasha hahahahahahaha
Hehede mpaka 2 yrs
MUNTHU NGATI UYU SIOFUNIKA KUMUSEKELELA ,MAHULE SIANTHU OWAPATSA UFULU , I WONDER WHY THE GOVt HAD DECIDE TO RELISH THESE INHUMAN LADIES . JUST TRUSH ALL THE BITCHES NOW AND WE’LL HVE A BETTER MALAWI.
Ukapanda Mano Usamaswe Phale Ngat Suenda Usiku Kulibwino Kungokhala Phee Azimayiwa Aliso Ndubwino Wawo Ngat M’modz Walakwisa Sionse
AAA KOMA IWE ! KUGONA NDI MAHULE NDIKUMENE KUKUPANGITSASO KUTI MA PROSTITUTES AZIPEZA ZISANGALALO KOMA ZOPANDA VISION .AZIMUNA NGATI INU NDIAMENE MUKUPANGA FACILLITATE PROSTITUTIONISM IN MALAWI .
Osayiwala kuti tili mmasiku omaliza, athu adzakonda zoyipa. ali ndi maso awone, ali ndi mzimu wachidziwitso adziwe basi.
Kkk
Eeeeeeeeeiiiiiiiiiiisssssssshhhhhhhh
vuto ndiufulu apasidwawo nde akuugwilitsa ntchito molakwika,muziawuzanso kut munthu akakhala ndi ufulu amakhalanso ndiudindo
MAHULE kp it up..!! mwina azibambo osakhulupilikawa asiye. osangokwatila bwanji??
Kkkkkkkkk no comment
Don’t say Madzi panyemba maman Dziko Linavuta ili!
Kkkkk madzi pa panyemba mwendo wake umeneo esakanachitila mwina
He deserve it Bambo! Court that’s unfair!!! PnPay business.
True @yonneck mbizi
Mukumanyenga mahule ndeosamapatsa ndalama et akamakuonchelan manyumbamo nde muzamanga apolice inu ndikhalidwelanu lomanyengela mphavu pasana panu mwanva
Hule,sanalakwe azibambo mumatiyalusa kwambiri chomupatsira map akunyumba hule ndichani???.azibambo amasikuano ndi ACHISIKA.wawachitabwino.
KKKKK Koma #mmadalo nkata
Tikasanthula bwinolomwe tipeza kuti osewa ndi olakwa, kukhala hule sichithu chabwino, kukhlaso mzibambo wama hule sichabwinoso. Ngakhale bible limakanitsitsa.
Hohohoho kuseka mwanjala kikikikiki ndipo inu,koma inuyo hohohohohoho
Amangidwe omweyo apite kukaidi. FROM LUSAKA ZAMBIA!
Kkkkkk..ukapolo oyendera vs ziwanda
Mahule afika pamenepa katundu waulele ngati ameneyo
Kkkkkkk koma ndie zachabe.mpaka pamenepo?
Kkkk! Kumenya Madzi Mwa Bure.
akolola zomwe anafetsa..sry guys kkkkkk zimachitika
kkkk hule siokwa amunge mdalayo bc amango browser alibe miracle money
Akuti anagwilzana ma round awiri ndi chingosha, koma game ya chiwiri ili mkati zinasintha, ada aja mkudya maround 4 plain, hule ameneyu amachaja k150 per nyekhu. Mpomwe panayambira nkhani….
Kkkkkkkkk kom
K150 per nyekhu, mmene zikunvekera mkuluyu analipira ya ma nyekhu 8, iyeyo ndikumenya ma nyekhu 21. Moti inaontchesa den ndi,defecit ya 13 nyekhu’s…amalawi ena kufuna udolo paliponse uyu waziona.
Please nigga..its mzimayi oyendayenda
Tchimo kuzunza ochita
Anakwela Zaulele,, Wakmananazo! 🙂
Kkkkk
Kkkkkkkkklkkkkkk mayo!! Mayo!! Nyasaland wataninso nanga
Akuluwo anapita kukagula malonda koma alibe ndalama? Hahahahaha! Anamuputa apa court lakondera. Mkuluyo anachitayo ndi theft by trick. lol..
Kkkkkkkkkk kasitomala kkkkkkkk kwa hule
Kumalipila zinthuzi mukadya, mapeto ake sizimenezo? loss of property
Hule mpaka kudziwa kunyumba kwa bambo some men they think around their balls
Like you Gravel Masinja
Kkkkkkk choka apa
Hahaha
Analitu kastomala kkkkkk
Nde kasitomala mpaka kudziwa nyumba Hahaha Hahaha Chiccago Firston Nguli
Mmmmmm
Eish eeeeeeeh
Mahule ena amakhala ojaira mpaka mwini mamuna kumamuziwa,nyumba yake nkumaiziwa,,chifukwa pofika pongongozana ndiye kuti zinapitilira pa 3/4 banja
Kkkkkkkkk mavuto
zovuta kumvetsa kwa ife achimidzi
Bola pamenepo
Ndiye anthu okondana amagulitsana chikondicho? Imeneyi inali bizinesi.
2 yrs yachepa mukanamutchaja 5 yrs
Mpaka kungongozana zomwezi,,, ndiye zalowa chisebwe,bamboyonso ndi olakwa bwanji amaputa vumbwe alibe nkhuku
Sanavane mitengo mphongo imafuna kusiya ka mpamba kandiwo wana amavuta akafika opanda ka bonya .hule amafuna waleti yose, kkkkk akabwela m’mwana kukaidiko kuli adzongue adadyela kale ma 1000 MK.
bolani pamenepo mauhe tsopano ayamba kujayila kwambiri mwina ena angatengelepo example
Hahahahahaha fair play
Walapa Ameye SaZathenthaso Nyumba
Bwanj sanamvane mitengo kapena bwanj?km sizoona kulipira Malawi mzako
Ndkamlipli Matuka Ameyo
Kodi bambowo amafuna adye zaulere mzawo ali pageni? Akhoti mukadamuganizirapo bwino mayiyu