Two people have died in Chikhwawa for drinking alcohol on an empty stomach, Malawi24 has learnt.
The two have been identified as Wyson Phokonyo, 30, from Ntwana village and Martin Mafunga, 29, from Chadula village in Traditional Authority Mlola in Chikhwawa.
According to Chikhwawa police, the two started drinking on 15th October 2016 as part of Mother’s day celebrations.
But the following day one of them was found dead at his house while the other died at Chikhwawa district hospital where he was taken for treatment.
Recently, a woman and a man from Balaka and Mangochi respectively also died due to drinking beer without eating food.
Drug Fight Malawi, an organisation that fight drug and substance abuse, has in the past been asking government to introduce regulations that would curb excessive beer drinking.
Kkkkk abro musatiyankhulitsepo mwano apa vuto siboma kodi mow a ndiboma kungoti chamba cangowaculukila m’mutu mwawo zausilu akhuta moyo asova.
Hahahaha kubwerea kwa mulungu oledzera?
Hahaha ndiye kuti afa ndi njala aiise
GOD IS GREAT AND GRITTER THROUGH THE world
Ine ndasiya dzulo kumwa mowa.
What kind of beer is that,, I understand dat u can drink beer on an empty stomach nd still live,, unless uve gone for days without food,, or the percentage is too high,,
They have died because of hunger not because of alcohol…. alcohol doesnt kill people…hunger does
So whats de prblem dea alcohol remains alcohol and empty stomach remains empty
Don’t ban beer but ban hunger bcoz it is the one killing ppo
So Bad!!
Kkkkkkk!! Zadala
The best thing its to stop drinking a lcohol to avoid some malawians to die.no matter mabwana enanu sukulu zanu ndalama zake makolo anuwo amphika ndikugulisa pelese yemweyo. lelo ma office inuyo kumatchedwa boss thats why ndinu mabwana osagwira mitu kuwasiya madam anu kunyumba kuma hopera creaner.mzelu zinasala mumpiya yamatokoso.
Moya sumapha OK ,nanga kuba ,chigololo,kusuta etc kodi mazi samapha?!????nowo tisiyekumwa empty stomach kkkkkkkk
UMBONI WA BIBLE, MUMASIKU OSILIZA,
Shooter mowa waukali zedi!
Instead of banning beer in Nyasaland Iguess you have to ban hunger which kills mo People in Malawi especially in dense overpopulation South region
koma nawonso akumakhara ndi ndalama yogulira Bawa mkumasowa yogulira chakudya zoona, zitsilu za anthu.
mowa umenewuu akanaletsa coz :ndi ma sachet omwe aja pano aika ma five litre bottles mkuma uti mkalabo:ngo ena akt boxer e:a shooter akufa achinyamata letsani mowa otchipawu chonde
AKUFUNA KUONONGA MBIRI YA MOWA,KUMWA MOWA USANADYE MCHIMODZIMOZI KUMWA MAMKHWARA AMPHAMVU USANADYE,
Guys dont talk mutch lets put them in hands of god
Alcohol controls are lacking in Malawi such that the populace thinks its ok to over imbibe. It is pathetic. The youths are the most affected..
congratulations
Anthu mowa adayamba kumwa kalekale, bwanji samafa nawo nthawi imeneyo? Ingolembani kuti akufa ndi njala. Akumwa osadya popeza alibe chakudyacho!
alcohol is the most dangerous legalised drug. It is far worse than cannabis
RIP WTH Mowa
Banning beer hahhaha,u must b crazy
Prz sizandale izi afa okha awa inde boma ndila mbola koma palibe anakatsazika ku boma kuti tiku kamwa mowa mayazi amati odya zake alibe mulandu amwelaso zawo afelaso zawo boma likamaletsa mumatukwana apa mukufa mudziti boma likulekelela anthu ake achinyamata kuti adzifa poti ndatsogoleli amawa kkkk ntengo ngati anakanika kuuongola uli waung.ono nde boma linga kwanitse ku ongola utakula kale siutchola
Chakumwa chasatana
mowa sumapha koma njala bax timaxiputa titadya bhobho oxakamba xamowa tingatemanepo mwava et
Kkkkkkkkkkkk
Its Unwise To Call For The Ban Of Alcohol Coz Sellers Do Not FORCE Anybody To BUY And DRINK Their Commodity. Just Tell Ur Citizen To Be Wise And Mature Enough When Taking That ‘free From Germ ‘ Product And Tell Them Its Difference From Fanta & Frozy.
Think before you do
Think before you start
Think before drink
Hello friends, my name is Esther Mashabai was one of those millions of people living with HIV/AIDS, i received my breakthrough with the help of Doctor Abumen whom i met through the testimony of someone he has helped, after some series of conversation with the person sharing the testimony i decided to contact Doctor Abumen which i did, after some negotiation he sent me the medicine with an instruction on how to use it, i notice some change in my body when using the medicine, after completing the dose as instruct i went for test only to be confirm negative by the doctor after the result came out, words on the internet can not express it all, if you are in the same condition and you are looking for a way out of it you can contact DR ABUMEN on his email address,([email protected]), or you can call or whatsapp via +2347085071418
mowa ochita kuyeza ngati paraffin utipweteka.anzako akumwa fanta iwe ikuitanitsa kafanta. i cry for my malawi
U can,t ban beer because others do not drink that beer and Malawi is a poor country we import some then the government gets interest because of beer
ine ndagura kake utatu eish! nkhani zakezo koma tilezeladi apa!??????
imwani koma musaledzele.ena samamvabe amamwa modutsa bible
Mowawo ndi wachabe komanso china njala yavutanso ndiye kangachepe wapeza gulani zakudya zokomera inuyo womwa mowa ndi mabanja anu. Chonde munthu wina aliyense ndiwofunikira ku banja lake komanso ku dziko.
sanadye ameneyo
Sizikufanana ndi ku banner mowa patumbo panu
zachamba ayiii…palibe ataletse mowaaa
Ziletsedwe zimenezo zoipazo
Izo nde zinaso,,, maliro akapolo salemekezeka, amasiyana ndi amwana wamfumu!
Those who drink on an empty stomach, do so at their own peril. No banning of alcohol in Malawi, you are now opening flood gates of smuggling.
koma guys. mtsinje umalimba ndi miyala
Anthuwa amwalila chifukwa cha njala osati mowa… mowa wo ndi umene unawapangisa kuti alimbekoso wezi ndi njala yo
kumwa sibalesa koma mwamwedwe mnthu ukudziwa zot sunadye basi kuuyambano kuusosola RIP
All the best alcohol Brewers keep it up
Beer be banned?????? Zachamba eti!!! Osangowalangiza kuti azidyela bwaa???? Timwa ma nip mpaka woooo
Don’t blame beer.they say DRINK RESPONSIBLY
Kkkkk! Malawi24 don’t make me laugh please. Ngakhale osamwa mowa amagwa ndi njinga man
So who’s to blame here, drinking on an empty stomach or alcohol???
vuto ndi njala osati mowa,chofunika kuuza anthu okumwao kuti azidya asanayambe kumwa komanso azimayi ogulitsa kachasu aziphikira makasitomala awo chakudya
I saw this mostly at nchalo trading….very awful..
Funso ndiloti anthuwo sankadziwa kuti mowa tikumwawu ndioyipa ngati sunadye kalikonse? tiyeni tiyesetse kudya kaye tisanayambe kumenya bawa.
Be serious for once pliz. Those people have died of empty stomach. If the stomach was not empty they would not have died. They have died of hunger full stop.
Anthuwa samwa mowa koma enthanol.
Koma silingakhale vuto la boma iyeyo amaziwa kuti mowa munthu suumwa usanadye basi akupita kumowa
Fuso kumati mukasiya mowawo mukuona kuti musove vutolo kapena kukhaulitsa company yopangayo
Lekani nikomoke na castle light
Am 19 Koma Ndikuwumwa Osati Sewero!
That’s why i salute my brother he always drunk with empty stomach but he never die
Kkkkkkkkkkk bwana kkkkk
Kkkkkkk bwanj boss?
kkkkkkkk koma yaaaa
shooter atipweteka eee
KOMA MOWA WAKE OMWE UKUMWEDWA LELOWO ANGAKHALETU KACHASO ANACHOKA PA CHASO, KUNGOTI MPHELANJILU. DZOMWE AKUPHIKA LELO NDI M’DULA MOYO WENI WENI. ANTHU ANGOTUPA NAZO.
On early hours of last Sunday, a woman in Mpemba ( Chadzunda), died after taking the same alcohol on an empty stomach and was laid to rest yesterday. This is true, hope Milare Police might have information on the same.
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk! Dis alcohol no good at all.
zoti munthu akafa ndi njara inu muziti mowa sizabwino
Kkkkk anthu amwalira ndi njala finish and kraa
DZINA LA MOWA LIKAKHALE SHOOTER INU KUMASEKELERA
eeee!!!!!shooter yekhayo nde leka,ndikamowa kabwino kaya kusiyana ndi zimowa zinazi.
Hahahaha kkkkkkkk asiyananayo njala amenewo iya nanga tiname hahahaha fokolo zawo amla shatapu !!!!
Boma la mtundu wanji losaganizira anthu ake, achinyamata omwe ali atsogoleli a mawa akutha ndi mowa opangidwa ndi enthanol ngati charger ndi anzizake, uku lili busy kulandila misonkho, anzathu kuzambia analetsa kale kale mowa umenewu atawuwona kuyipa kwake.
Those who are dying,is a matter of time. Their time has come to an end.
Zofuna izi go well
Naye Kumamwa Oxadyera Bwanji? Ngat Inasowa Ndalama Ya Ufa Bwanj Ndalama Anagulira Mowayo Osagula Chakudya?
Hahahaha Sindingasiye Bawa!! Sindingasiye Bawa Wafa Ndi Njala Ameneyo Osati Mowa! Kumanena Chilungamo Apa!!!
Kodi ndi mowa? Ine ndikuona kut ndi njala yasuzga ku malawi kwali
no beer no life
zolesa mowazo nde ay chibwana mapaz anu
Wy goin ku mowa on an empty stomach? vuto si mowawo bt okumwawo
Chibwana sikachaso ameneyu nde october aise hahahahahaha 45degree kutentha nkat Inno Ken G Namaona
What ever drink win shooter on a full stomach
let dem die to minimise de population
nsimowa koma empty stomach kkkkkk
Matumbo kulimbana ndizisulo ndimamuyami Chauta posandipasa ka Ntima kameneko kokonda Mowa amen
don’t mislead people they died cos of hunger not alcohol
ndiye bwin0 uzikuphani m0waw0 iyaaa muku0njeza ndip0 uphe ambiri ndithu m0wawu usasiye kuphak0
Nde iwe ukuona ngati osamwa mowa samafa? An empty stomach has killed them
Kwachema
ngati mungaletse Mowa pachifukwa choti anthu akumwalila nawo? nde lesaninso anthu kupita kunyanja pazisangalalo….bullshit