Traditional leaders in Blantyre under the umbrella body of Blantyre Traditional Chiefs Network (BTCN) have asked President Peter Mutharika to reverse his decision on the new land laws by calling Parliament to re-table the bill within 21 days.
This was said at a press briefing which took place at Group Village Headman Makata’s residence in the commercial city of Blantyre.
Speaking after the function, Group Village Headman Somanje who is also the Secretary General of the body blamed government for not consulting them to have a say on the new laws.
“We came to strategise on what we should do because people in our villages are against this law and us as chiefs we were not consulted and we are in total disagreement with this law that’s why we want the president to reverse his decision,” said Somanje.
He added that many Malawians are in total disagreement with the law because it seems to favor the rich while the less privileged and land owners in rural areas are the ones to suffer the most.
The event was attended by chiefs from different districts surrounding Blantyre.
When the land bills were tabled during the last sitting of Parliament, members of Parliament from the opposition side walked out of the chamber in protest and claimed that government was unwilling to consider their views.
Anthu akuba awa a dpp safunsa maganizo athu asanapangezinthu zawo pogulitsa bank anafusanda ?nanga ndalamazake ziliku? dzikoli anagulitsa kale ndalama anakhathula kale sakadakufusani maganizo kuopa muwasokoneza akaona ndalama amalorera kupha munthu kapena kulanda katundu bola matumba awo akhute basi akutitengera kumtoso ngati marilo anjoka.
mxiiiiii munthu wamkulu koma opanda nzeru
chitsiru
Y ppls call Him Bwampini o i see akuyesa ngati akakhazikisa land Bill ndiye kuti ziyenda mmmmmmm Mr president please mulungu atithandinze ngati mwatopa ndikulamulira let other ppls rulling de country
Leave the land to the government,not chiefs
simesa munavota nokha musiyeni president apange zomwe akufuna, amalawi kugona muzasiya liti kkkk
good news malo asapite mmanja mwa boma tingadzakhale pa vuto lalikuru kuposa omwe tili nawo panowa.
good news malo asapite mmanja mwa boma tingadzakhale pa vuto lalikuru kuposa omwe tili nawo panowa.
Mama P Kaliyati and you young Muluzi,would you plz take these chiefs to kuchawe Inn and civic educate them well about this good law? they are not conversant with this law.tell them all the land is in the hands of gvt if it is not leased and the gvt can come and say we're building a school at this land, no compasation or wat so ever or you go to court sukaphula kanthu.
Mafumu a mtown ndiakuba ndiye spa akuwona kuti zawo zada tsopano
Adyela mafumu akuBT kuteloko mukufuna ma envelope a ndalama
mafumu nthawi yanu osayang’ona munthu kepena udindo dziko ndi lathu mchona asatisokoneze mutu more fire osachita matha inu mulungu anakuyikani kutsogolo kwa anthu kuti zikamavuta inu ndamene mutithandize ili ndi pembezo langa ndi pemphero langa ulendo wanu mulungu akudziwa zimenezo osati akunyengereni kumeneko koma ngani zaanthu a nu
that’s good issue chiefs don’t loss our land like south Africa people we are Nyasaland mzuka Malawi dzuka ndipo ngat President alindimzelu zaumunthu atengapo mbali pakhaniyi keep it up chiefs osafooka kuyakhulako mpaka kumpandoko ayakheko … (My poor flames)
congraturations bt chiefs keep it up
Zikanakhala kuti mafumu onse n’ngwanzelu zotelo bwezi dziko lino litatukuka,
ok
Mafumu otsafuna zopusa ngati zinazi
mcthona wavutauyu.akulandamalo eeeee atipwetekamunthu uyu
mcthona wavutauyu.akulandamalo eeeee atipwetekamunthu uyu
Malo anga ndinagula ndi Rand osati kwacha ai ndiye wina akuchuluka nzeru ndizamusenga mutu ndithu
Vuto Ndandogwa,sindikuvetsetsa,??
Zaziiiii , anfumu amene atakapange zimenzo kwathu akakumanayo nkhwangwa .
Azolowe kudyara anthu amenewo. Land bill yisinthidwe fast
Zkodi Mp kapena president akafuna kulowa mboma amawafuniranji mafumu.
A wise chief chosen by God! Keep it up!!!
Amazing Race
Mtauni simukhala mzika,mafumu meachokela kuti, kuti muzigulitsa malo?Bwino apa
yes!! this bill is so evil end greats for the action of opposition during Parliament session though it doesn’t work. End I repent here that oooo!!!! I have sin for voting this DPP just coz of my tribe. For oppositions this is your time now for campaigning but look what you are doing hahahaha. …. Ochakwera nanu ndiye osava za anthu mmmmmm no good leader in our beloved country.
nthawi yosangalasa iyi…yomaonelela andale ndi anthu ake…ine anga malo palibe akatenge ndithu..agogo anga anathana nazo kale zonse..kulibe mafumu kapena boma koma ndi apamudzi wathu..zimenezo azikapanga kundatako osati ku mafarm aenafe.
maro molimbana ndinyanja ikupita ku tanzania mukulimba ndikufuna kubera anthu ovutika koma mulungu akutengeni anthu oyipa inu ozikonda opanda chisoni anyapapi abwampini akhakhakha muzafike kwathu kuzatorela chambarecho muzareka pomwe mayiko enawa akumenyera ufulu kuti akhare ndi maro awoawo mpomwee inu mukufuna kutiranda koma tilodzana ndithu chaka chino
Akatsutsa a mcp mumati ndi ndale! Bravo our Kings
Kodi mmene amapanga lamuloli anayamba anfusa ndani? Ngati mafumu asa kugwilizana nazo munawafunsa? Congratuation to the chiefs of blantyre keep itup please!!
kkkkk
Anthu ambili akhala akulandidwa malo ndi mafumu komanso achibale .Lamuloli lithandiza kuthetsa uchitsilu umenewu.
Tanenani maina a mafumuwo ndiwadziwe lero lomwe ndipite ku state house ufumu wawo uthe asssaaaa mufuna kusokonza DPP eti
atambasule tinvetse kulipo kunydira zosanyadira ikankhala nkhani yalent mafumu anayamba kale kulandira ukamanga nyumba akuti ukapereke ndalama
Amenewo ndiye mafumu anzeru.Tisalandidwe dziko tikuona ngati anthu aku SA amakhala mmothinana ngati makoswe kuuna.
nice thinking by mafumu
Mafumu anzeru amenewo! Dziko lisapite tikuwona ili.
tachioneni kunyasa
Hahaha mwatsekukano mmaso
So mafumu okha angavutike iwenso ulipamavuto ndi bill imeneyi chifukwa uzdilipira lend malo okhala ako.peza nthawi uyiwerenge usanapereke macoment ako opusawo
Ada Shuzi Imeney Ndimbuz Kwambir Ikungocomenta Koma Skudziwa Ichi Mchan!
Ameneyu Sanawelenge Akungowona Komwe Kukuchokela Kasimakambale Zotiakasiya Kumponyela Aliranawo Sakudziwa Galu Wachabechabe Ameneyu Ndakwiyanaye Kwambiri.
Ukudziwa Ben away ndi ana adzaziona
Mzangommana voti basi wakhaura, sathekatu uyu
Sinanga akudziwa kuti basi mchere watha sapezaso zammanja
Kkkkkkk mafumu sono akufuna ndalama za pitala