Malawi Police officers in Kasungu district are keeping in custody a 26 year-old woman who was found in possession of three bags of cannabis sativa which is locally known as Indian hemp.
Deputy Public Relations Officer for Kasungu Police Harry Namwaza identified the suspect as Agness Chisale.
He said Chisale was arrested on Friday 19 August at Chisazima Roadblock by police officers who were on duty that day.
Meanwhile the seized bags of Indian hemp will be taken to Chitedze Research for analysis and when tests confirm that the herb is the illegal drug, the woman will appear in court to answer charges of being found in possession of Indian hemp.
Agness Chisale comes Kantchere village, traditional authority Kayembe in Dowa district.
Ihate police
Malawi
Dont forget that Malawi Police is full of retards and psychotics
Mesa munkati munachita legalize chamba
zitxilu
ndikufuna mayina anduna zinaba ndalama za anthu ovutika mziko muno ndizitumizile mphezi zandikwana,,
kkkk malawi saza theka 3 bags chamba sanabe ka busines koti kazipezesa ina yake koma,,,
It’s unfortunate that they don’t know becoz they know not, no wonder they are always anti………..no one is above the law.
It’s unfortunate that they don’t know becoz they know not, no wonder they are always anti………..no one is above the law.
Don’t curse her that is a natural plant
Don’t curse her that is a natural plant
Arrest K577 billion cash gate Thieves.Imeneyo ndi nkhani nanuso
Mumusiye ganjayoso mubwenzele
Hmmmm ifeel xory fo my fellow poor malawians amene timazidalira tokha kusaka ndalama and thru hard working nkumatimanganso.Kod apolice mumafuna chan? Anyapala inu ntchito kumanga anthu osauka basi? What about nduna 7 zinja? Dikilan tiyambise Boko halam tizikudulan makos anuwo
Komatu chambachi chisasowe chili ku police.
TIMAPOLICE TOPANDA PHINDU ULEKA GWAPE NUKAGWILA CHIDINI UPUSA
240,billion komanso nyumba yaboma koma osamangidwa ndiye mukamange wachambayi?aaaaaa ayimmm,ntayeni Nate azitolele
Munthu wakana kuba uyo wanganya chakumumangıra palıje apa kamangenı dankha nduna 7 zıra zılıkuba ndalama zaboma lakusuzgıka ılı ıse tıkufwa na njala chıfukwa cha ıwo walıkuba ndalama zaboma awa panjı tıtı ma cashgaters awo munthu mulekenı uyo wana wakufwa na njala kunyumba sono wakukola apa na apa kutı wasange chakulya cha wana
Mesa mumati mwavomeleza chamba kulimidwa mu dziko..kodi tiva zingati ? Nde tiuzeni zoona zakhe mumangolemba chabe ….
Kusowa chochita basi.
Galu iwe tayankha apa shupit zako ndikubwera konko Dalitso Van Ma
sadziwa zoti anthu amagulisa ndikusuta chamba ndani ?
sadziwa zoti anthu amagulisa ndikusuta chamba ndani ?
http://earnwithinvite.com/index.php?ref=215799
Are u a student or jobless ? Have an online job here….click the link to register!
apa nde ndikuwona ngati apolice alakwa kwabasi,,zimayiyo ndi Malawi ndipo sanaphe munthu,,,musiyeni aliyese yemwe akulima CHAMBA akhale mwawufulu…
Ine akulephera bwanji kaya
What afearless lady i salute u on that cz thats not easy job
Sipanavute apa kungomufufuza wapoliceyo anakanga zimayiyo osamupha kungodula zanja kapena mwendo azizakumbukira kut wachita zolakwika
KODI INU APOLICE VUTO LANU NDICHIANI? MUNTHU MWAMULANDA KATUNDU WAKE KOMASO MUKUMUMANGANSO, WOSAMANGA ANTHU AMENE ANABA NDLAMA ZABOMA BWANJII NTHAWI ZAMBIRI MUMAZITUKWANISA NOKHA CHIFUKWA CHA UCHITSIRU UMENE MUMAPANGA
Pamkodzo pamu inu apolice, mzimayiyo walakwa chani? Inu simukuziwa kuti fodya ameneyi akhonza kulemelesa ziko lasaukisidwali? Mmalo momanga mbava za nduna7 zikulu zikulu zinaba moononga zija mukuziopa ndikumamanga munthu osalakwa musiileni mayiyo chambacho akagulitse apeze ndalama akagule chakudya inu simukuona njalayi??
akufuna adzi kamu gwililila nzimayiyo
Kodi inu munalora kulima chamba mukufunanso mudzigulitsa Nokha ?? Kapena mukutanthauza kuti boma ndilo lidzilima chambacho. BOMA lachamba ili
Legalise weed
apolice aku malawi sadzathekanso amathamangila za ziii mwalo momanga akuba ndalama za boma kkkkk malawi sadzathekanso
walakwa chani mzimai simesa ndalama mudabisa leave her alone mapazi anu apolice
chamba bax mpaka kumumanga? milandu ing’ono ing’ono nde mumathamanga kumangatu koma za nduna zija zimathera tifufuze kaye! ndende ndiza anthu osauka okhadi eti?
jst leave her waba zaboma?
bvuto lake m’matenga chochuluka pakamodzi…Rome wasn’t built in a day
Takamangani nduna 7 zija
Aww palibe chifukwa chomumangila mzimayi ameneyo amazinthandiza yenkha, Apolice pls takamangani anthu acashgate duna zija mukukanika kuzimanga zija issa shame.
Osangomusiya Munthu Akapange Ndalama Bwanj,nduna Zukuvutani Koma Akati Munthu Wa Business Ndiye Number One!
Mbuzi A za police mboli za manu kusowa chochita eti
Machende wanu apolisi! Kumanga munthu osalakwa bwanji?
Eti adha akamange munthu kamba ka weed? 😀 😀
Arrest cash gaters pliz. Makamaka nduna 7 zija ndi bwanankubwa wawo uja
sanalakwe musiyeni tikuchifuna kuno,tizabande ife
nawo mapolicia waku malawi wakamutola muzimai pankhani vachamba kusiya vakuba ndalama za boma.
Kodi waba katundu wa boma?musiyeni munthu bwanji nanga
tima police takumalawi kuno
Mulekeni amuke,mmesa chinapasa ku paliament.
Moti muzimanga zigawenga mukulimbana ndi munthu wamalonda
osamanga acash gate mukulimbana ndi wamalonda