…sex meant to heal her epileptic condition
The Magistrate court in Mangochi district recently convicted 47 year old, White Taimu to a 30 months jail term for incest which is contrary to section 157 of the penal code.
The convict who hails from Makula village in Traditional Authority Jalasi in Mangochi, had carnal knowledge of his 20 year old biological daughter with a belief that it would heal her epileptic condition and as a result of the act, the girl fell pregnant.
It was after this that the matter was reported to police who arrested the offender.
When passing the judgment, the First Grade Magistrate in the district, Ronald Mbwana stated that such acts cannot be condoned in society.
Malawi Police Service has since asked the general public to report such cases to the law enforcers as such behaviour is unbecoming.
Ife anthu aku Mangochi sitimaopa munthu, tili ndi ufulu kukwatira akazi ngakhale 7, bola kuwasamala onse chimodzimodzi.
Mitunduina amalola zimenezi sizachilendo
mahule onse ali kumenekowo akuchita kusowa anthu ngat iwe m’dala kupusa mpaka kubonza mwana wako.
atlest 25yrs
atlest 25yrs
Sleeping???
His name shows how stupid he is. White Time?
Ena Chingende Chimawavutadi. Moti Zakuti Mtsikanayu Ndiwakhunyu Simumvetse Munkhaniyi??? Internet Yaphwekadi Kkkk
Anthu Nd Makape Bwanj Mpaka Pamenep
Koma anthu ena ndioyaluka,,mtsikanayo ndiye amalorela bwanji
Akanampasa ngombe imukwane imukwane ameneyo
kwaaaaaaaa
Thats Tru And I Too Agree To That,mwina Midala Inanxo Ingagelelepo Apopo.Koma Amkululukilaka Ikanakala Hanz Months.
Thats Tru And I Too Agree To That,mwina Midala Inanxo Ingagelelepo Apopo.Koma Amkululukilaka Ikanakala Hanz Months.
khuku imamwa mazila ake
Whats wrong with us men?
chindele chakufikapo
Ayao ameneo
No no no wachewa nınthena no mahara munthu mulala wanyıvwı zake mbwe wakugona na mwana wake no no no nındapulıkepo ugalu wanthena uwo ıne chıwıro chane.Mukulenge na muwenge na mahala mukutılengeska sonı haa nachımwana wıwo kuvulıra dada wake mose vımıtı vambula phındu
Lkkkk 30months =2yrs 6months thts a joke! If it ws in my country Zambia tht man would hv bin slapped wt atleast 5yrs nd abov ..
Zaka zachepa, kugwilira ndi 7 kapena 14 why a slashed punishment lyk zat, when he goz behind bars n disclose to others who commited ze same claim, enawo akamva bwanji? Its not fear oooh!
Mjomba nde yake imeneyo musiyeni anjoye
Kodi kumangochi ndikwaachawa okhaokha? Maina amenewonso siamidyomba achawa samapanga usilu umenewo and ahell chilango miyezi 30 basi
Mdyomba kukhwimira uterara
Basitu mwanayo akawawona Bambi akewo piano sibambo akenso
Kunkhwima dyomba
Uchitsiru achawa akafere kundende konko
Stupid
I think anali mwana omupeza,
koma nkhani zogwililira zatikwana iyaaa
30 months! This is joke! Judiciary is not serious
Amafuna kukhwima ameneyo malinga ndi njalayi alemele mosavuta galuyo ife tikudya marand kuno
Amangidwe Kunthetsa nkhalidwe lopusalo
koma kumangochi mwafatsakotu, bola mtumbuka amakalamba asakudziwa madyedwe akatundu ameneyu.
Comment loading
Wadya iwe eeh wadya iwe, nanga wadya ndan zimenezizi…….
Kkkk stupid father mwina kufuna kulemera
Zeru za achewa zimenezo “no guts”
achawa ndichoncho
Upusaa!!! chitsilu kwambiri ndi mwanayo, kenako mzibamboyo, adatani kuuzilapo anthu ena iyeyo ataona kuti bambo ake eni eni akufusa zodya katundu??
Vuto ndiloti munthu wa khunyu nzeru zake zimakhala zoperewela chifukwa cha matenda.moti tisaganize kuti mwina nayeso anafuna ayi.its like he has slept with adisabled person.Bambowo alowe ndithu akaseve.
Mtsikanayo amagwa khunyu eeti?? Ok, bambo ndi ofunika kumumenya kaye makofi angapo, kuti akaseweze bwino.
Mwana Ali Lyt Mwina Anamuopyeza,O Analinxo Ndi Zlakolako Kale,nde Hu Reported About This To The Court.
Osati ufiti koma
nduchitsilu tambala
Koma ndiye mwafatsakotu kumeneko ….
nkhuku kumwa mazila ake shame on you
Mwina ndi hyena bamba ameneyo
Wadya kake alibe mbili paja amatero ankuluakuluwa
Anthu aku Mangochi amaonjeza kwambiri
Iwenso ndebola mdala yako ikachindira condom tu kuti usabadwe do u mean anthu amagwilirira kumangochi kokha
Mapwala ako
anthu osaphunzira akumwera ife kumpoto izo ayi anthu ndi asukulu
Nanunso musalakhule udyo apa. Mwaphunzilapo chani inu? Werengani mutu wa nkhani ndiye muyankhe osakamba zosephana
Timakati amtumbuka ndi agalu nde izi
Phunzirani kuzakuone ku blantyre
blantyre nditauninso mumene ukuonera sunayende blantyre ndi komboni kumaiko aanzanu
odyazake alibe mlandu kkk
lol,ngati panali kumvana pakati pawo m’dalayo amusiye
Amagidwe amaneyo ndichitsiru kwabasi
why arresting him wadya zake…
ife kwathu athu ameneo timati ndizitsilu zitsilu zenizeni zomwa madzi ometela ma ndevu..
eeeee zoopya2 hevy !!
Adagwirizana Chifukwa Munthu Wa Zaka 20 Zakubadwa Is Able To Make Decision, Tiwunikirepo Apa, Zavuta Chifukwa Pabwera Mimba, Pokana Kuchita Manyazi Amangitsana Osatitseka M’maso Tadziwabe.