News coming through to Malawi24 indicates that Malawi President Peter Mutharika has pardoned 243 prisoners across the country’s prisons.
According to a statement from the the Ministry of Home Affairs and Internal Security this is ”a symbol of forgiveness during this Year’s Republic Celebrations.”
”The prisoners who have been pardoned are those who have served at least half of their prison sentences, with good behavior and were not convicted of serious offences. Some prisoners have been considered for pardon because of their medical conditions.” reads the statement in part.
This comes hot in the heels of fears of continued congestion in Malawi’s prisons.
Eeeeeeeeee mbava zija zatulukaso shaaaaaaaa yalakwaso mtauni muja
Nd mbava za m’boma zomwe zatuluka nawo?
Podziwa kt mumagawananawo, wankhuku simumapindula naye
Ndie mutuluse okuba ndi mfuti kuleka oba nkhuku
To create space,baba tangomangani ma prison okwanila
Birds of the same feathers considers each other
Mistake””, Cellphones and ladies handbags on fire again “” let’s be aware
Do not lough at them, because may be tomorrow it’s u . Enanu ndiakuba koma kusagwidwa hahahaha monga ujeniyo ndinamvapo kuti anaba panti wa mkazi wa m’mwenye akumugwilira ntchito utame mwai kuti sanakugwire , nawenso ukanalowa hahahaha yebo
Amadya koma samakhuta kkkkk, .
Good there is overcrowding in prisons
Aaaaaa koma iwe peter 243 okhha basi
Ndende zakumalawi zodzadza ndi anthu ogwidwa vakabu ya masana.akakugwira akuonela video masana kumsika ndende shame.
Masulani ndalamanso big
Good news
Omweo basi?
Tivhutika
Loading….
After kuishosha yokwiya kkkk
hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651.
EE MWATULUKA KOMA MUKUMANA NDI NJALA. MUDYA ZITETE. KOMANSO SUGA, MCHERE ZINADULA. NGATINSO MUNASIYA MUNDA DZIWANI KUTI BOMA LINALANDA. KAYA MUNALI A TA SINDINUNSO CHALO AYI. MUKUVA KUWAWA.
zakumatako malo mokoza mavuto amene ali kumalawiko kumangopangabe zapachispethe
Early campaining.
400akuti 4000000
Mwathandiza kuti malo ogona RNA awapeze
Ndizofunika zimenezo.
So what can I do? Eeeeee fool…..
Once athief always athief.
waitha koma bola pasakhale wa cashgate ndi albino killer… tikawapeza tithananawo kunja konkuno
ationesa ukaidi wa umphaw
Slious abro inenso ndawona kale.
Thanks APM,,, zinayamba ndi muluzi zopanga pardonzi,,, continue.. You are a great man,,, UDF blood flowing in your veins,,
Thanks APM,,, zinayamba ndi muluzi zopanga pardonzi,,, continue.. You are a great man,,, UDF blood flowing in your veins,,
Oloko akutuluseni mudzatipezabe mwina nkhope zathu zatsoka
Oloko akutuluseni mudzatipezabe mwina nkhope zathu zatsoka
Achepa taonjezani fugure
Achepa taonjezani fugure
Albino killer among others,ok z not all de prisoners r guity!
Albino killer among others,ok z not all de prisoners r guity!
Welcom home azatibelenso ndikugwililira tiana mugetto muno!!!
Welcom home azatibelenso ndikugwililira tiana mugetto muno!!!
Kkkkkkkkkkk zandiwaza heavy
Zigawenga za dpp zatuluka ziphe ma alubino tsopano
Mbava kulusa mbava zinzake , lol .
Haaaaa onsewo? Aaaiyayi kwinaku nkupungula achulukisa
Thanx Mr President that’s a gud move
GOD IS ABLE.
Moti enanu nkuyamba kwanu kumva izizi
Amasowa chowadyetsa
Onse a cashgate aturuka!
zachambaaa
amalawi24 nkhani zonse zokhuza ndale basi?chanzeru palibe.
Luteponso watuluka
Bola kundende kunjaku kulibeko mtendere! Chibadwireni chamalawi zaka zitatuzi mwatilangadi!
Kenako mumva kuti Lutepo ali mgulu la anthu otulutsidwalo akuti wawonetsa khalidwe labwino kundende, lol
Kkkkk hahahaha, kodi nawenso utichani, Ukunena kuti achita bwino kuwatulutsa kapena Bambo ako alipompo paakaidiwo hahaha, akuumbuza uwona, Munthu akatulukatu mundende mutu sumagwira Oky.
to create rum for Kasambara
#Unimafeesmustfall
No ways…then kugwila mbava kulanga tokha ndi dzikwanje..
Palibe chimene nkuchiwona kuti nchanzeru, malo mositsa school fees ndikuthesa njala . Akuluwa Ali very weak in mind .
Too Let Mr President why doing dis on Freedom day
of course it is the duty of presdent to pardon the inmates but he must to do so only to those who are changed their behaviour
How can the president k ow who is or not changed the behaviour?
he has his minster on this issue who work everydy hence during this time of pardoning the minster is like superviser(kapitao) who xplains everything to his master on the work,so president is oso told by his minster who are suposd to be released
kkkkk ndietu kunali kuthamanga mpaka zitende kumagunda kunkhongo ati adzaona ngati anenanso kuti basi tasintha maganizo bwereraninso limenero ndilo dziko pamene ena akutulutsidwa ena akulowa achina Ralph kasambara
Kķkkk,Pasadi
kkkkkk kunalibe malo a Kasambara pano apezeka
Akutinso amene atulusidwawo pali Kasambara, Kumwembe ndi Manondo??? Tiuzeni zoona
Kuti ena apeze malo kkkk
Shaaaa mbava zalowanso mtown
243 prisoners, esh ! What is the plan of the President ? Did he already give them something to do ? He is not wrong but he was supposed to see how is he going to helping them, Otherwise those prisoners they are going to troubling other people. Now ,if we can see something wrong with these prisoners, Muthalika is going to be fired up, yeah ! Many Malawian people are well educated, we can even take Mr M. Usi (Manganya) to be the President of the Republic of Malawi. What’s wrong with you Muthalika ? Eee answer me ! Don’t you see that people are dying of hunger ? You are busy realising the prisoners instead of fighting for hunger are you normal ? You luck, because am faraway, Otherwise I was supposed to come there by ur place and shouting you a lot . I’m not afraid of you ! And this is beyond now. Think about the people who are dying of hunger and school fees , reduce your speed you can fall down B4 2019, you make me angry . Fuck Off !
Malawi is on fire bro
Ku prison ko ndiye akuuzani kuti amadya?
Koma ndiye ife ndiwongomvera basi,chitukuko chathu chamalawi chizingokhara chimenechi,
plus opha ma alubino nawo atuluka?
atululutsa alomwe okhaokha
U ve just made m day,u ve truly spoken well m brother life s so unbearable..@Phillimon Geoffrey Moyo
ouh does it include kasambara,kumwembe n manondo?
#Unimafeesmustfall#
Ma prisoners omwe atulusidwatu ndi a Cashgate only,not everyone_kkkkk
How do you know ?
Kkkkk,inu simukuziwa?
kasambala ali ndi mwayi kikiki mwina atha kukhala gulu lotulukalo Lol sizingadziwike
Better adziwapatsa kandalama koyabira ma businesses otherwise enawo ndi akabwelebwele.vuto lake uphawi ndi omwe wachuluka
A malawi aphempha nsomba mu ma university mu, akupatsidwa njoka, kkkkkk koma dziko ili….
kkkkkk including kasambala and the friends, any way I think it’s a matter of creating space for these new convicts.
nde chitukuko chimenecho zopepera peturo iwe .Ufa uli mwana
Bac ongotseka ndi ndende zomwe tisamveso mau oti prisoner chifukwa ena amenene akugidwa pakali pano nawonso azafuna kuti atuluke muzakaniza? kumeneko nde tikuti kuchita encourage upanda ndi ubava dziko lathu lino!
Not all prisoners are robbers or thieves
Vuto nloti enawa sananamuzilidwepo mpaka kumangidwa,every person needs a second chance
Many are Malawians who are dying in prison but they ain’t guilty
I’m happy with that people change everyday they even change
Yes @Robert I knw abt tht koma sibwino chifukwa azolowera kuti loko atimange tikatulukanso wayiona imeneyo
When u reached home please don’t it u gonna back to prison
thank u baba.
Kosowa choti unenepo. Kusangalira 6 July!
Welcome back to Republic of cashgate guys
???
wachita bwino munthalika nanga mbavazo malo moti zizasaka zokha zakudya zizingodya ndalama za boma ?zituluke ndiye zikatuluka ndikubaso tizaziyatsa ndimateyala tazisungira ..
Welcome to another kind of prison. i hope some of u in few days to come u wil not wish to go back coz of tough life. the good part now is dat u hv de right to dress wat u want, right to good shelter and even freedom of movement but when it comes to food, mmmm u wil wish to go back for sure
Kikikikik komabe asovera kunja konkuno
Kkkkk but its a gd move coz anadzadza kwambiri anthuwa muma prison
zozizzla bas,akfuna atzuze mmakwalalamu et
Zandale izi ndizovuta. Kaya zanu izo poti chomwe mukuchita mukuchidziwa nokha. Malawi walero!
Atizuzanso amenewo
kma pitala nde zichan nkhan yavuta nd yamalo kmaso ya fees ,wat kind ov human are u
Boladi asatizunzenso m’makomomu
Inuso mmabeledwa?ine dabwiiiiiii
Inuso mmabeledwa?ine dabwiiiiiii
Ndipo ndinkangova kuti anthu amaberedwa koma chaka chino ndaziona adachita kutitcholera nyumba masana
Ndipo ndinkangova kuti anthu amaberedwa koma chaka chino ndaziona adachita kutitcholera nyumba masana
Better
foolishness
Zaziiiii
kkkkkkk bola akhale amene anaba mbuzi aja guyz.
He is crazy muthalika
creating space for raphael ndi amzake
Bola asatinzunzenso mmakomomu mix munjira….apa alindimwana agwiritse.