
News coming through to Malawi24 indicates that Malawi President Peter Mutharika has pardoned 243 prisoners across the country’s prisons.
According to a statement from the the Ministry of Home Affairs and Internal Security this is ”a symbol of forgiveness during this Year’s Republic Celebrations.”
”The prisoners who have been pardoned are those who have served at least half of their prison sentences, with good behavior and were not convicted of serious offences. Some prisoners have been considered for pardon because of their medical conditions.” reads the statement in part.
This comes hot in the heels of fears of continued congestion in Malawi’s prisons.
117 thoughts on “Just in: Mutharika sets free 243 prisoners”
Comments are closed.


Eeeeeeeeee mbava zija zatulukaso shaaaaaaaa yalakwaso mtauni muja
Nd mbava za m’boma zomwe zatuluka nawo?
Podziwa kt mumagawananawo, wankhuku simumapindula naye
Ndie mutuluse okuba ndi mfuti kuleka oba nkhuku
To create space,baba tangomangani ma prison okwanila
Birds of the same feathers considers each other
Mistake””, Cellphones and ladies handbags on fire again “” let’s be aware
Do not lough at them, because may be tomorrow it’s u . Enanu ndiakuba koma kusagwidwa hahahaha monga ujeniyo ndinamvapo kuti anaba panti wa mkazi wa m’mwenye akumugwilira ntchito utame mwai kuti sanakugwire , nawenso ukanalowa hahahaha yebo
Amadya koma samakhuta kkkkk, .
Good there is overcrowding in prisons
Aaaaaa koma iwe peter 243 okhha basi
Ndende zakumalawi zodzadza ndi anthu ogwidwa vakabu ya masana.akakugwira akuonela video masana kumsika ndende shame.
Masulani ndalamanso big
Good news
Omweo basi?
Tivhutika
Loading….
After kuishosha yokwiya kkkk