Tough times are upon Malawians following the announcement by the Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) of a hike in fuel prices effective midnight, 10 June 2016.
Mera has announced that Petrol will sell at K788.30 per litre from K743.30 representing 6.05 percent increase.
Diesel will be selling at K766.90/litre from K 722.80 representing a 6.10 percent increase.
Paraffin will be selling at K609.80 a litre from K580 representing a 5.07 increase.
Pepani akuluakulu. Musalimbane ndi President. Malawi siipanga mafuta. Understand market dynamics. Mundifunse mawa ngati sitipezeka pa pump tikugula mafuta omwe anabwera mMalawi muno mwezi watha.
Kwezan pot mampanda kumaso alive problem
& u call this boma loganizila anthu…or lachitukuko…..
Think 4 the poor not just rise the price,mpaka pati?
To those who are saying kuti wakwera kuli konse do your researches well,kukwera ku SA and other two to three countries doesn’t mean wakwera dziko lonse. Even on Southern part of Africa countries like Mozambique the price ddint rise
Things will never go back.
It’s not knew .we get used now
Its international crisis….no need to blame malawi…always….we dont have oil wells here….we shld not forget!
Last days eeish
Why do we elect leaders here in Malawi & can somebody tell me what they do coz ths is bullshit at its best , who is manning our economy now?
Xry
fuel prices has gone up in all countries or may be only in malawi? this question goes to ministry of energy and mining.
Basi tiziyendera njinga ya kapalasa
kodi anthu inu mukukhala ngat izizi nzachilendo bwanji kuti nkhani ya chimalizilo cha dziko simuchidziwa bwanji??? As it is written in the scriptures that there shall be an increase of things so if this is happening why are you complaining instead of getting prepared for the eternal life,,,remember when Adam sinned against God,he was cursed that he shall work on hard labour for him to have his daily food,,,,so just work hard and lean on God the father,,,,,stop complaining,,,,this is just a foundation of an increase
kunono ku SA anakwera ndi ndi 50 cent per litre nanga kwanthuko akukwera chochi bwanj? dziko la malawi mwina tonse tinthaweko akhale wokhava bwanawo kkkkkk
Hlw amalawi
Zawonjeza Malawi mavuto osatha kalanga ine ndithawira kuti azanga
Palibe vuto ngati kuno Ku South Africa fuel wakwera katatu mondondozana pa mwezi iwiri yokha ndiye akanene kwathuko ku Malawi
Time for the Light is coming!!!!When there shall be no any sorrow.The whole world under one government!!!United world.Under one King(The Light)!!!.No poverty!!Cnt wait to see it coming.
u will never see that dark one world gorv. in ur life time
Its all over de world guys
Zachita kukwela nkoko kowengako,, muzizisata kaye osamakobwetuka apa,,,
Even here in RSA wakweranso palibe chodabwitsa apa
No where to go and no-one to blaim lets kp 4ward gentlemen, hopefully God ‘ll fight for us.
WINA DZIKO LIMUKANIKA KAYA. RUNNING A GOVT IS INDEED SERIOUS BUSINESS.
kulikonse Mafuta akwela inu koma umbuli onyoza boma udzatha ena mpaka maphuzo ndithu chonsecho olo galimoto alibe mkomwe u savage basi
By the end of apm term we shl buy pt at 2000,dz at 1700,pr at 1500,or more bliv it or not
nde nafe tikwezeso ama minbus
Ku RSA anakweza last week ndi 70cents /ltr nde tisamude wina kulikonse akwexa basi
Malawi suzgo pa suzgo.
Malawi suzgo pa suzgo.
Kukwera kwa FUEL sikuMalawi kokha nde sivuto lamunthu
Boma iloooooo !
ndiye a Kabanzanso tikweza ndi 50%
nanga dizilo
Zili bwino mafutawo samapangidwa mdziko lathu ndiye tikufuna profit yoti tikaodelenso
RSA FUEL WENT UP LAST WEEK ….KUMALAWIKONSO KWEDZANI BASI…
Fuel prices is changing now & then but the salaries is unchange
Even here in RSA fuel is up since last week, its not only in Malawi. stop blemming our government guys.
This is not government fault ,let’s grow up, we can’t blame government for everything,
Pa ntumbo pa Peter Mthalika galu wachabe ameneyo u professor wake uli pati tsono manyi ake tizivutika ndikuyenda nkomwe galu iwe ukutani makamaka pa mpandopo chitsiru cha munthu nde iwe chindere cha munthu nde iwe the most stupid person nde iwe by Bishop Zuza agalu obera boma mumakhala pa u president ncholinga muzibera boma pa matako pako ponunkha stupid mxiiiiiiiiiiiiiiii
mafuta sakweza masana koma usiku okha okha kuna basi mwayambaso
Mmmmmmmmm 788 yooooo ndinamusiya Ayi pa 234 ine yooooooo Malawi for Sale kkkkkkkkk
Amalawi muzasankhe2 president oti azatsitse zinthu ngati mungamupeze paziko lapansi
Ndimene malonda akhalira.
In RSA fuel is @ R10.89,equivalent to kwacha sikufika or six hundred nde I wonder why only in Malawi,Eeeeeeee koma mukutupweteka kwambiri
upange check bo bo petrol wakwera last week ndi 52cents moti akulu akulu akulu a transport akukambirana zokweza mitengo yokwerera makumbi
Muuzedi ameneyu 73 %petro n 52% diesel
Mtengo umene ndalemba pamenepo ndiumene ndathira diezel lero pa garage ya Elegeant fuels,200 litres lero leroli nde inu mukuti bwanji
MALAWI FAIL 0 PA HUNDRED
Pavuta apa, tingopakila tizithatha tathu, tifune ndalama tigule makapalasa basi
Chitsiru Cheni President
nde boma la DPP limenelo kenako tiyamba kulipila kuti tigone ndi akazi athu
Owelenga khala maso…..osadela nkhawa…we will never go back in old days…we are moving forward….lets go on…nothing we can do stop criticise.
Poor Malawian cannot afford to preserve anything.
ITS not only Malawi, each country, is in trouble, don’t u read the scriptures???? Kut zdzafka nthawi zowawisa??
Ku SA Kuno nako mafuta adakwela, koma petrol ali pa K600/litre kumalawi kwathuko ndiye zanyanyitsa
Asaaa!! Malawi tiri pa mavuto yooo!!!
Yooo ya iiiii. Koma
Wakwera kulikonse sikumalawi kokha
Simunati zikubwelaso zina pajatu mkulu wanuyo alibe pulobulemu ndiye eeeee
Guyz zikuongeza koma tkuganizilidwa?
ena inu tizakupatsan boma muzayendetseko too much tokota zilizose……
Nkhani ikhale yomakweza fuel basi asapangako zina malawi uyooo bolaso azungu anyasaland
alimi tidalakwanji? 80% ku malawi kuno chuma chathu chili nthaka
nde iwe ukuti R12 malawi kwacha ndibwanji imeneyo ukuyankhula ngati posintha sukudziwa zoti akutchipa kumalawi sukudziwa ayi nanga asanakwere ndekuti kotsika kwambiri kunali ku malawi
iweso nde mbuzi yopanda teeth 12*45 upeza makwacha angati???? or kugeli sunavayeko unangopita ku Theba pa truck bac,,,,,wandibowa ndi comment yako
zikomo bwana pamayankhulidwe anu ndine mbuzi yopanda teeth mukadadziwa kuti RSA mafuta awo amakanyamula okha pa ship while malawi amanyamula atanyamulilidwa paship sibwezi mukutero ayi mafuta kumalawi amayenda pa truck from Nampula or Durban RSA kukafika kumalawi or sindingafane ndi tanzania ayi and mafuta kunonse akweza last week while malawi akweza lero komanso kuti K788.30 muyike mukwacha its about R15 basi nde ayi ine mbuzi achikulile koma samalani mayankhulidwe anu mafuta ndi world wide even Nigeria akudandaula basi komwenso kukuchoka mafutako kuti akwera kwambiri
kkkkkkkk N’CHIYANI a MALAWI? Mukanakhala inu mukanatani?
Nthawi yake.Kodi mumafuna angokhala pomwe paja? Zinazi kumangovomereza bax.
Malawi!
Thats Malawi the home of cashgate!!!!
Is there any one who would like to buy Malawi out there? Maybe it’s time, coz only Kamuzu manage to run it, my opinion
izi zikuonesa kuti kunO kwathu kuli nkhondo because mavuto omwe akukumana nawo anthu akumaiko komwe kuli nkhondo sizikusiyana ndi athu kuno chifukwa chili chose chimakwera mtengo mmene akufunila kotero a malawife timavutika kwambili za chisoni ndithu
Tipangebwanji bwana kuthetsa nkhondoi. Asaname kuno kubotswana kulibe kukwela ngati kumalawiko
kuba bas mulungu angoti menyela nkhondo ngati ija ya 2012
It is normal. Did you think that fuel price will never rise till when? It is a global crisis not Malawi only!
Muzipanga follow world economy on international channels osamangowawata zopusa. Ngati mafuta akwera ku Nigeria kwao kwa zitsime.
Again koma pa Malawi
Kmatu mzimu wa kamuzu uzavuta nthawi ina kkkkkkk apanso sugar, mbatata, nandolo zikwelanso! Mera ikungofuna kumapezapo masalaries awo basi.
bcz of dpp gvmnt & pitala mr nilibe problem
Ndiribe problem, anthu ankayenda wapansi kupita ku theba samalakwisa!
I am not scared or hestate with the hike of fuel. I am a Malawian bonafed no where to go. I born and I will die here no matte how tuff things will b no runaway. This tuff times were arleady pridicted in the bible
That they will be no Fuel in Malawi?
Znaztu osamalinamizira bible
Chilichose bible, ndi zopusa zomwe
Lets nt compare MW wth countries lk Moz,TZ,ZA don’t we know kut Malawi is land landlocked country chilichonse chkamalowa muno boma lim?aononganso ndalama zambiri lets change our mindset of critsizing alwayz
Mudzipanga comment after mutafufuza. Don’t you know that Zambia is a landlocked country?
Tell him broza peter,mwina geography simunatenge ku xul et?
Kkkk,Zambia is also a landlocked country
and Zimbabwe too
May be iye sizimukhudza.
Ine mwina ndi mbuli koma apa zaonjeza !!!! Geography pliz
koma yaah sitinati!
Masiku otsiliza Yesu Khristu wayandika…..tsoka okwanilitsa mayembayo
Uku Ndkuonjezer Mavuto Pamavuto Azake
Koma Tilimba? Dzulo Kwathu Kuno-jenda Anasowelatu Pa Filling Station..Ndagula K 1000 Per Litre Ku Wa Vendor…Tien Tipilire, Nanga Tipanga Bwanji?
Kubako
kukhala m’ Malawi ndikulimba mtima
Mavuto alipo basi
Reformation at its best
No wonder sizachilendo kwa ife amatero asiyeni ndi nthawi yawo olo muwalankhule sangakumvereni
Only Kamuzu knew Kwacha
Only Kamuzu knew Kwacha
NDE Malawi too! sikuza sintha
NDE Malawi too! sikuza sintha
Mayiko Ena fluel ndi otchipa monga moshoko Zambia Tamzania mtengo wake siufika 600 per litre koma timakaoda kofafanana boma lamalawi kuba basi
Mayiko Ena fluel ndi otchipa monga moshoko Zambia Tamzania mtengo wake siufika 600 per litre koma timakaoda kofafanana boma lamalawi kuba basi
Mayiko Ena fluel ndi otchipa monga moshoko Zambia Tamzania mtengo wake siufika 600 per litre koma timakaoda kofafanana boma lamalawi kuba basi
I get your your point kooda kofanana but tieni tone ku tz akangotsitsa mu port sayenda mtunda wautali koma ifeyo kuno timuchotse ku dares kudzafika kuno how much will it coast ?so am not against your your point.pena pake akutionjezadi anthuwa
Late us pray to God we should be like a Zimbabwe otherwise we will suffer like never b4
Zinthu kumangokweza,malipilo nde ndiomwe aja eish!!its 2 bad
Tough times indeed!
Ha Ha Ha Mukafuna Madala Tinazo Tizithamanga Ndizugumbu Soon
No problem paja tilibe zisime……
Tiyisova !
Eish ndalilira malawi
Mpaka mk800 per Ltr? Pamene kuno anthu akudandaula koma ali pa r12=mk500 almost.
Man economy ya SA and MW ndizosiyana,kumangovomeleza basi mpaka tifika pa Zimbabwe
Zoona Man
Am not an economist but a couple of months the price of crude oil on the international market has been low/ decreasing. MERA dd not reasonably reduce the price here in Malawi to match the trend on the internal market. This week, the price of oil has slightly increased on the intl market, immediately, MERA has increased it too. May i be schooled on wat has triggered this increase???? obviously, prices for commodities will increase ( at least from my past experience). From this perspective, i call upon the government to revisit the the proposed increments for civil servants to match the current inflation rate, the continuous increase in prices of commodities,…. as the buying power of the kwacha keep on loosing value
Fact!!
Aiming @ making bzness not assisting Malawians
Aiming @ making bzness not assisting Malawians
Aiming @ making bzness not assisting Malawians
This country of ours nothing good
This country of ours nothing good
This country of ours nothing good
Apm Has Failed To Manage The Country
Malawi forward ever backwards never…
Awa akufuna tithamangeso,why do these politians always wait for action to change things..
i can see they look at increase only not reduction, pain to Malawian with our low income
Eeeee Ambuye atichitire chifundo
Where r we heading to?
Its not only Malawi its now up to many.
Nde malawi ameneyo kukweza samakaika koma muti asise salolanso
Every iterm goes on sky high but still no money in some pocket , slave continue.
tikakumana ku msewu konko Olo afike Mk20 000 / L sikt tingasiyende kuthamanga ai .
Same here in Nigeria
One of the poorest it the world iz mw shame.
Zambia its K9.87n
DPP..Chitukuko,Chitetezo,Chilungamo…Tell us again.
amalawi munangozolowera kunyinyirika zili zonse muziyenda muziona mmene zinthu mmaiko anzanu mmene za kwelera ntengo maiko ena fuel wakwera katatu chaka chino chokha ndipo akuyembekezeraso kuti akweleso ntengo
tell them
U R TRU BIG MAN.SAKUDZIWA IWY KWAWO NDIKUNENA NGATI OZINDIKIRA.
True,unfortunately ……loading comment
NDE kuno akukwera kachingati. Apapa?
mpha chaka chino akwera kangati mafuta kumalawi? ndipo ma transport akweza kangati? kumayamika nthawi zina
Nde awowo akukankhawo alibe ya fuel? Kapena anatenga ya mtengo wakale nde yapelewela basi aKupita?
Yapelewera k50
Kkkkkk agulitse mirror imodziyo basi ipezeka
kkkkkkkk
palibe chokoma chili chonse kuno kwanthu ku malawi.may be akufuna ku bweza zija aononga ku moqz.kunkhala malawi ndikulimba mtima bac
Ziyambikanso zija zomagona muma fuel station.mmmmm! Malawi wanunkhila ngati mvula yogwela kutali.poor managing of government put Nyasalandi again in trouble yes! indeed you are a professor.
Ziyambikanso zija zomagona muma fuel station.mmmmm! Malawi wanunkhila ngati mvula yogwela kutali.poor managing of government put Nyasalandi again in trouble yes! indeed you are a professor.
Naweso iwe Frank amati muma fuel station sukuludi yanyasalandidi koma futsa azigogo ako ngati alipo akuwuza zomwe akaziwona those days but today life sweat
Kkkkkkkkk leeeeeeee…. Ziggy, eti fuel station
nothing wrong wth that(fuel station)filling station its general coz u can find gas,fuel&many more.wat mataz is a figure of speech.inunso kafunseni ambuyanu
malawi is on fire because sugar nayonso akweraso mmtengo kufika kusonga ndipo tizigula k1000 mayi ine malawi
Kodi ku malawi amawenga mafuta???? Mafuta akwela mtengo padziko lonse check the price of blent cruide oil
100&osadziwa ndinu cause (fuel station en filing station is de same) is a place where you can find this tin like this ting petrol,gas paraffin and diesel.
kkkkkkkkkkkkkkk! ndakufilani madolo.
Nothing wrong. Sometimes it’s called a gas station
Thieves
Osamangoti Malawi akupita kuti mayiko ambiri padziko la pansi katundu akukwera nde poti Ku Malawi zakwera zinthu yikhale nkhani
Zambia loading malawi wandikanika
its time,ma transport adakweza kale
Zambia loading malawi wandikanika
Zayang’ana ngolo,esh!
Ndidamva wina ananena kuti chuma chikuyenda bwino ku state house kokha ena kumasutsa si izi kodi?
Malawi wanga ukupita kuti? shaaaa kukhaladi mmalawi ndikulimba
malawi where are going
Olo mutamagulitsa k1,000.00 pa lita sikuti anthu apachika zokwera.
Anzanu anakwela kale, komaso amasisa koma inu simusisa nchifukwa chake ali pamenepo
Even here in south africa akwera last week nde mukudabwa chani US dolla ili ndi mphamvu
price?
kkkk creativity at its best
shaaaaa Malawi
kuno tiugula 11.2 Rand peR litre petrol musova
ankolo sibho.. ife $1.2 litre hahaha
Kwanu nkwanu mudalaka njoka mthengo…tizasovela limodzi man..
@ Rich Armson EG Gomani,I dare call u a slut,disgrace,sell out,who isn’t concerned with affairs in ones homeland 4getting dat ‘no bird flies 4ever’,yet u expect us 2 sympathise with u when zenophobia strikes.1 who hides in nebas house when his is on fire 4getting it will also catch fire or u’ll outlive ur stay.I thought u’re capable of constructive criticism.Enjoy while the cake lasts.
we were born poor we shall die poor no mata how u work harder in a foren cantry
Eeeeeee
Kkkkk Chithumzicho ka 6.5 komweka??
Koma kumalawi kwanukha
RSA here i come