Fuel prices up

Advertisement
Malawi fuel prices up
Malawi fuel prices up
Hard times ahead

Tough times are upon Malawians following the announcement by the Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) of a hike in fuel prices effective midnight, 10 June 2016.

Mera has announced that Petrol will sell at K788.30 per litre  from K743.30 representing 6.05 percent increase.

Diesel will be selling at K766.90/litre from K 722.80 representing a 6.10 percent increase.

Paraffin will be selling at K609.80 a litre from K580 representing a 5.07 increase.

Advertisement

187 Comments

 1. Pepani akuluakulu. Musalimbane ndi President. Malawi siipanga mafuta. Understand market dynamics. Mundifunse mawa ngati sitipezeka pa pump tikugula mafuta omwe anabwera mMalawi muno mwezi watha.

 2. To those who are saying kuti wakwera kuli konse do your researches well,kukwera ku SA and other two to three countries doesn’t mean wakwera dziko lonse. Even on Southern part of Africa countries like Mozambique the price ddint rise

 3. Why do we elect leaders here in Malawi & can somebody tell me what they do coz ths is bullshit at its best , who is manning our economy now?

 4. kodi anthu inu mukukhala ngat izizi nzachilendo bwanji kuti nkhani ya chimalizilo cha dziko simuchidziwa bwanji??? As it is written in the scriptures that there shall be an increase of things so if this is happening why are you complaining instead of getting prepared for the eternal life,,,remember when Adam sinned against God,he was cursed that he shall work on hard labour for him to have his daily food,,,,so just work hard and lean on God the father,,,,,stop complaining,,,,this is just a foundation of an increase

 5. kunono ku SA anakwera ndi ndi 50 cent per litre nanga kwanthuko akukwera chochi bwanj? dziko la malawi mwina tonse tinthaweko akhale wokhava bwanawo kkkkkk

 6. Time for the Light is coming!!!!When there shall be no any sorrow.The whole world under one government!!!United world.Under one King(The Light)!!!.No poverty!!Cnt wait to see it coming.

 7. Pa ntumbo pa Peter Mthalika galu wachabe ameneyo u professor wake uli pati tsono manyi ake tizivutika ndikuyenda nkomwe galu iwe ukutani makamaka pa mpandopo chitsiru cha munthu nde iwe chindere cha munthu nde iwe the most stupid person nde iwe by Bishop Zuza agalu obera boma mumakhala pa u president ncholinga muzibera boma pa matako pako ponunkha stupid mxiiiiiiiiiiiiiiii

  1. upange check bo bo petrol wakwera last week ndi 52cents moti akulu akulu akulu a transport akukambirana zokweza mitengo yokwerera makumbi

 8. nde boma la DPP limenelo kenako tiyamba kulipila kuti tigone ndi akazi athu

 9. Owelenga khala maso…..osadela nkhawa…we will never go back in old days…we are moving forward….lets go on…nothing we can do stop criticise.

 10. nde iwe ukuti R12 malawi kwacha ndibwanji imeneyo ukuyankhula ngati posintha sukudziwa zoti akutchipa kumalawi sukudziwa ayi nanga asanakwere ndekuti kotsika kwambiri kunali ku malawi

  1. iweso nde mbuzi yopanda teeth 12*45 upeza makwacha angati???? or kugeli sunavayeko unangopita ku Theba pa truck bac,,,,,wandibowa ndi comment yako

  2. zikomo bwana pamayankhulidwe anu ndine mbuzi yopanda teeth mukadadziwa kuti RSA mafuta awo amakanyamula okha pa ship while malawi amanyamula atanyamulilidwa paship sibwezi mukutero ayi mafuta kumalawi amayenda pa truck from Nampula or Durban RSA kukafika kumalawi or sindingafane ndi tanzania ayi and mafuta kunonse akweza last week while malawi akweza lero komanso kuti K788.30 muyike mukwacha its about R15 basi nde ayi ine mbuzi achikulile koma samalani mayankhulidwe anu mafuta ndi world wide even Nigeria akudandaula basi komwenso kukuchoka mafutako kuti akwera kwambiri

 11. izi zikuonesa kuti kunO kwathu kuli nkhondo because mavuto omwe akukumana nawo anthu akumaiko komwe kuli nkhondo sizikusiyana ndi athu kuno chifukwa chili chose chimakwera mtengo mmene akufunila kotero a malawife timavutika kwambili za chisoni ndithu

 12. Kmatu mzimu wa kamuzu uzavuta nthawi ina kkkkkkk apanso sugar, mbatata, nandolo zikwelanso! Mera ikungofuna kumapezapo masalaries awo basi.

 13. I am not scared or hestate with the hike of fuel. I am a Malawian bonafed no where to go. I born and I will die here no matte how tuff things will b no runaway. This tuff times were arleady pridicted in the bible

 14. Lets nt compare MW wth countries lk Moz,TZ,ZA don’t we know kut Malawi is land landlocked country chilichonse chkamalowa muno boma lim?aononganso ndalama zambiri lets change our mindset of critsizing alwayz

 15. Koma Tilimba? Dzulo Kwathu Kuno-jenda Anasowelatu Pa Filling Station..Ndagula K 1000 Per Litre Ku Wa Vendor…Tien Tipilire, Nanga Tipanga Bwanji?

  1. I get your your point kooda kofanana but tieni tone ku tz akangotsitsa mu port sayenda mtunda wautali koma ifeyo kuno timuchotse ku dares kudzafika kuno how much will it coast ?so am not against your your point.pena pake akutionjezadi anthuwa

 16. Am not an economist but a couple of months the price of crude oil on the international market has been low/ decreasing. MERA dd not reasonably reduce the price here in Malawi to match the trend on the internal market. This week, the price of oil has slightly increased on the intl market, immediately, MERA has increased it too. May i be schooled on wat has triggered this increase???? obviously, prices for commodities will increase ( at least from my past experience). From this perspective, i call upon the government to revisit the the proposed increments for civil servants to match the current inflation rate, the continuous increase in prices of commodities,…. as the buying power of the kwacha keep on loosing value

 17. amalawi munangozolowera kunyinyirika zili zonse muziyenda muziona mmene zinthu mmaiko anzanu mmene za kwelera ntengo maiko ena fuel wakwera katatu chaka chino chokha ndipo akuyembekezeraso kuti akweleso ntengo

  1. mpha chaka chino akwera kangati mafuta kumalawi? ndipo ma transport akweza kangati? kumayamika nthawi zina

 18. palibe chokoma chili chonse kuno kwanthu ku malawi.may be akufuna ku bweza zija aononga ku moqz.kunkhala malawi ndikulimba mtima bac

 19. Ziyambikanso zija zomagona muma fuel station.mmmmm! Malawi wanunkhila ngati mvula yogwela kutali.poor managing of government put Nyasalandi again in trouble yes! indeed you are a professor.

 20. Ziyambikanso zija zomagona muma fuel station.mmmmm! Malawi wanunkhila ngati mvula yogwela kutali.poor managing of government put Nyasalandi again in trouble yes! indeed you are a professor.

  1. Naweso iwe Frank amati muma fuel station sukuludi yanyasalandidi koma futsa azigogo ako ngati alipo akuwuza zomwe akaziwona those days but today life sweat

  2. nothing wrong wth that(fuel station)filling station its general coz u can find gas,fuel&many more.wat mataz is a figure of speech.inunso kafunseni ambuyanu

  3. 100&osadziwa ndinu cause (fuel station en filing station is de same) is a place where you can find this tin like this ting petrol,gas paraffin and diesel.

 21. Osamangoti Malawi akupita kuti mayiko ambiri padziko la pansi katundu akukwera nde poti Ku Malawi zakwera zinthu yikhale nkhani

  1. @ Rich Armson EG Gomani,I dare call u a slut,disgrace,sell out,who isn’t concerned with affairs in ones homeland 4getting dat ‘no bird flies 4ever’,yet u expect us 2 sympathise with u when zenophobia strikes.1 who hides in nebas house when his is on fire 4getting it will also catch fire or u’ll outlive ur stay.I thought u’re capable of constructive criticism.Enjoy while the cake lasts.

Comments are closed.