You see, when people say that the economic times are hard in Malawi now, they could give you a few example, but this one is one of a kind.
Hell broke loose on Sunday when a lady (name withheld) was caught stealing money at a wedding at HHI Hall in Blantyre, Malawi24 has learnt.
According to a source, the lady pretended to be part of the team that helped to pick the money splashed by people to the newly wedded couple only to be caught by the lens of a camera.
”She pretended to be on the people who helped in picking of the Pelekani-Pelekani money. But the camera man who was shooting the proceedings, noticed that she could put some of the money in her pockets’ a source told Malawi24.
With the help of police officers who were at the wedding, she was interrogated and admitted to have been stealing at a number of weddings in Blantyre in the company of her friends.
According to reports, she has since been arrested.
Maludzi
ndinali konko koma mayiyu sanamangidwe! mkwati adalamula kuti akhululukiridwe.
ndinali konko koma mayiyu sanamangidwe! mkwati adalamula kuti akhululukiridwe.
ndinali konko koma mayiyu sanamangidwe! mkwati adalamula kuti akhululukiridwe.
Kdi mukamuzega mulandu otani otola ndalama pa ukwati kapena? wakuba? Osagwila a cush gate anja bwanji?

Let her do her business.Without that her family cannot survive.She went to xul of this and has diploma in cash wedding steeling .Ndiye pataunipo.

inunso aboma osakawamanga akutiphera azibale athuo bwanji mukulimbana ndi mzimayi otinso wabereka mwana kumbuyo osanva chisoni bwanji
Wedding gate kkkkk
hahahahahaha
Kwacha yavuta
Wed-gate kkk bt azimayi musamaonjeze
Mxm kusowa cholemba chani?ndalama zobedwa mdziko mukulephera kuzitsata ndye mukalembe zopusa ngati zimenezi
Boma linalesa kuponya ndalama pansi nkumapondapo so she was just helping kutolera ndalama nkuziika malo abwino amaopa anthu aziziponda ndalamazo.
The woman is a day light robber denying new couples chances to recoup what had been spent on the function must be taken to task to discourage similar offenders
Anthu amaba mkachisi what more ku ukwat?useless
sanabe amangotola aba bwanj eni ake ali pompo
Howard Johnson”s Hotels,Toronto is now recruiting workers from around the world for their June/July session to fill in these vacant positions : Receptionists,Room service,Pool management,Kitchen references,Securities,Gardeners,2Cashiers and Hotel drivers….forward your cvs to [email protected] if interested….or
contact us on whatsapp +16474920576 ….for interested applicants from africa call or whatsapp our west african representative on +221708781126 or forward your cvs to [email protected]….Goodluck….

Isn’t there any opportunities for truck Drivers as well?
Akazi kukonda ndalama chifukwa chakenso amadulitsa chigololo….eeeeeeee
Mtayeni sinkhani imeneyo and mukamumanga remember to take care of the baby on her back plz
Mtayeni sinkhani imeneyo and mukamumanga remember to take care of the baby on her back plz
Nkhani yovuta kwambili ntchito zikusowa nanga nkutani? Sanalakwe amati uzadya 2kuta lako naye 2kuta lake limenero, sha….koma mama mpaka pa ukwati.
vuto siiwo kma umphawi.
vuto siiwo kma umphawi.
palibe vuto mam
palibe vuto mam
huleyo amakatani kumeneko? mada fuck inyo ya magho umaswe fkn
huleyo amakatani kumeneko? mada fuck inyo ya magho umaswe fkn
maluzi akakupweteka timatenga ma option ngati amenewa bola utakhala ndi kena kake n’thumba.koma a police musange anthu chifukwa budget yake mwayiona kale.
Mwina anafuna kuonjezera pa airtym
koma dyerarinali
ki ki ki
Bola kubako kusiyana ndikucita uhule
kalipo kagulu ka azimayi kakuba mzikwati amagawana kupita madera osiyana siyana amayenda awiri awiri nkofunika kumachenjera amakakamira kuti auzidwa kukhala nawo ma cashier ……muzikhala tcheru angazakubereni.
Sorry
imadya pomwe yasungidwa
kkakaka koma azimayi enawa
Ndalama za pa ukwati zilibe mwini wake ukwati sibizinesi ndi macheza
Pa liu loti “anaba” ayenekera kukageba basi. Likanakhala liu loti “anatenga kapena anatola” tikanati akabweza zatha. kuba kumayambila pakang’ono kumakula.
Don’t make me lough kkkkkk is that true?????
Hahaha nde paka police waba zingat
Shaaa! Ameneyu ndiamene anandibera ‘one million kwacha’ paukwati wanga eti?
How much she is that fucken stolen money?
Pa ukwati some women take advantage to sell but it is not good to do that,muganize ndalama zomwe wawonga zanuyo kugwa mungongole,chikhalidwe tamusiyirandani amalawi
Hesh ndi tumizileni number 4n nditumiza pa Mukulu lelo pompano osamanga bby gys bwanjikodi
Then hw many yrs in jail with hard labour??
12yrs
kkkkkk ok?
She was trying to use my proverb”stealing can pay once u never caught” nde wazionatu ndimangonama ineeee!! Stealing does not pay!!
azimayi nanu mumaonjeza kupita ku maukwati! ukwati wina ulionse basi muli konko
koma nun new axse
koma nun new axse
Kkkkk kungomva kuti mbuxi imadya pomwe ayi mangilila eti hahahaha you got jokes ma’am
Kkkkk kungomva kuti mbuxi imadya pomwe ayi mangilila eti hahahaha you got jokes ma’am
Iyi sikhani yoti paka amagwidwe.anthu amaba maukwati kumene sizachilendo izi.molo molimbana ndi omwe akupha anthu mukulimbana ndi otola ndalama kuukwati? Stupid u boma.
Iyi sikhani yoti paka amagwidwe.anthu amaba maukwati kumene sizachilendo izi.molo molimbana ndi omwe akupha anthu mukulimbana ndi otola ndalama kuukwati? Stupid u boma.
Pali Nkhani Yaboma Apa?Its A Woman Against Wedding Owners
Apolice ndiye bomalo.ngati sumadziwa mudziwe lero
Mesa ali manja mwa apolice sali manja mwa anthu amene amaonera ukwati koma ali manja mwa boma
WALAKWA CHANI APOLICE MMENE AKUBERA MMA GATE KU STADIUM KOMANSO CHONDE APOLISI NDALAMA ZOMWE MUMABA TAKAMWANI MOWA WABWINO KOMA ZOONA WAPOLICE KUMAPEMPHA NKALABONGO KACHASU ZOONA KUKANIKA KUGULA KACHIBUKU KENIKENIKA

Chenjedzo kwa apolice akumusunga munthuyo; Don’t try to do anaything to her, she is my sister and ndinamuudza ndi ine kuti abe chifukwa cha mwano wa a mkwati so minde on you business. Iwenso wa camera ndirinawe.

Komanso system yoponya ndalama pansi muzikwati yithetsedwe.
Komanso system yoponya ndalama pansi muzikwati yithetsedwe.
Sanali kuba koma mwina amafuna kuponda chabe ,paja kuponda ndi kuba zimasiyana
Sanali kuba koma mwina amafuna kuponda chabe ,paja kuponda ndi kuba zimasiyana
Ok
Ok
Hahahahahahahaha awa asowa nkhani tamalembani zama millions osati otolo zogwa muliselo
Hahahahahahahaha awa asowa nkhani tamalembani zama millions osati otolo zogwa muliselo
Police yaku Malawi kuteroko mulibe manyaz kumanga munthu wongoba ka thousand kokha paukwat kusiya kukasaka okuba azazana mma office’mu
anaika chingamu kuphanzi?
Wachita bwino mayiyu akagone ndi njala ndalama akudziwona
mavuto anthu ndi ambili koma kuba si yankho la mavuto koma boma livomereze kuti anthu akuvutika kwambili
eeeeh dollar ya suzya muno muchalo..
Simunazione pa maukwati anu kapena achabale anu,nkana mukumuikila kumbuyo,mayiyu, but its sad and stupid kumaba mmaukwati,zaonjeza pa Malawi pano zimenezi,muzabela lucifer,nde muzaziona,kkkkkkk
Kkkk sanabe amatoleratu ndalamazo
Nanu Malawi24 Mwapysora Myeso,mpaka Pamenepo Osaman’khala Chete Zinazi Bwa? Amabweza Zake Zosupazo
Thus Malawi 24 i kno ..alws busy with foolish thing …
The wedding was on Saturday and this is a second time for this woman to be caught, the first time she was caught at Comesa Hall so its her behaviour
Mukunene zoona inuyo?
Yes cuz I was chief vice protocal for the wedding. It was the wedding of Ken and Thoko Phombeya and I even interviwed the lady. She comes from Chilobwe side and we let her go cuz she had a baby. There were two of them, one escaped before we caught her.
Was it of ken and chisomo phombeya?not thoko
Should be Chisomo not Thoko
Should be Chisomo not Thoko
Imadwa pomwe ayimangilila
It’s not fair,kuba paukwati adaganiza bwanj nayeso
Amai kutakata patown
Shameful woman
tsotsi mukadzi uyu
Eish musamange nditumizire account ndibweze zomwe anatengazo
Wavutika mpatseni ngati inali business!! Vito lanu munamuyika ndinu
Za ulere zimenezo kuba kwa chani mutayeni ameneyo
Ameneyo Amazibela Ndiwo Mumpoto (Shame)
sizikugwilizana nkhani ina reason mukupeleka ina, mmmm bwino2 mungayambe ndale!!
Ok ndamva koma dziwani kuti tonse ndi akuba koma kusagwidwa.
Imeneyo ndi nkhani nanunso?
Anthu akuba ma million mu boma nde tikathyoke khosi ndi oba ka sauzande ka ukwati…..aliyense anabapo apa nde tisamuweruze uyuyu
Kkkkkkkkkkk atayeni amenewo
sanayambe ndi iyeyo evn ma minister amaba plz dont arrest her
Komaso news iyi kusowa zolemba.
That is a sign & symptoms of poverty in our country
it happens
maluzi guys sicholinga
Umphawi palibe angaugonjetse umagonjetsedwa ndi akufa ???
U cant eat without plan just understand her kkkkkkkkkkk
U cant eat without plan just understand her kkkkkkkkkkk
mhu!!!!!
amaiswatu ameneyo
amaiswatu ameneyo
Part of lyf
Part of lyf
Balancing gender, fifty fifty campaign.
Balancing gender, fifty fifty campaign.
ITS PARTY OF LIFE
Wangokhala Wakuba Basi Coz Economic Hardship Does Not Give Us Opportunity Wakuba
Wangokhala Wakuba Basi Coz Economic Hardship Does Not Give Us Opportunity Wakuba
Wakuba ndi wakuba basi , its not because of economic hardship ,
Wakuba ndi wakuba basi , its not because of economic hardship ,
That has nothing to do with economic crisis. Learn to post relavant issues admin
That has nothing to do with economic crisis. Learn to post relavant issues admin
Ha Ha Ha Angomuotcha Bax
Ha Ha Ha Angomuotcha Bax
Eish! Shame.
Eish! Shame.
99
99
heheheheeeeee anaganiza bwa? la fourty tu linakwana apa
Malawi wa lero lol
Nawenso Malawi24 Reporter, why are you hidding this thief who was stealing money at the wedding? You’ve heard for yourself that this is her behavior of stealing money. As you’ve put it that this is her tendancy of stealing ” she has been stealing at a number of weddings in Blantyre in the company of her friends.” Is there any need to hide her name here? Bwinotu mwina umadya nawotu. Stealing is stealing basi NO need to hide her name.
its not hard times but she is a thief
Maluzi.com
Umphawi
Kkkkkkkl
She’s just a thief,it has nothing to do with the economy….
She’s just a thief,it has nothing to do with the economy….
sha,zavutatu pa Malawi,mpakana pamenepa
sha,zavutatu pa Malawi,mpakana pamenepa