A lot has been said about Levels Remix, a song by Malawi’s dancehall kingpin, Malinga Mafia that features Fredokiss, Martse, Malcelba and Episodez.
A number of people on social media have connected the music video to illuminati. The connection follows a scene where the Bible is shown burning.
A quick look by Malawi24 establishes that the burning is just an art through the use of red smoke flares.
However, you are the last judge. Take a look below:
OK ! Wait a minute I got ur ans still loading.
mukadisadisa nde mukazii just remember levels
I feel sorry about my malawi,,, why fond of spreading bullshit stories?? nothing is wrong in that video,,, eeeeee instead of promoting our musicians u busy posting shit,, fuck malawi24
Ukusuwa zolemba et osangokhala bwanj
Amalawi..chirichose illuminat? Xese r signs of unschooled minds…what u shud no z dat music is an ‘Art’..its needs creativity…
kkkkk okonza m tchalitchi cha satanic nanga umphawi umenewu kumakamba za satanic
Sanasowe chonena…mudzazindikira ili mmutu
kkkkkkk wasowa chonena bwanji tizovala tocheaper ngati timene tija koma guys kkkkk kumayenda muzaona zoona
Not every anti- religion act has connections with illuminat. Stop thinking small guys. That talk is cheap
Not every anti- religion act has connections with illuminat. Stop thinking small guys. That talk is cheap
The only person qualified to be called an illuminati in Malawi is bushiri, all y’all go back to basics (Ufiti).Stop Hating good Art
The only person qualified to be called an illuminati in Malawi is bushiri, all y’all go back to basics (Ufiti).Stop Hating good Art
uli ngati sinner sumatha kulapa(malceba) the bible was there just to compliment that part of the song! bad mind bad mind malawians! by the way who sent yu! it is somehow impossible to develop in malawi cos of bad mind pple! remember the scenario of gabadinho pple talked shit abot his JCE results! but today he is swimming in bunches of millions! let he who the cap fits wear! ukaipa dziwa nyimbo! pangani zanu zooneka kugulu! i rest my case!
malaw sidzathek bax maling mudana naye ndpo simunat kusalil amalawi
Anzanu akapanga chinthu chabwino inu mumangofuna kuipisa bax #anyapara_inu levels
Anzanu akapanga chinthu chabwino inu mumangofuna kuipisa bax #anyapara_inu levels
bomboclat malawians full of judgements, I see no bible burning in the levels remix video all I see is comments of badminded Malawians.
udzisankhile wekha yemwe udzamtukira
illuminat samapanga ma artist osa brower komaso ku malawi kuno ili kuti illuminat’yo…amafuna internationally fame artist’s osati ana osasamba aku malawi
Amalawi tili ndi vuto timakonda kupekelana nkhani ndi chifukwa chani?
but act ndi ya satanic ndithu or mukane!!!
ndinataya nthawi yanga kuwelenga zopusazi ok ndingozipepesa ndekha
Ine sididandaula zambiri. Ngakhale mphasa ndikugonera ndi yakutha, koma ndimadziwa, kuti mpweye omwe ndikupupa siwanga. Alipo wina yemwe akupangitsa ine kupumako. Komanso kuti ndidye nsima ya ndiwo chigwada ndimulungu yemweyo wandipatsa nzeruzo. Nde mukamati mulungu kulibe, izo ndikumvera inu. Odi ndidzipite pakaphasa kanga kakuthaka.
vuto lake mumawonerela pa ma screen a old model!!!!!! ife tikuwonera clear pa HD screen, zonama izo.
Kumaganiza b4 kuzipopa kwanuko, ndakwiya nanu ana asatana.
TF??
macelba malinga amva zimenezi?….nde inuyo mungoyamba kuimba tione nao ma kanema anu……LEVEL
they revealed themselves that they under darkness kingdom
We Must 2awake 4m Slping 4ur Salvetion Is Nearer Than Wen We Started Believing (romans 13:11)
aaa inu kulibe illuminati kumalawi zongotera jut awa akumayimika zara ziwiri inensi ndipange ndikhale wa illuminati
aaa inu kulibe illuminati kumalawi zongotera kut awa akumayimika zara ziwiri inenso ndipange ndikhale wa illuminati
Ana anjoka
Kkkk Galu Iwe Ulibe Manyazi Musiye Mwana Zokhawapangazi Wamatchukitsaso Panyopakoso Ndipo
Kambani chonde zinthu zanzelu asati Izi,mmakomo mwa Anthu mwaatchulawo munaonamo?umphawi uli thoo!ndiye muziti Iluminati,Iluminati yake usiku kapena? do you know the meaning of Illuminate or you just talking because is easy to say?nkhani iyi ikufunika loya
Kambani chonde zinthu zanzelu asati Izi,mmakomo mwa Anthu mwaatchulawo munaonamo?umphawi uli thoo!ndiye muziti Iluminati,Iluminati yake usiku kapena?
So what if it was burning?
Inu machende anu…. why hate?…. anzanu apanga sweat kuti apeze ndrama … apanga sacrifice kuti apange music video with an expectation of making more money. …. inu muku dissa… zimakhala zowawa mumangoziwona kuphwka fuck you once again
The song is a hit but the video is a total wack and crap, However I didn’t notice the burning of the bible due to poor video clipping; the video doesn’t have that levels image!!! only one scene! crap!!!

mwatokota ya chinga panonso mwayamba ya malinga.anawa anavaya funani chochita guyz levels to dis thing ndi more.
mwatokota ya chinga panonso mwayamba ya malinga.anawa anavaya funani chochita guyz levels to dis thing ndi more.
hahaha malawi wll never change untill our mind set change.
hahaha malawi wll never change untill our mind set change.
Now ppo google my bio Oyimbo(Macelba) Thats y anaonesa books ija and panalibe bible pamenepaja…. kkkkkkkk Illuminat yake nde yaumphawtu…. and palibe amene angandpose kutchena in that video amene akutsutsa check my profile…

umatchenadi koma vuto umangobweleza zomwezomwezo, sory 4 dat bt u r fyn broo
Ndimayang’ana ndati ndisilire koma aa zovala zomwe mukuzimenya nazo pa mtimazo mbola nsapato ikumapezeka yokutumula zingwe zosiyana mtundu kuti tifunse utha kumatinamiza kuti swag aaa zazii
Ndimayang’ana ndati ndisilire koma aa zovala zomwe mukuzimenya nazo pa mtimazo mbola nsapato ikumapezeka yokutumula zingwe zosiyana mtundu kuti tifunse utha kumatinamiza kuti swag aaa zazii
pa level yanga nd mmene ndlili……
Zaulendo uno! iiiih kaya
pa bible alongosole bobo nyimboyo ndizabaibolo sizikhuzana olo pang’ono ngati akufuna bwanji asango borna ndiauxilu oxe
tiana tasataniki tokhatokha
nde opelekera tea ku satanikiko, nanga amalinga mafia ali ndi kathu?
a Malawi akasowa chochita amapeka nkhani
this is madness cant you guess chifukwa chimene adayikira bible mu video?? any way amene akuyankhula zimenezi ndi mafollower a Mady P
za chamba eti video ya ndani inapyamo bibles in malawi its just a negative attitude towards developed videos ihave watched the whole video closely but the bible wasn’t burning kma ma effects kuti lima wala ngati ndichoncho bwanji silinanyeke,,za chamba zausilu eti levels to dis thing still keeping de fresh men

send me the video bro
send me the video bro
plis can you send me 0621058282
out of credit guys kma mutandipasa ican do so my whatsaap contact:0885283799
Ndedzavutatu dzilizoxe?
Amalawi sadzathekaxo
malawi as acountry tiziti ma videoz mukufuna ndiakale kale omwe aja ziko lina sintha pano kunabwera ma efects za chikalekale mtima osafuna kuyamikirana osafuna kutukuka kuli za makono nowadays anakunamizani ma prophet anu,,,, levels to dis thing

Malawians we have alot of time on our hands
guyz osamanyoza anzanu akakhara pa higher illuminati yachan?
guyz osamanyoza anzanu akakhara pa higher illuminati yachan?
levers woyeee!!!
levers woyeee!!!
l dont see dat in da video. you write something worthy to our desire of reading not that nosense.
l dont see dat in da video. you write something worthy to our desire of reading not that nosense.
Wow!
Wow!
Shame on you who says God doesn’t exist,
Shame on you who says God doesn’t exist,
sindili mbali yadzikoli ine Yehova ndie m busa wanga ndipo sindidzasowa in Jesus name amen
sindili mbali yadzikoli ine Yehova ndie m busa wanga ndipo sindidzasowa in Jesus name amen
kkkkkkkkkkkkk kkkkkkk
ine ndilibe polobulemu ozikamba azikamba… level to this thing
ine ndilibe polobulemu ozikamba azikamba… level to this thing
which video is that?…the Bible wasnt being burned look closely…take a deep analysis before you publish your stories otherwise you might just be sued on silly issues
which video is that?…the Bible wasnt being burned look closely…take a deep analysis before you publish your stories otherwise you might just be sued on silly issues
watched the video i cant even for over 6 times ……they never burnt any bible
watched the video i cant even for over 6 times ……they never burnt any bible
Aaaa wen u will start appreciating art you will never question things in videos. It’s called being creative mwazolowera ma video ngat a Billy kaunda or luciua Banda. The thing is malceba says uli ngat sinner sutha kulapa. The bible is shown as that bar drops in reddish/pink smoke. That’s how creative the director was connectin that bible to the bar that was dropped instead of showin someone in a church or wateva u can think of as the best alternative. Another thing bible silinapse mene muja muonesese and that’s not fire. They are just smoke flares as those used by people who wants to be rescued I think u have watched those in movies

Zitsilu za anthu izi zoonadi zoti nsanje pa malawi pano ndipachimake koma aziwe zokuti munthu alibe mulandu ndi amene amadya zako,, Basi busy kumangoweruza anthu abho bho apange zawo kuti ziwathandize omasangoweruza anthu oti Illuminant samaiganiza iyi

dude stop being an ass hole. you piece of shit.
Man ndigaileni video yake pa whatsapp pliz pliz 0881397445
God/Allah or Satan do not exist. These things were inverted by rapists, killers, drunkards etc , just to get what they wanted. The earth is our home and this life we are living in not in anyway a rehearsal of a future life. We shld concentrate on making our earth a better place to live.
Shame on u
u dont have time to live on earth hell is calling u
if God does not exist then why are u saying of Him…can you talk of something which does not exist….
the fool says in his heart there z no God…watch ur mouth brah He can shut it forever
Fire !!!you are son of satan may almighty lord forgive you..you are devil himself
Dan Bon Liyaya simunayimbeko nthano? zimene zija nzabodza koma mesa timakamba.
OMG! M sorry for young man,u are really lost and may God help you,there were people who were thinking like you,but they regret it,so as of just sit down and spend 5 minutes stay silent God is going to talk to you,dont be lyk an idiots coz d bible say if u say dat there is no God then u r an idiot
God/Allah or Satan do not exist. These things were inverted by rapists, killers, drunkards etc , just to get what they wanted. The earth is our home and this life we are living in not in anyway a rehearsal of a future life. We shld concentrate on making our earth a better place to live.
Shame on u
u dont have time to live on earth hell is calling u
if God does not exist then why are u saying of Him…can you talk of something which does not exist….
the fool says in his heart there z no God…watch ur mouth brah He can shut it forever
Fire !!!you are son of satan may almighty lord forgive you..you are devil himself
Dan Bon Liyaya simunayimbeko nthano? zimene zija nzabodza koma mesa timakamba.
Prove to me that there is god or allah.
Humans are resistant to change
Imeneyi Ndinkhumba Ndithu, Simunthunso Ukanakhala Mugulu La Tidoyo Akanakhala Inda
Pano enanu you do not even know that Gehenna which is Hell is just a place just outside Jerusalem and you can google it to confirm koma mmati oipa apita kujaherna kumoto aaah abale ku jahena kulibe moto and kumakhala anthu. Just google Gehenna and see the map.
Uyu Akunena Kuti Cauta Kulibe
So that means you don’t believe in Bible neh? ?
hmmm…. Mulungu akukhululukireni achimwene
Iiiiiiiii ndili ndi mantha chifukwa sindimadziwa kuti ku Malawinso kuli anthu omwe amati kulibe Mulungu. M’bale ingokhulupirira kuti Mulungu aliko ndipo Dzina lake ndi Yehova “Masalimo 83:18. Aliyense ali ndi kosamila, iwe mulungu wako ndi uti? Ndipo chimakulimbitsa mtima kuti kulibe Yehova ndi chani? ngati ndi choncho ndiye kuti palibe chimakuletsa kuchita choyipa sichoncho? Ukuchedwa mzanga
God exists
God exists
Illuminati yake nde yaumphawimphawi eee….coz olo timphasha anavalato mtima fong Kong…Ma R20 pa medical mu Jozi mu. Mukapsa za ziii. Umphawi sizinthu guys
Illuminati yake nde yaumphawimphawi eee….coz olo timphasha anavalato mtima fong Kong…Ma R20 pa medical mu Jozi mu. Mukapsa za ziii. Umphawi sizinthu guys
Ndipo akamati oimba ena aku Mpanje ndi a illuminati ndimadabwa nazo kuti kapena iliponso ina ya amphawi. ..coz anthu amangotchuka kuti ndi a illuminati koma alibe kalikonse. ..awa nde akapseradi za zii!!! mxxm
kikkkkkkkKkkk R20?
Eya Che Madengu….kkkk…akuti a Illuminati koma akufukula wapansi olo ya kapaza alibe
Eya Che Madengu….kkkk…akuti a Illuminati koma akufukula wapansi olo ya kapaza alibe
Ndaonera awawa kuti ya Amphawi iliponso
Ndaonera awawa kuti ya Amphawi iliponso
Eee ndakuthadi kuona choncho. ….kkkkk aaa
Eee ndakuthadi kuona choncho. ….kkkkk aaa
Swag ya ku Malawi adha kkkkkk
Swag ya ku Malawi adha kkkkkk
That’s satans trick most people are helping satan to promote wickedness without pay. They say they are urban artists. Unknowingly proclaiming evil without gain
That’s satans trick most people are helping satan to promote wickedness without pay. They say they are urban artists. Unknowingly proclaiming evil without gain
Ur 2r bro angopelekeza amzao kulezera bas
Ur 2r bro angopelekeza amzao kulezera bas
Tigailen nafeso tizionere tokha #0884939655
Ok boss
tigaireniko tionere plis 0621058282
tiponyeleni man +27630885039
Kkkkkkk +27832428560
0888752993….? tigaileni.. mwina tingakomente zanzeru pa nkhanii!!
Lord 4give me my awkwardness
Lord 4give me my awkwardness
aaaaa ife nde sitionera oimba achisawawa amenewa,Lucius Banda amatikwanira kuvera tsiku lonse
aaaaa ife nde sitionera oimba achisawawa amenewa,Lucius Banda amatikwanira kuvera tsiku lonse
have mercy jesus
have mercy jesus
Ok
Ok
koma bible limatanimo mu nyimboy zmagwirizana bwanj nyimbo nd bible?
koma bible limatanimo mu nyimboy zmagwirizana bwanj nyimbo nd bible?
Ndikhale mbuli pankhaniyi
Ndikhale mbuli pankhaniyi
forgive them Jehovah GOD Because they don’t know what they are doing.
forgive them Jehovah GOD Because they don’t know what they are doing.
illuminat@its best in the last day little wonder ..
illuminat@its best in the last day little wonder ..
God giv me a sign
God giv me a sign
ahahaha
hmmmm nanu kungofuna kuipisa mbili za anzanu bas.
hmmmm nanu kungofuna kuipisa mbili za anzanu bas.
bible silinaotchedwe man muzionesesa usi ndiomwe umapita komwe kunali bibleko os@ moto
bible silinaotchedwe man muzionesesa usi ndiomwe umapita komwe kunali bibleko os@ moto
dont judge for you be judged… akudziwa okha zomwe akupanga
Why use the bible in such circumstances in the first place.
Muzionesesa bhobho palibe chimaotchedwa kungot mahaterz ndamene akumatero
Inu wina andithandize mumatani kuti mukachita comment pazioeka nkhope yanu ?