The MK1.7 Billion corruption case involving ex Malawi President Bakili MuluzI and his ex assistant Lyness Whiskey still has its progress unknown as on a day Justice Mclean Kamwambe was supposed to make a verdict on its progress, it was revealed he was busy with other engagements in Lilongwe.
Kamwambe yesterday was supposed to give a verdict whether to discontinue the case or not after the Anti-Corruption Bureau (ACB) deputy Reyneck Matemba who was lead state prosecutor and another prosecutor Chrispin Khunga asked Kamwambe to stand aside from the case.
Kamwambe granted the two the application, a move which prompted the defence team to ask the same court to discharge the case.
Court is to announce of the day the verdict will be made.
For over six years, Muluzi has been answering charges of corruption in which he is accused of squandering public funds amounting to 1.7 billion Kwacha.
Pliz leave Muluzi alone.This case lacks incriminating evidence.Tifunseni ife tikuuzeni za milandu.
So many cases for late Bingu was mutharica who judging him?
Acheya omwewo kumachenjera patawun
Aliyense amene wapedzeka kuti wasokonedza ndalama za fuko la malawi, wapha tsogolo la Malawi……chifukwa chiyani, kuba chithandidzo cha miyoyo yopitilira 15,000000 ndikupha. Ndichifukwa dziko lathu la Malawi aliyense amene akhale mtsogoleri wa dziko choyambilira kuganiza, amaganidza zoba ndalama za miyoyo ya anthu ochuluka, komanso ndalamadzo kukhala zobwereka kudziko lina kuti dzithandize wanthu kumaproject osiyana- osiyana. Kukabwereka ndalama ndziko lina zikusonyedza kuti…….inu mukukabwerekanu mulibe ndalama zopangira budget yokwanira zothandidzira anthu chaka chonse. Tsono ndalama zobwereka kuti muthandidzire anthu ena akudya ndalamadzo ngati mwana wosadziwa kubvuta kwa ndalama, tsono zimenezi achite atsogoleri atatu dziko litukuka?????? Wake up Malawi mukabisa chilungamo mukupha ufulu wa ana amulungu, ndipo yense amene waba ndalama zaboma abvomeredze kuti wabadi. Ndipo panopa zikuwoneka ngati zochedza koma pa judgment day kulibe corruption koma kuli justice.
Nkulu ameneyu talent yake ndi commedy sizingatheke kumangidwa..kuchipatala anavayako ..ma vistor ake anali mr bones..mr ibu ndi ukwa jst wait …munva zomwe angapeke..loi ..achakulugwa awa kuchitekekete.
Leave my mudala alone. U r westing ur time with Dr mluzi. Atafuna atha kukupatsani pompano cash cash
Corruption will never ever end in our dziko no mata w@…….. it was there, is there & it wanna b there!!! Cashgate.com
amangidwe uyu bastard thief!
the government is blaffing coz they have his baby in their cabinet xo how can they pin his dad at the sametime? Raw deal!
Awaist of taxi payers money to pursue acase which we believe can’t change current economic woes,work on how to sustain amalawi which needs Gods interventions as quoted by Goodal Gondwe,than to play hatred politics,old function baba
Malamulo oyendetsera dziko la2 asinthe bac. Kodi mungamangomuyang’ana munthu kulowa mnyumba mwanu kukuberani mpaka kupita kwao kenako inu nkumutsatira kuti wandibera mnyumba mwanga? President adziyimbidwa mlandu ali pa mpando komanso adzidulidwa msonkho bac tonse tigonjere malamulo a dziko lathu posatengera kuti uyu ndi mbuzi ya president.
Ada mwenendiukhungu wauzeleza kukusaniyape tiotchengi iwi
eey you guyz leave Mr Muluzi alone..try 2 find other thingz that can help our country n development..”leave Him alone
This madala is a good man
Zoonadi bro
Olakwila malamulo alimbana ndi malamulo. Olo atamutaya olo atamumanga palibe ndingaluzepo ine, ngati anaba wakuba amamangidwa, ndipo kukhuruluka kulipo komanso samakakamiza kuti khululuka
the muluzi family and the mutharikaz are friends and pipo shud now kno dat this case will end in vain…. and kupanda kut anasemphana maganizo the late and muluzi bliv um sizkanafikaso apa and 4u tobeliev this see how today muluz and mutharika r playing their game
Akuba onse ankasangalalatu nthawi imeneija ndikukumbukila nthawi imeneija ndinkagulitsa zikwanje munsikawina masapota a UDF anangobwela kunditengela zikwanje zonse ulendo wokamenya mfumuinayake,geni yanga inathela pomwepo kwamene simunakumanenazo mutha kumangoyankhulapo basi,afunseni anthu bwinobwino akuuzani osangoti poti munadyanawo tindalama tafegi tija.
Awuzeni ngamo madala. Anthuwa ndi ana kwambiri akungoyankhulira kusadziwa. A buzinez amathawa katundu ali wao pa Wayenera. Akuba amagwira ganyu yosapangana ndi mwini wake.kusitsa katundu mu train kapena pamwamba pa bus akatero amalamula ndalama yochuluka pamene mwini wake sanawauze. Wina ndinauwopsedza kuti ndikulodzatu ine, wapepesa nkusitsa katundu wanga ulele
nkhani iyi sili bwino
first Mulandu 10yrs munthu akuyenderA
ku khoti? Chilungamo palibe ..
And the more it. z being delayed its the
more Muluzi zinkupangitsa kukhala ngati osalakwa.
10yrs? no judgement. no justice. nanga atawina?
Munthu azalikokola boma ndalama uyu.
Ali bho Muluzi kutsogolo ku Mulandu uzamukomera.
Alibe Mulandu. anakakhala ali ndi mulandu kalekale ata server ndikumalizanso.
Ndikumulimbitsa Muluzi asadande alemeranso ka chikena whether anaba/sanabe
Pali nkhani zina zimene zimapangitsa kuti newspaper ziziyenda malonda .kwaine munthu ngati waba osagwidwa siwakuba pajaso atcheyawo ankanenachoncho ,koma vuto mulandu suwola,lamulo liposa mphanvu atcheya timawakonda ngakhale panopo koma ngati anasolola penapake ngakhale patatha zaka20 mlandu udzatuluka osati chifukwa chamunthu koma lamulo .
Conclude the case or Legalise corruption
Why u work hard on the healed wound rather than treating the fresh one?
Atcheya ndikumtunda, kumtunda kwache kwa mbwiyanu?Mukungoyankhulapo za zii apa, nzanuyotu ali ndi ndindalama; anamanganso chi Atupere properties. Ndiye mupite kwao ku Ntaja mukaone mmene anamangira.Ali ndindalama zambiri mma bank osiyanasiyana,ngakhale ana aku zibwenzi sazavutika mpaka kalekale, bomanso limamulipira ndalama ngati president opuma. Inu muli ndi chani apa kuti muzibwebweta, kumtunda kumtunda!! Iye akuziwa kuti mukumuchemerera?Kupusa, mix mukungogonanso pa mphasa apa makape.Mpakana maso pamtunda zomwezi? Ndi a mbwiyako chani?
Kodi Killa mwalembachi ndi chi pwitikizi eti?
Nosense
Message from Pastor Zoe ” The word of God must be more real to you than the person next to you in order for you to activate your miracle process . What you see in The Word is what you experience in the world”. like our page
https://mobile.facebook.com/ChurchAlive-Ministries-1161841847171147/
insights/?section=likecount
Let set example to lock up this Big Thief at Maula prison so that other Thieves in Dpp learn a lesson.
Sizigwiridzana ndi APM idzi,kodi khani ndiya liti, mayi Joice sanaipedze ndikuisuya,bwanji sananene kuti khaniyi ingotha? Khani ikambidwe ndipo idziwike mutu wake. Tchimo ndi tchimo olo mutalivalika jekete ndi tchimo basi. Is what Lucky Dube said b4, he’ll be happy if he’ll see all the people are equal in the eyes of ze law. No matter kuti anali president, lamulo ligwire tchito basi. Mkasa anati lamuro lopotsa phavu,liri ndi mano achitsuro,yemwe ali pute lithana nae motsayang’ana khope kuti ndi ndani?anali ndani? amapanga chani?ndi wafuko lanji?kaya ndi m’bale wake wa ndani? Ilo liribe nazo tchito. Musie ma judge aweluze kenako ngati angadzafune kukhulukila iyo idzakhala khani ina. Naeso APM akadzaba kaya akuba,akadzangogwida naetso lamuro lidzagwira tchito basi.
So is that Bakili Muluzi mxieew
Mungotaya nthawi yanu pachabe kapoloma boys imeneyo mukuchepa mukabadwe kasanu yawuzilu leave muluzi alone Geez
Kodi inu aboma mwatsowa chochta tsiyeni muthu wakulu aphume mwaiwala kuti kunali misongo kale ndani kodi amene anachotsa ngat mulibe ndalama musalimbane ndimuthu wakuluyo
#Jelson its all about time… U tnk till today azionekabe like he is 30? Give urself 30 yrs from today ngati muzakhale the same.. Somethings even money CNT buy,, getting old is one of the tngs
bwana mupambana osadanda
Feel like crying for him… Leave Muluzi plzzzzz… Palibe yemwe sanabebo m’bomaa ..
Kkkkk kwalira kumtunda kkkk, kodi ameneyi ndi Bakili Muluzidi? Ngati yankho lake ndi EEEE , ndiye eee dziko ndilodzunguliradi eee… Nkhope ya kuntunda mpanakuoneka chonchi?? Ine sindikukhulupilira ndipo sindikumvensetsa.
akuluwa kukalambatu uku
Peter mutalika mutumwake siziyenda akuwonangati bakili mulusi angafanane ndikutunda liphupa shitekete abaki woye boma la dpp mukamalimbana ndi nsheya muzingofutika
Achalume kuchiteketa uku!!!! Munthu uyu aaaaaaaaaaaaaa ndikakumbukila mmene anali pa udindo wake aaaaaaa ndikulemphera kuyakhula,ulemuwani munthu wankulu. ndamphunzila prayimary yaulere ndi zina zotero kamba kameneyu.wina aliyense amalakwa oro iwenso perter ungandiuze zoti [email protected] zopunsa ngati brather wako unja .brather wako anamumangatu mwana waketu usaiwale zimandimphwetekatu ndikakumbukila B Careffffffffffffff
If i hv chance to dictate i will say bakili is best president in malawi ever ever hv,john mtembo is best opposition reader malawi will ever ever hv.
Avaye bas chamaboza chimenech kwabas
I thanx many who have liked my comments I humbly thank you guys once again my idea was Malawi as a country we have failed hence our sickness exposed in the massive failure of many valuable sectors of our government systemes like agriculture and education just to mention a few
Osangowasiya bwanji munthu wakula uyu.
Zaziiiiiiiiiiiiiii!!!!!!!!!;;;;
Thank you to contact with the French lady who made me happy this month Ms. jacqueline guichard. I received a loan of €
45,000.00 and several friends have also received loans to its level at no cost in advance. I publish this post because currently there
are only criminal on the net which only hurt the people it I’m good with that loan. Today I have solved my problem. I thank the
honest and generous lady.Take contact, she is honest and sincere in addition, the loan offer is free.
Here is his email: [email protected]
thanks for understanding.
Please share: the message to help those in need
Mutayeni man.ife timasangalala kale chifukwa cha iye
apikane nkhani syakuwalanga idilisa kalisinje kuwecheta ngani syamdalaea kwasa ndawi ligongo wakulungwawa kumatumbi kumachenje kumbugu kwesokoche nagakwikuta nigona ngamtanda jwine tuchiwenesyana moto gamasanje wa dpp wosope mmatongo mwenumo
munthu musiyeni wakula osamusiya azisangalala bwanji uchitsiru eti
munthu wakulu kwambiri
We are tired of this story from when up to date. God knows
Justice cannot take place while da pple whom u call judges r corruptible
Umadya bwino kamba ka UDF wayiwala kuti nkulu wako anasiya chipani kuyambisa DPP musiyeni muluzi
Peter ndiwe mbuzi basi
Final ija ili lero. Liverpool vs Sevilla @21:00 shap
munthu ndiokalamba uyu uzipitanaye kuti iiiiiii usiyeni mzanu apumule mulandu wakalekale mukanaukumbabe eeeeeee eshi mukusowa zochitakapena mwina mmmmmmm ayi sibwinokoma
Mr president mupezanazo minyamatu zimenezo, osangomutaya bwanj?? Nkhalamba ngati imeneyo muzikhalanayo jijili jijili
arrest him…………..
tamutayeni m’dala wakula uyu.
We will never have a good leader in land;)
Let him go!!!!!!!!
ndichikhala ine piter muluzi ndikanamutaya adzipuma munthuyu komaso amweyi ndiamene anawatora iowa lero lino ndi ndichochezera chao munthu ndi bambo wao or kuti mayi amene wa achina muthalikawa chifukwa anawakonda mu UDF nthawi ija munali mitu ya bho ya anthu azeluso koma ndiko nanga awa achina JB bwanji simukuwagwedeza
Uku ndikundunda kwa zithunda zonse ana apatawoni, amatetule ,mfumu,munthu wamkulu kuyambira chitipa mpaka nsanje.palibe a ngamututumunse ANALIPO akuti amututumuse KOMA analemphera, timakhala pa mbuyo mpake ndipo tizakhalabe pa mbuyo mpaka mitsitsi ikazaola ifenso mansamba tizayoyoka ANA ACHEPA.Mukunama mbamva inu mbudzi imadya aimagilila,ADYA ANGA@ndipo papita anthu angati chipumileni munthuyi???mukakhuta chimanga chokadzinga muzamakambe zamunthuyii mwamva???? Musiyeni.mkamwa mwanu mumayambwa mukapanda kuyakhula zinthu zopunsa et.
Ana okuba pa town
this issue is becoming very boring no matter what mr bakili muluzi wil never get arrested coz he speaks thru money
Thanx wackera and adujai for likn my comment
Akuluwa aziona zomwe amkamuchita kamuzu zija abweze ndalamazo
African leaders have one problem that is wealthy competetion.Any president want to be the richiest person in the land by the end of his/her term.You will find villains praising these presidents wealthy without telling us where they got the money.I remember that theres was time when people were fighting just because of Muluzi and Kamuzu wealthy,When Bingu came back from exile where he was fired from PTA in Lusaka, he formed United Party and lost in general elections of 1994, he came sixth. He lived in Area 47 in a three bedroomed house and had one small hiace mini bus written Bineth which he was running. Muluzi later picked him and appointed deputy reserve bank governor and the rest is history. By 2008, he was a multi billionaire, a thing that can only happen under the nose of docile people.The same thing happened in 2013 people comparing Joyce Banda and young Muthalika’s wealthy.We are in deep hypnosis..Better we be recolonised again we have fail to govern ourselves…..2019 the forbes will tell us That Peter Muthalika is the richest In the Land .mark my words
problem is we born to vote these others the born to be voted but I wish malawian the should realize one day dont go to vote these fools and mind our busines because is same u do u dnt d
i am Dpp die mhard but sometimes i like exposing the evils these leaders
mwalemba mwazeru,koma chipanicho ndiye mavuto.
kkkkkkkk Thabks Henry there will always be a change in life Brother
Thank you to contact with the French lady who made me happy this month Ms. jacqueline guichard. I received a loan of €
45,000.00 and several friends have also received loans to its level at no cost in advance. I publish this post because currently there
are only criminal on the net which only hurt the people it I’m good with that loan. Today I have solved my problem. I thank the
honest and generous lady.Take contact, she is honest and sincere in addition, the loan offer is free.
Here is his email: [email protected]
thanks for understanding.
Please share: the message to help those in need
kulimbana ndi tcheya mapeto ake ndizija kumangofa osadwala mukulimbana ndimilandu yoti mboni zina zili kulichete Fupatu lokakamidza silichedwa kuswa mphika nkhani imeneyi ena alandilanayo Red card
A Malawi timayiwala nsanga Bakili ankanena nthawi zambiri kuri CHANGU pa MALO lero mukafunse kuti anaba kapena ayi.Komanso anakweza ma judge angati?nanga kuti achina Mutharika apezeke pomwe alipopo engineer ndi ndani? Ango mutaya zadutsapo izo
we will never hav smile president lyk him in malawi, basi becz we had deases in our mind, we think of today nt tommrw, wobwe akumuimba mulanduyo anapanga chani malawi muno kopotsela kutseka ma school, ndikwapatsa anthu ma T shrt wojambula chimanga basi, siyeni munthu wakulu apume sikuti mukamanga ndiye tisakufotelani ayi mulibe ulemu anthu wosanga mitundu inu
Atcheya ndi chair basi muti mungotaya nthawi basi.
Chitukuko chikukukanikani mmalo mwake mukulimbana ndi munthu osalakwa…..kodi ndalama zimene zinapezeka kunyumba kwa mbuzi in a inamwalira ija inapita kuti? Musiyeni munthu akhale ndi ulemu wake ife umphawi tauziwa mu ulamuliro wa galu uja mumamutcha bingu uja. …..agalu inu
Iyeyo ndi iweyo mwina nkuthekanso kuti iweyo ndi amene uli mbuzi kwambiri. Kumachepetsa kulalata nthawi zina ndibwino.Mavuto a za ndale ali paliponse pa dziko lapansi.Tikamadalira kuti uyu atithandiza mapeto ake umphawi sungathe
So the prisons are for a poor man like me…what a shame
mwana kubadwa m banja mpaka kukula tikumva mulandu umodzi wa a chair nanga atsogoleri enawa milandu yawo adzayankha ife titamwalira,koma malawi walero ndiwotani,achair don’t regrate mmenemu ndimmene adamulengera munthu
Usova ndi tcheya wakoyo Bingu yemweyo kuti wawawa
Izi zikuchitika chifukwa kwanthu kuno ndi kosauka basi maiko ena azanthu izi kulibe!
Ife zopoilazo ayi , nthawi ya muluzi tikava kukoma
There’s no party that can save our nation they are all the same
Itheletu Nkhani Imeneyo Osamanga Abwampin Anaba Ndalama Zambiriwa Bwanji?
Leroooo aaaaa zachikaleeee. This is the big man remaining among the living malawian presidents please leave this man for God’s sake. Apume mu ntendere wake.
Our concern shouldn’t be on a chair case only our entire political system is sick of corruption no wonder hunger is our friend more are to die
l feel ashamed of these corrupt cases against our leaders.What image are they portraing to the world.They do forget that we leave on fundraised finances that our beloved brothers and sisters out there are campaigning for.Even now look how they are giving Government Tenders,is as if they are receiving deceased benefits.What a shame!!!!
Noah politicians are sick people they are like a virus to our country traitors our country has lost a lot now we don’t have food yet we are busy clapping hands for thieves we are sick. All parties needs mental reformation
mukamutha chair mundifuse! kulimbana nd chair nd chimidzi!!!!!! kkk
Thanks v NGO for likn my comment thanx
Adali a Chairman nthawi..! adawafunsa anthu kumsonkham wina motero..! Ndamva anthu dzana ndidakutukani {anthu onse:AYI..!} Ena akut dzulo ndidakutukanan..?{anthu onse: AYI..!} Tsopano leo ndkut panya panu..!! {anthu onse..! Lyolyolyolyolyo,uku,akuimbira mmanja ndikunena. Acheya Acheya Acheya……..!! Acheya oyeeeeee…!!!!
Waikwanitsa
Zopanda Pake Basi.Mmene Mudayambira Muja Bwanji Osangouthetsa Mulanduwu.Kodi Kuchoka Nthawi Imene Ija Mwaononga Ndalama Zingati.Zaziiiii,,,,,,,,,,,,ambiri Ndiokuba Koma Kusagwidwa.
fighting a never ending battle..its high time the offhandedly ones unite to fight the conniving ones osati kumangotokota apa
Awa kumbali yaine ndimawaika mgulu lamugabe ndie iwe ukulimbikira mulandu wadhawa ungotaya nthawi yako yocheza ndimkazi wako
The fact that no one is behind bars despite the many billions Malawi has lost for the past 25 years it shows how sick our leaderships are I can’t trust any party
imagine man ati case inayamba kukambidwa 9 Years ago no judgement
Angofuna kusokonezaanthu muluzi sangamangidwe
Mpaka mawa ata uja ndi mtunda wina
Kodi tcheya mukutola eti anyapapiwa ndiye samaba? Asa musiyeni munthuyo! Mwadya zake mochuluka asa pulezident wokwanila Atcheya
kambani zina,ngati mwasowa zochita mukakolope mu nyanja,achair omweo kuti wawawawa,mutangosova
hahahahahhahhahaha nde ineyo yaya
Thanx Symon for likyn ma comment its our country we must love it die for it build it protect it let’s change our thinking status
Then after Muluzi’s case then we should also hear that Bingu Mutharika’s corruption case is in the court and JB’s
Akamati a chair ndi kuntunda mumayesa masewera eti??? Ingovomerani kuti mwaalephera basi osamangochulutsa ma excuse..yambani cashgate basi tinve zina
I wish I was a president
Corruption is a dangerous animal that is so deadly than war it makes countries fall the laws are weak the judicially system become ruthless and vulnerable to evil works devolopements are fake doctors are heartless. People die
How much dat Bingu Wamuthalika corapt?if u cannot answer me dat meanz lets to leave it coz ndinthawi yomanga umozi ino to build 1 nation as malawian,In Lesotho we have politics kumapezeka kuti anthu aba ndalama zochuluka koma angoti musiyeni avutika yekha pamene if buzy mangisana solution ndikumangisa.
If I steal a chicken you will barbarically burn me with fire b4 police come to the scene yet here you keep writing nosence
Ndisanzamve kuti patiente anyoza Odwala pano..! Tikumvana kodi…???
Kubisa 577 Bilion Tiziva Izizi Pliz Tamakozan Miseu
That’s why Africa is poor dyers the prisons are built for the poor to lot the reach are untouchable …what a shame!!! Our countries lose a lot of money tracking down cases that just disappears… Currently hunger is hitting hard when billions are with minorities…traitors…country. Sellers…
mukungodzivuta coz sangabweze ndalama or kumangidwa
#Feesmustfall
mwawononga ndalama zingati zoyendetsera mulandu umeneu, uyu patavuta bwanji sangapite kundende awa ndi achalume, lipupa asyene njuwa…
Leave him alone
cashgate mwayiwala et
anthu owononga ziko awa ngati sikwawo
Amangwetu
mulandu uwu mpaka yesu azawupeza ulipobe
Akuti.. Aaah akulimbana ndi zakale kale .. osawamanga awa aba cashgate panowa bwanj kkkkk koma tcheya kuche njera pakamwa eeeh!
bakili simwana ayi mwava kodi!
Anthu ompenga mwapanga bwanj?
amene akulimbana nayeyo haaa,achedwa
Let him be,,,,,,mwapenga kod et
peopie with money
peopie with money
just leave him alone
Mukapanga chibwana ohoo!
da da da da tha da da da
Pa malawi pano chilungamo palibe, zowona mukufuna kubisa chilungamo koma anthu atadziwa ndithu kuti Bakili adatenga ndalama. Mesa ndi Dpp yomweyi idayambitsa nkhani imeneyi ndipo umboni udalipo kuti adatenga ndalamazi. Mulungu zonsezi akuwona akukanthani sure. Wina ku khoti konko mudamugamula 4years koma adangoba K 4 800 ndiye awa basi apitirize kukadya ndalamazo sichoncho?