Bakili Muluzi’s corruption case continues to stall

Advertisement
Albinos Malawi

The MK1.7 Billion corruption case involving ex Malawi President Bakili MuluzI and his ex assistant Lyness Whiskey still has its progress unknown as on a day Justice Mclean Kamwambe was supposed to make a verdict on its progress, it was revealed he was busy with other engagements in Lilongwe.

Bakili Muluzi
Bakili Muluzi : His case still stalls in court.

Kamwambe yesterday was supposed to give a verdict whether to discontinue the case or not after the Anti-Corruption Bureau (ACB) deputy Reyneck Matemba who was lead state prosecutor and another prosecutor Chrispin Khunga asked Kamwambe to stand aside from the case.

Kamwambe granted the two the application, a move which prompted the defence team to ask the same court to discharge the case.

Court is to announce of the day the verdict will be made.

For over six years, Muluzi has been answering charges of corruption in which he is accused of squandering public funds amounting to 1.7 billion Kwacha.

Advertisement

132 Comments

 1. Aliyense amene wapedzeka kuti wasokonedza ndalama za fuko la malawi, wapha tsogolo la Malawi……chifukwa chiyani, kuba chithandidzo cha miyoyo yopitilira 15,000000 ndikupha. Ndichifukwa dziko lathu la Malawi aliyense amene akhale mtsogoleri wa dziko choyambilira kuganiza, amaganidza zoba ndalama za miyoyo ya anthu ochuluka, komanso ndalamadzo kukhala zobwereka kudziko lina kuti dzithandize wanthu kumaproject osiyana- osiyana. Kukabwereka ndalama ndziko lina zikusonyedza kuti…….inu mukukabwerekanu mulibe ndalama zopangira budget yokwanira zothandidzira anthu chaka chonse. Tsono ndalama zobwereka kuti muthandidzire anthu ena akudya ndalamadzo ngati mwana wosadziwa kubvuta kwa ndalama, tsono zimenezi achite atsogoleri atatu dziko litukuka?????? Wake up Malawi mukabisa chilungamo mukupha ufulu wa ana amulungu, ndipo yense amene waba ndalama zaboma abvomeredze kuti wabadi. Ndipo panopa zikuwoneka ngati zochedza koma pa judgment day kulibe corruption koma kuli justice.

 2. Nkulu ameneyu talent yake ndi commedy sizingatheke kumangidwa..kuchipatala anavayako ..ma vistor ake anali mr bones..mr ibu ndi ukwa jst wait …munva zomwe angapeke..loi ..achakulugwa awa kuchitekekete.

 3. amangidwe uyu bastard thief!
  the government is blaffing coz they have his baby in their cabinet xo how can they pin his dad at the sametime? Raw deal!

 4. Awaist of taxi payers money to pursue acase which we believe can’t change current economic woes,work on how to sustain amalawi which needs Gods interventions as quoted by Goodal Gondwe,than to play hatred politics,old function baba

 5. Malamulo oyendetsera dziko la2 asinthe bac. Kodi mungamangomuyang’ana munthu kulowa mnyumba mwanu kukuberani mpaka kupita kwao kenako inu nkumutsatira kuti wandibera mnyumba mwanga? President adziyimbidwa mlandu ali pa mpando komanso adzidulidwa msonkho bac tonse tigonjere malamulo a dziko lathu posatengera kuti uyu ndi mbuzi ya president.

 6. Olakwila malamulo alimbana ndi malamulo. Olo atamutaya olo atamumanga palibe ndingaluzepo ine, ngati anaba wakuba amamangidwa, ndipo kukhuruluka kulipo komanso samakakamiza kuti khululuka

 7. the muluzi family and the mutharikaz are friends and pipo shud now kno dat this case will end in vain…. and kupanda kut anasemphana maganizo the late and muluzi bliv um sizkanafikaso apa and 4u tobeliev this see how today muluz and mutharika r playing their game

 8. Akuba onse ankasangalalatu nthawi imeneija ndikukumbukila nthawi imeneija ndinkagulitsa zikwanje munsikawina masapota a UDF anangobwela kunditengela zikwanje zonse ulendo wokamenya mfumuinayake,geni yanga inathela pomwepo kwamene simunakumanenazo mutha kumangoyankhulapo basi,afunseni anthu bwinobwino akuuzani osangoti poti munadyanawo tindalama tafegi tija.

  1. Awuzeni ngamo madala. Anthuwa ndi ana kwambiri akungoyankhulira kusadziwa. A buzinez amathawa katundu ali wao pa Wayenera. Akuba amagwira ganyu yosapangana ndi mwini wake.kusitsa katundu mu train kapena pamwamba pa bus akatero amalamula ndalama yochuluka pamene mwini wake sanawauze. Wina ndinauwopsedza kuti ndikulodzatu ine, wapepesa nkusitsa katundu wanga ulele

 9. nkhani iyi sili bwino
  first Mulandu 10yrs munthu akuyenderA
  ku khoti? Chilungamo palibe ..
  And the more it. z being delayed its the
  more Muluzi zinkupangitsa kukhala ngati osalakwa.
  10yrs? no judgement. no justice. nanga atawina?
  Munthu azalikokola boma ndalama uyu.
  Ali bho Muluzi kutsogolo ku Mulandu uzamukomera.
  Alibe Mulandu. anakakhala ali ndi mulandu kalekale ata server ndikumalizanso.
  Ndikumulimbitsa Muluzi asadande alemeranso ka chikena whether anaba/sanabe

 10. Pali nkhani zina zimene zimapangitsa kuti newspaper ziziyenda malonda .kwaine munthu ngati waba osagwidwa siwakuba pajaso atcheyawo ankanenachoncho ,koma vuto mulandu suwola,lamulo liposa mphanvu atcheya timawakonda ngakhale panopo koma ngati anasolola penapake ngakhale patatha zaka20 mlandu udzatuluka osati chifukwa chamunthu koma lamulo .

 11. Atcheya ndikumtunda, kumtunda kwache kwa mbwiyanu?Mukungoyankhulapo za zii apa, nzanuyotu ali ndi ndindalama; anamanganso chi Atupere properties. Ndiye mupite kwao ku Ntaja mukaone mmene anamangira.Ali ndindalama zambiri mma bank osiyanasiyana,ngakhale ana aku zibwenzi sazavutika mpaka kalekale, bomanso limamulipira ndalama ngati president opuma. Inu muli ndi chani apa kuti muzibwebweta, kumtunda kumtunda!! Iye akuziwa kuti mukumuchemerera?Kupusa, mix mukungogonanso pa mphasa apa makape.Mpakana maso pamtunda zomwezi? Ndi a mbwiyako chani?

 12. Sizigwiridzana ndi APM idzi,kodi khani ndiya liti, mayi Joice sanaipedze ndikuisuya,bwanji sananene kuti khaniyi ingotha? Khani ikambidwe ndipo idziwike mutu wake. Tchimo ndi tchimo olo mutalivalika jekete ndi tchimo basi. Is what Lucky Dube said b4, he’ll be happy if he’ll see all the people are equal in the eyes of ze law. No matter kuti anali president, lamulo ligwire tchito basi. Mkasa anati lamuro lopotsa phavu,liri ndi mano achitsuro,yemwe ali pute lithana nae motsayang’ana khope kuti ndi ndani?anali ndani? amapanga chani?ndi wafuko lanji?kaya ndi m’bale wake wa ndani? Ilo liribe nazo tchito. Musie ma judge aweluze kenako ngati angadzafune kukhulukila iyo idzakhala khani ina. Naeso APM akadzaba kaya akuba,akadzangogwida naetso lamuro lidzagwira tchito basi.

 13. Kodi inu aboma mwatsowa chochta tsiyeni muthu wakulu aphume mwaiwala kuti kunali misongo kale ndani kodi amene anachotsa ngat mulibe ndalama musalimbane ndimuthu wakuluyo

 14. #Jelson its all about time… U tnk till today azionekabe like he is 30? Give urself 30 yrs from today ngati muzakhale the same.. Somethings even money CNT buy,, getting old is one of the tngs

 15. Kkkkk kwalira kumtunda kkkk, kodi ameneyi ndi Bakili Muluzidi? Ngati yankho lake ndi EEEE , ndiye eee dziko ndilodzunguliradi eee… Nkhope ya kuntunda mpanakuoneka chonchi?? Ine sindikukhulupilira ndipo sindikumvensetsa.

 16. Peter mutalika mutumwake siziyenda akuwonangati bakili mulusi angafanane ndikutunda liphupa shitekete abaki woye boma la dpp mukamalimbana ndi nsheya muzingofutika

 17. Achalume kuchiteketa uku!!!! Munthu uyu aaaaaaaaaaaaaa ndikakumbukila mmene anali pa udindo wake aaaaaaa ndikulemphera kuyakhula,ulemuwani munthu wankulu. ndamphunzila prayimary yaulere ndi zina zotero kamba kameneyu.wina aliyense amalakwa oro iwenso perter ungandiuze zoti [email protected] zopunsa ngati brather wako unja .brather wako anamumangatu mwana waketu usaiwale zimandimphwetekatu ndikakumbukila B Careffffffffffffff

 18. If i hv chance to dictate i will say bakili is best president in malawi ever ever hv,john mtembo is best opposition reader malawi will ever ever hv.

 19. I thanx many who have liked my comments I humbly thank you guys once again my idea was Malawi as a country we have failed hence our sickness exposed in the massive failure of many valuable sectors of our government systemes like agriculture and education just to mention a few

 20. Thank you to contact with the French lady who made me happy this month Ms. jacqueline guichard. I received a loan of €
  45,000.00 and several friends have also received loans to its level at no cost in advance. I publish this post because currently there
  are only criminal on the net which only hurt the people it I’m good with that loan. Today I have solved my problem. I thank the
  honest and generous lady.Take contact, she is honest and sincere in addition, the loan offer is free.
  Here is his email: [email protected]
  thanks for understanding.
  Please share: the message to help those in need

 21. apikane nkhani syakuwalanga idilisa kalisinje kuwecheta ngani syamdalaea kwasa ndawi ligongo wakulungwawa kumatumbi kumachenje kumbugu kwesokoche nagakwikuta nigona ngamtanda jwine tuchiwenesyana moto gamasanje wa dpp wosope mmatongo mwenumo

 22. munthu ndiokalamba uyu uzipitanaye kuti iiiiiii usiyeni mzanu apumule mulandu wakalekale mukanaukumbabe eeeeeee eshi mukusowa zochitakapena mwina mmmmmmm ayi sibwinokoma

 23. Mr president mupezanazo minyamatu zimenezo, osangomutaya bwanj?? Nkhalamba ngati imeneyo muzikhalanayo jijili jijili

 24. ndichikhala ine piter muluzi ndikanamutaya adzipuma munthuyu komaso amweyi ndiamene anawatora iowa lero lino ndi ndichochezera chao munthu ndi bambo wao or kuti mayi amene wa achina muthalikawa chifukwa anawakonda mu UDF nthawi ija munali mitu ya bho ya anthu azeluso koma ndiko nanga awa achina JB bwanji simukuwagwedeza

 25. Uku ndikundunda kwa zithunda zonse ana apatawoni, amatetule ,mfumu,munthu wamkulu kuyambira chitipa mpaka nsanje.palibe a ngamututumunse ANALIPO akuti amututumuse KOMA analemphera, timakhala pa mbuyo mpake ndipo tizakhalabe pa mbuyo mpaka mitsitsi ikazaola ifenso mansamba tizayoyoka ANA ACHEPA.Mukunama mbamva inu mbudzi imadya aimagilila,ADYA ANGA@ndipo papita anthu angati chipumileni munthuyi???mukakhuta chimanga chokadzinga muzamakambe zamunthuyii mwamva???? Musiyeni.mkamwa mwanu mumayambwa mukapanda kuyakhula zinthu zopunsa et.

 26. African leaders have one problem that is wealthy competetion.Any president want to be the richiest person in the land by the end of his/her term.You will find villains praising these presidents wealthy without telling us where they got the money.I remember that theres was time when people were fighting just because of Muluzi and Kamuzu wealthy,When Bingu came back from exile where he was fired from PTA in Lusaka, he formed United Party and lost in general elections of 1994, he came sixth. He lived in Area 47 in a three bedroomed house and had one small hiace mini bus written Bineth which he was running. Muluzi later picked him and appointed deputy reserve bank governor and the rest is history. By 2008, he was a multi billionaire, a thing that can only happen under the nose of docile people.The same thing happened in 2013 people comparing Joyce Banda and young Muthalika’s wealthy.We are in deep hypnosis..Better we be recolonised again we have fail to govern ourselves…..2019 the forbes will tell us That Peter Muthalika is the richest In the Land .mark my words

  1. problem is we born to vote these others the born to be voted but I wish malawian the should realize one day dont go to vote these fools and mind our busines because is same u do u dnt d

  2. Thank you to contact with the French lady who made me happy this month Ms. jacqueline guichard. I received a loan of €
   45,000.00 and several friends have also received loans to its level at no cost in advance. I publish this post because currently there
   are only criminal on the net which only hurt the people it I’m good with that loan. Today I have solved my problem. I thank the
   honest and generous lady.Take contact, she is honest and sincere in addition, the loan offer is free.
   Here is his email: [email protected]
   thanks for understanding.
   Please share: the message to help those in need

 27. kulimbana ndi tcheya mapeto ake ndizija kumangofa osadwala mukulimbana ndimilandu yoti mboni zina zili kulichete Fupatu lokakamidza silichedwa kuswa mphika nkhani imeneyi ena alandilanayo Red card

 28. A Malawi timayiwala nsanga Bakili ankanena nthawi zambiri kuri CHANGU pa MALO lero mukafunse kuti anaba kapena ayi.Komanso anakweza ma judge angati?nanga kuti achina Mutharika apezeke pomwe alipopo engineer ndi ndani? Ango mutaya zadutsapo izo

 29. we will never hav smile president lyk him in malawi, basi becz we had deases in our mind, we think of today nt tommrw, wobwe akumuimba mulanduyo anapanga chani malawi muno kopotsela kutseka ma school, ndikwapatsa anthu ma T shrt wojambula chimanga basi, siyeni munthu wakulu apume sikuti mukamanga ndiye tisakufotelani ayi mulibe ulemu anthu wosanga mitundu inu

 30. Chitukuko chikukukanikani mmalo mwake mukulimbana ndi munthu osalakwa…..kodi ndalama zimene zinapezeka kunyumba kwa mbuzi in a inamwalira ija inapita kuti? Musiyeni munthu akhale ndi ulemu wake ife umphawi tauziwa mu ulamuliro wa galu uja mumamutcha bingu uja. …..agalu inu

  1. Iyeyo ndi iweyo mwina nkuthekanso kuti iweyo ndi amene uli mbuzi kwambiri. Kumachepetsa kulalata nthawi zina ndibwino.Mavuto a za ndale ali paliponse pa dziko lapansi.Tikamadalira kuti uyu atithandiza mapeto ake umphawi sungathe

 31. mwana kubadwa m banja mpaka kukula tikumva mulandu umodzi wa a chair nanga atsogoleri enawa milandu yawo adzayankha ife titamwalira,koma malawi walero ndiwotani,achair don’t regrate mmenemu ndimmene adamulengera munthu

 32. Leroooo aaaaa zachikaleeee. This is the big man remaining among the living malawian presidents please leave this man for God’s sake. Apume mu ntendere wake.

 33. Our concern shouldn’t be on a chair case only our entire political system is sick of corruption no wonder hunger is our friend more are to die

 34. l feel ashamed of these corrupt cases against our leaders.What image are they portraing to the world.They do forget that we leave on fundraised finances that our beloved brothers and sisters out there are campaigning for.Even now look how they are giving Government Tenders,is as if they are receiving deceased benefits.What a shame!!!!

 35. Noah politicians are sick people they are like a virus to our country traitors our country has lost a lot now we don’t have food yet we are busy clapping hands for thieves we are sick. All parties needs mental reformation

 36. Adali a Chairman nthawi..! adawafunsa anthu kumsonkham wina motero..! Ndamva anthu dzana ndidakutukani {anthu onse:AYI..!} Ena akut dzulo ndidakutukanan..?{anthu onse: AYI..!} Tsopano leo ndkut panya panu..!! {anthu onse..! Lyolyolyolyolyo,uku,akuimbira mmanja ndikunena. Acheya Acheya Acheya……..!! Acheya oyeeeeee…!!!!

 37. Zopanda Pake Basi.Mmene Mudayambira Muja Bwanji Osangouthetsa Mulanduwu.Kodi Kuchoka Nthawi Imene Ija Mwaononga Ndalama Zingati.Zaziiiii,,,,,,,,,,,,ambiri Ndiokuba Koma Kusagwidwa.

 38. fighting a never ending battle..its high time the offhandedly ones unite to fight the conniving ones osati kumangotokota apa

 39. The fact that no one is behind bars despite the many billions Malawi has lost for the past 25 years it shows how sick our leaderships are I can’t trust any party

 40. Thanx Symon for likyn ma comment its our country we must love it die for it build it protect it let’s change our thinking status

 41. Corruption is a dangerous animal that is so deadly than war it makes countries fall the laws are weak the judicially system become ruthless and vulnerable to evil works devolopements are fake doctors are heartless. People die

 42. How much dat Bingu Wamuthalika corapt?if u cannot answer me dat meanz lets to leave it coz ndinthawi yomanga umozi ino to build 1 nation as malawian,In Lesotho we have politics kumapezeka kuti anthu aba ndalama zochuluka koma angoti musiyeni avutika yekha pamene if buzy mangisana solution ndikumangisa.

 43. That’s why Africa is poor dyers the prisons are built for the poor to lot the reach are untouchable …what a shame!!! Our countries lose a lot of money tracking down cases that just disappears… Currently hunger is hitting hard when billions are with minorities…traitors…country. Sellers…

 44. mwawononga ndalama zingati zoyendetsera mulandu umeneu, uyu patavuta bwanji sangapite kundende awa ndi achalume, lipupa asyene njuwa…

 45. Pa malawi pano chilungamo palibe, zowona mukufuna kubisa chilungamo koma anthu atadziwa ndithu kuti Bakili adatenga ndalama. Mesa ndi Dpp yomweyi idayambitsa nkhani imeneyi ndipo umboni udalipo kuti adatenga ndalamazi. Mulungu zonsezi akuwona akukanthani sure. Wina ku khoti konko mudamugamula 4years koma adangoba K 4 800 ndiye awa basi apitirize kukadya ndalamazo sichoncho?

Comments are closed.