The hit-song Chauta ndi wamphamvu that was originally performed by Evison Matafale but has gained prominence after a redo by San B who has involved Nepman and Young K will land the three in trouble.
Media reports have quoted Matafale’s half-brother, Toza, as faulting the two for not having sought prior permission before redoing the song.
Malawi24 understands that Toza has since taken up the issue with the Copyright Society of Malawi (COSOMA) and Musicians Union of Malawi (MUM) to discipline the two.
San B has been known to redo songs of other people with Saleta Phiri and Paul Banda being some of the people he has used their music before.
Nepman was once accused of stealing a song he was featured in Chilawe changachi. The owner of the song complained that Nepman was performing the song in stage appearances as his own.
It is not yet known if the Matafale family is considering taking a legal action against the two.
Bola ife tikumvera nyimboyo kkkkkkkk San B nd dolo
ifeso tikufila yomweyo pa theba pano mix manyawa mafilu okhaokha akuna nkinga dont arrest them ang’eke probrem malawi musamvele anthu achamba mwatani kodi amalawi nonse mukudya chamba kodi?
Kuba kmeneko kkkkkkkkk osapepha bwa
Palibe zomamgana apa nde mwamange onse akumayimba nyimbo za Allan namoko wa kaye
its all about messege…..mesa chauta ndiwamphavu….. MATAFALE SANA IMBIRE AZIBALE AKE OKHA ….KOMANSO NTUNDU WA AMALAWI…..NDE AZIBALEO ATHA KUKHALASO KUTI SI MA RASTA NGATI EVISON…#Bless
kkkkkkk
sindikuona chimene alakwitsa,km poti lidangozolowera kudana ndi anthu a luso,mwina akufuna awaphe ngati mmene adaphera Matafale,amuyaya mukhale inu, km ife nyimbozo adatiimbira bwino ndipo timazikonda.
sindikuona chimene alakwitsa,km poti lidangozolowera kudana ndi anthu a luso,mwina akufuna awaphe ngati mmene adaphera Matafale,amuyaya mukhale inu, km ife nyimbozo adatiimbira bwino ndipo timazikonda.
Sports,Political ,Business
how many times were you listening to that matafale’s chauta ngwamphavu and how manytimes are you listening to the same track only that it was redone??? ngat chauta siwamphavu then San b ndi azakewa ndiolakwadi. otherwise nothing wrong here. majelous Basi kut thoo!! munakhala bwanji?????????
Kubeledwa nkowawa guys mukongonena poti sanabere inu komaso mkuti anayiyimba bwino ashina Sun B anasithapo chani iwowo zachamba basi amangeni
Iiiiii zanyanya kumalawi oyimba onse eti kubona zikatha .
Hey my people please work up!! Its a matter of memory to the owner, thats all. Ndiye mupite ku Zambia mukamange Dalisoul first coz mayamba zachamba tsopano. Umbuli kapena Jerous??
kodinso satanikiyo yochita kumulowetsa inu nomwe? zamanyazi majelasi thooooooooo
Kodi eti packet ya sugar ndi bwanji???????????
@@(1:(0:1:Kodi tidanirananji?))
mmm koma nkhani zinazi anakaimba muchizingu munakatinso abela? komazinazi abale nyinbo ilbwino iyi ine ndimangoi bweleza bweleza
mmm koma nkhani zinazi anakaimba muchizingu munakatinso abela? komazinazi abale nyinbo ilbwino iyi ine ndimangoi bweleza bweleza
mmm koma nkhani zinazi anakaimba muchizingu munakatinso abela? komazinazi abale nyinbo ilbwino iyi ine ndimangoi bweleza bweleza
But y ma complants nkhani ya zii ngati imeneyi dont u kno theres so many musician amene amaimba nyimbo zoti zinaimbidwa kale without zinkhani koma inu mmmh; its fyn i kno de story jealous thoooo osanyadira kuti its rememberance
San b ,Npman mmakwana osaopa palibepo nkhani apaaaa, iyaaaaaa
uku nde timati kumpusa kusowa chochita okuba onsewa mmalo mowagwila mufuna kumanga mu2 ot akupanga zake kupusa open up your eyes maso pasogolo #san_b_nep_man_young_k like david say #OSAOPA
anakhala ķut yomwei waimba busy sigñal bwez tkuñyadila koma pot nd achibalewa zalakwika??
aya ma musician asiyeni elo atikumbusha vakudala va Evison Matafale.Gwirani kawalala mkulu wa Cashgate mu government. Sewenza kuti udyeko,ma jealous awe.
Dziko Lamalawi guys ndilolephera limalimbana ndi zinthu za simple akulimbana ndi anthu oti angoimba sanatukwane koma kulimbana nawo ayiwala kut dziko la2li iri pa moto wazaoneni ndikuvutika ndiumphawi kamba ka ndalama zomwe zidabedwa ku capitalo zija sono mmalo mosova mavuto amenewo mukulimbanana ndi zinthu zoti sizingapindulire ziko why my country malawi bd wise pochita zinthu taonan amalawi tili pa moto wazaneni kamba kandalama zomwe zidabedwa zomwe zikadathandiza malawi kukhala pa map koma kuli zii anthu olemera kale ndi amene akusangalala choncho musathamangire zasopanozi kamba koti ndi zophhweka ai muthane kae ndi cashgate then go through with oyimbawa. tipange malawi wabwino wolemera ngati maiko anzathu osati kulimbana ndi zinthu zomwe sizingakweze malawi
Osakamumanga Dalitso anaimba = ndani andichilitse ujabwa?
mbuli mukukomenta zanzi pano kusumilana kumatengelano amene akuva kupwetekayo ndiye ngati Toza Matafale akuona kuti ndichosakhala bwino wina kuimbaso nyimbo iliyose yam’bale wake akuyeneladi kupita pakhoti matafale ndani sadziwa kuti adafa ngati nkhuku? ndipo kuonjeza apa iye mwini adaimba kale ma albam awiri yomwe adatulutsindwa ndikugulitsindwa ndiye ndichanzeru chanji kuti mbuli ina ikatenge nyimbo yamatafale ndikumaimbaso? nyimbo zamatafale zilipobe ndipo akuzigulitsabe m’ma shop ambiri kulibwanji kugula nyimboyo yake matafale ndikumaivela sitingamukumbukile pamenepo komaso timakhala ndi 28 Nov nditsikuso lomwe timamukumbukilaso ndipo sindikuonapo chifukwa choti adaimba nyimboyi ndicholinga chokumbukila matafale no! San B ndichizolowezi chobweleza kuimba nyimbo zayeni:
.Moda
.Anjiru
.Toza
.Chizondi
.Hazwel
.Yanjanan
.Chokani’s Family
Musamutaye Toza pangani chimodzi mpaka aone polekela pajasa mukuti san b adabona kagulu kamene kamakana kuyenda ndi mablacks ati amasuta chamba ndiye mukuimba nyimbo zawo?
To say the truth nyimboyi ikumveka bwino. Olo mwiniwake akanakhalapo akanayamikira.
guyz muimbenso poison so sweet mwamva????? mukutha mukutha kuimba ndipo ngati apite ku Court musakalipire ….ku malawi music inalowa pansi kwachuluka ku burner
Ndinavaso a mp alani ngumuya anayimba yomweyi ndezitha bwanji
yooooo guys mwaimba bho palibes angananee zilibho
Flamez sizathekaso kukokelana pansi basi wakeup u bunch of sleep heads dammmm!!!!
Pali zifukwa zenizeni guyz osati izizi kikikikiki
iwowo anangofikira kuimba asanakapemphe chilolezo ku chileka.kaya zanu muisolver mwakula mwatha.
If you sing a spiritual song. You are preaching the Word of God, The song belongs to God and you spread it to many souls, so if people sing the same song it means they have received your preaching, that’s your goal of singing. If Matafale sang this song to win souls and praise God, then he is happy people singing these songs, unlike you focussing on money as your god. Well done Son B and Fellows. Behold the Temple curtain was torn during the death of Jesus on the Cross. Just see the hidden now. Who triggers your speech in your heart?
Oyamba ndi San B kuyimba kawiri nyimbo ya wina? Misala eti kodi mwasowa zolembano……..
Makape amafuna kukolola posalima.lyf in jail bas mwina timveko zina
if u eva imprizoned mo than 5 pple due de issue lyk dis,u can do accordngly 2 thse dear brthers BUT!,if not i should not hear dat u h’ve jailed thse men,,,,but if u delay i wll narrat 2 mr Shphrd Bushri 2 do smethng upon them to aim at rescuing thm and cursing u!!!! i min those who r follwng ths stry 4 these nicknamed guyz Sun B, Young K & Nepman, MafewDefiah!!! az Shadrk, Misheck and Abrnegoh respectvly, Keep It Up Guyz Never Gve Up!!,, Those Frogs shd not bother u az wel az me,,,,,,o de best u tri-guz
Amangidwe kuba sikwanyatwa
iiiiiii amalawi tatopa kumunena prophet pano mwaganiza kuyatsamula miromo yanu kwaoyimba? hahahahaha matafale RIP koma mkazisatira kwambiri nyimbo zomwe amaimba ma missionaries wo nawoso ndiakuba amaba ma meto a malemu joseph hill zonse nyimbo zawo kwamene amasatira nyimbo za raggea plz ingowatayani akuba azanuwo?
Uhuuu
zoonad, kukhala mmalawi nkulimbad mtima kkkk
kkkkKkkk kuyimba kwawatopetsano sopano. ma kapewa
Aaaaa Walembawe Wanama Sangamange Tie Betchu Bwanji!
Kodi mukamat amalawi amalawi chimakhala chili chan ?? Mukuganiza kuti mitu ya tonsefe imapeleka nawo mfundo zokhuza zimene mumawelengaz ?? Mumawaziwa amene amapanga post zoterowo so why nat pointing ya fingure straight to them ?? Mumaopa eti ?? Ndie mumaona kut its beter to put the blame on Malawians ?? If you blaming Malawians then then who you ?? Instead of commenting accusative comments here be the first commenting on how to change.. pointing anyone will never change anything … Everyone has his own opinion and to them its facts … So respect every opinion and overcome it by telling wise nat dissin …. Gud day
kkk! word up,iwowo ndiamalawi akujoni mwina..
Hahaha ndie asankhe mbali imodz kkkk
Iiiiish zalowa umphawi i used to say fuck the police. .now fuck the jail
nyimboyi ndinaiwala koma mmene yayimbibwamuso shaaaaa ine kunva kukoma kundikumbusa zana,koma guys mumatha tayimbaninso ina.
Malawi don’t judge these three brothers bcz i don’t want you Malawi to regret after judging these three brothers, San B is a well known artist since long time ago and he had been sharing the stage with Matafale before San B became a born again, and now San B is showing up a good memorial to the late artist Matafale, so i don’t see any reason to send them in prison. Hi San B and ur brothers imani njiiii pachoonadichi Mulungu akumenyelani nkhondoyi, and i wanna give you new names for it and these are Daniel, Misheck and Abilinego, opikisana nanu he/she will get what he/she deserves. Thanks.
that is a remix, amalawi kupusa palibe mulandu apa.Look at American music industry alot of remixes, they do remix the song which is a hit and still fresh on the market, nde nyimbo mukunenanoyo ndiyakalekale and they just trying to revive it,we already know that it was done by Matafale.
Nsanje chaipa nchani pa nyimbozo kkk malawi eish
wat remain is to sel the ho mw to america.
nkhani yosagwira mtima iyi…. a makina mwapala apa
mmmmm guies..sometyms musamangolemba ma dry copies munakavaya kwafanzyo mkukafunsa bhobho…ur story is lacking relevance, truthfulness, balance and fairness…. plz consider ourselves guies
Hahahahahaha Reporters of Malawi
Kutha kwa nzeru zopekera nyimbo za newone ndizimene zavuta
Osamanga akuba ndi kuzembetsa ma albinowa bwanj
ngatidi anaba nyimboyi, apitilize kuba zina ndithu chifukwa inali bho heavy.
Mesa its atribute to matafale
Atyoche apa usawi basi amalawi
Provided we know the truth on this matter
Mbwiyache,redo ikhale nkhani?asa nyasaland opepela sanamwalirebe eti!NEPMAN ndi SON B satikummbutsa nyimmbo zokoma zija apa?
Hager Werken Embalming powder hot pink 98 % made in Germany contact me on +27780016959
Sanabe Koma Kukumbusa Chikale Cha Evison Matafale
koma mwafatsa just jealous y uleave bushiri and arrest innocent pipo goverment of Malawi ur out of mind nonsense serous asiyen kod njala ? zaziiii asiyen athu
Kkkkkkk
aToza aona kut zalephera afuna amudyere San B,, heeeee “Omukonda San B amamukonda mbali ya kwanu ndili kuno konkuno ine aaaaa ndili kuno kunokooooo”
Listen Busy Signal’s rdm mumadziwa kubera kwa nyimbo inu? What’s wrong? San B ,young Kay don’t be discouraged
Anthu onse amayimba nyimbo za wanthu enawa samamanga bwanji?
Mwasowa zokamba eti.
kkk esh! No comment still Typing…
Dziko loipitsitsa mwina umbuli ndiumphawi.mukangofika form 4 mmaonangati ndiinuozindikila kupangitsa maanyazi
Malawi sadzathekanso, mmalo mofunirana zabwino tikumangananso.malawi umandikhumudwitsa
enawo azingoyimba nyimbo zam’gandazo aziti R musik…ngat mukulephera kuimba zolongosoka mungakwanitsa re-do zamatafale evison?…San B wakuposan zanu zomwe mwayamba nsanje..kkk
Talent is talent and is God’s gift
Kaya asova zinandikwana ine
Forgive them
prophet mboro yemweo
My fellow malawians,there is no music without copying someone.Those who copy,means anagomera the one who did it.
My fellow malawians,no music without copying someone.Those copy,means anagomera the one who did it.
musawaopseze coz eeh pano ndie achipha zenizeni.
Musicians plz learn to respect your friend’s talent I never say it is wrong to redo your friend’s songs but first of all follow right procedure before you come upwith the track , if you do so I think both parties will enjoy your talent
Kaya man……koma adayiimba booo2 madolo atatuwa
Kunena zoona anyamatawa nyimboyi ayimbaso bwino kwambili.kambilanani tonse nda malawi.
ma blacks amayimba nyimbo za buku la 7th day bwanji samangidwa kapena iwowa ndi kwaya?
mmmmh!guyz munthu walakwa chan
Nchiyani kod amalawi ?
Cool
Tupt zanu amalawi ndife otani what kid of pple we walawians ee bas mumangofuna munthu avutike mukatero muzimuseka fulshe!! Majeras bas akamakhala amakonda majerous sianzathu awa maheters ndipa machine thothothoo akudana weee mbuu!! ndashuta;):p;( 😎
Nyimbo ndiyamau amlengi,,mwini wake mlengi ndiwamtendere koma kudziko lapansi alibzy kukangana,,,,zipite kwakaisala!!
Hahahaha! They Have reminded me someone who said,” if that one did it,those ones did it why can’t we did it?” Awowo awo maluzi awapweteka ndiye akufuna achina SAN B mungo wachula kenakake.
malamulo amat wakuba amangidwe
Malawi is fine but people stay in that country are all fucked up
Mungotaya nthawi
Mukuyankhula zambiri chifukwa San B wayimba bwino?let’s talk developmental issues koma izi sizitithandiza ayi!Ask God to give you a talent like that of San B,San B salimbana ndi munthu ayi zipatseni ulemu
mmmmmmmmmm za ziiiiiiii ndiye bwezi kulibe ma variation
inu abro tazitayeni zamdziko izi zikuchedwetsanipo apa isaaa!
Kma malawi tsazatheka palimvuto apa
sun B bebi swagg up big up put head up stand on toll never give up bring it on.
Malawi sazathekanso basi. Achina Toza zangowavuta basi asowa yajada km sapanga choncho ndife amodzi. Nanu a COSOMA ndi a MUM timadziwa kale kt ndnu wadyera teleku pamenepa mwapeza cocita. Inu mene nyimbo #wamphamvu remix inatulukira bwino zakunyasadi ine ndkuziwa kt or mwina wa Evison mzimu wake wanasangalala kwambiri. Malawi sitingapite paxogolo khalidwe lomweli.
Sivuto mpaka kuwamanga but akanapempha permission kwa matafale family that so .achita bwino tisamayiwale matafale in other style
FREEDOM.! Mwina tingawone kusintha, #YEHOVA asanawononge!!
Malawi iz crying for……
Malawi iz crying for……
Sizachilendo munthu kuimba nyimbo yoti inaimbidwa kale, mwatani kodi?
dis is b**l sh*t kma ah nyimbo yake imeneyoyo ? N
mo fire sun b
wamiseche salipidwa akanakhala kuti amalipidwa bwenzi atalemera
so how can a brother sue as if he is e one who composed it..
Ngati zilichoncho ndiye muwamangeso achoir amene anayimba nyimboso yomweyi ya Matafaleyi
Zazii pali nkhani apa?Jelasi basi!
Amalawi munatan kaduka malo momanga obena mikumanga oimba malo momanga bushiri kut ndalama wazitanga kut malo mumuotan joice azayankhe milandu amasulen anthu osalakwa
Kapena amafuna aziyimba munthu yekha nyimbo yikakhala ya mtundu wakwawo okha ngati mene anachitila. Song Title Bwenzi Langa late Robert Fumulani anayimba kenaka late Gift Fumulani kuyimbanso ndizimene mukufuna zimenezi
Busy signal anaimba nyimbo ya Don williams “THE GAMBLER”koma he ddnt lebeled as thief! koma ku Malawi sitizathekaso basi
ndangomva nilibe polobulemu ati wachimalawi…..Kkkk. ……timuyembekezele zotani mkulu ameneyo.
Too bad!
matafaleyo adamwalila liti ponena kuti waba nyinbo
Amalawi Zinthu Timazitengera Pamgong’o!
Malawi sadzathekaso bansiii
Sanabe ndi nyimbo yam’baibulo sizimenezo nsanje bwanji San b ndi neo man mumatha achalume
Bwelan muone KU botswana ambili anaimba za eni ake koma no vuto NDE madolo aimba bwino mubwela kumati aba za ziii pezani zina zonena kip it up SAN B,NEPMAN+YOUNGK
Patha nthawi yaitalibwanji kut azindikire zaozo? Sbwnoyi nthawi yonseyi sankazimva nyimbozo? Aaa! No! Samamuona mzao waku jamaica Busy signal? Popeza nayenso amaimba zamzake koma alibe nthawi yomusaka chifukwa amakhalazoti akukwezanso lusolija.chifukwa tikati tione nyimbo yaatatuwotu mwiniwache anaidyelelakale.
Pachisilu pake Toza matafale, satha kuimba…. Chifukwa ndi hit song ndiye basi…,pachisiluuuuu!!! Amalawi sitizatukuka
Kkkkkkkkkkkkkk ha ha ha ha ha ha ha ha ha ha eheeeeeeee mwasowa chochita eti???? Mvetselani tsono, mukamangenso a boma for implementing one village one product (OVOP) chifukwa it was not their idea. It was Brown Mpinganjira’s idea but the govnt store and implemented it. Yet when Mpinganjira complained munamuyankha kuti IDEAS HAVE NO COPYRIGHT OWNERSHIP. Mxiiiiiiiiiiiiiw mwangofuna kuwabera anthuwo mwina mukuonangati alindindalama. Mumaleka kungowapempha mwachilungamo bwanji????? Foolish.
Pena pake kumalawi tilibe ufulu kodi basi tizifinyika kodi ambuye mulungu mubwera liti zoona ana anufe tizingothera mundende basi
Lack Of Apreciation Wen One Has Done A Gd Ting Honestly To Say It The Track Is Dope,,,# Hahahahahahahahaha Amalawi# Palibe Pulobulemu Apa*** Am Lovin Tha Song,..
mvelan iyi..http://mdubvibe.com/song-details/?sid=11007
ayambekaya amanga chimwemwe muhango ndi nyimboza Rabecca malope ngati wankulu akuba nanga anafe inenso ndiimba zopusa
MY NYASALAND MALAWI:Munthu akalemela ndi wa satanic, akasauka ndi wa ulesi,akakhala osakwatira ndi hule,akakhala lova ndi wakuba, akakhonza mayeso amawonera, Chipani chikawina chabela, Ugule chigayo wakhwima SAN B. DIS Z NYASALAND MALAWI,,ZOVU ZEDI ODALA KUZIVETSAA!!!
waiyambisa nkhaniwe ukufuna kutukwanidwa?peza nkhan yolemba cz nyimboy ndye yaphikika than mwini wake ma3lu defiyaaaah!!!!
hehehe lamulo lazimenezi likuti chani ndisanakomente sete ?
Hustling kaa
Gyz tien a Malawi tikondane, Ndiangat aimba nyimbo zobwereza kumalawi? Ndipo ndindan anaimbidwapo mlandu? Nyimbo bax pot anthu atchuka nayo wina apezelepo kanganyasee mpakana! Well done San B, Nepman and Young k mumatiimilira inuyo 2019 wina aimire pampando wa president,wina MP, wina khansala 2019 BOMA!!
Kkkk…. Umbulidi ndi matenda eti, paliso nkhan apa!
Prison my foot! Ayambe ndi a cashgate kubanduka ku maula. Pamenepa tchuzi kaye ndithu.
Matse Anaymba Ya Billy Kaunda_mwapindulanj Nanga Munawona Billy Kaunda Akudandaula? Ths Is What We Call Remix, Mumafuna Nepman, San B Nd Young K Aymbe Ya Gwalad Tumbocid Ndy Smukanawamanga??
Boma likulephera kugwira mbava zoxez nde laphwekera anthu oimba nkumat mbava? Angofuna kuipisirana mbiri bax
Mmmmmmmm koma inu mmmm
San b,Nepman keep on fire burning,never give up!!!!!
bola ine ndikunvela nyimboyo and ndaidziwa kwambili coz of these u call them thieves kkkkkkkk malawi dziko la nsanje
Kikikiikikikiiki!! Palinso mpaka prison apa? Koma yaaaàaaa!!! Law ndiyovutadi koma. Kayamwe
San Benet sokela satha kuyimba kwake ndi copyright that’s what he know zidawakanika,he did copyright Paul Banda song as well.zokakamiza
Palibepo za prison apa. Bwanji Kodi? Aaaaaaaa! Kharani ngati anthu ozindikira.
global rule is that you can re do any song of anybody who is late if atleast 10 years erapse
Kungoti tinene zoona anyamatawa chinyimbochi achikwapula mpakedi anthu kuchita majerous koma cmungapundule kanthu iotu alibe probulemu koma inu ma3lu nepiyaaaa
That song z jxt amazing n most of us we lyk t. They z no any prob on wat sun b dd lets us jxt enjoy the products of late evason matafale.
nde #busy signal akanamangidwaso cause every song busy do amamatula
hhhhhhhhh kkkkkkkk yes am indeed in malawi ……..
Toza ndi kamadzi samatha kuimba
Hahah Chipapapa!! Papa!!! Chinyunyunyu nyunyu!!!
Ola zimachitika chilolezo ndichofunika guyz
Dzuka iwe malawi dzuka
Nw I bliv in young kay (CMPHANVU ZANGA NDICHISOMO CHAKE,NDIOPASO CHAN WAIKAPO NKONO WAKE,DZIKO LITIWELUZA TKAMENYA NKHONDO YAKE) Here its in ua accusin them jct cox thy av spread the gospel news MAY U ALL LOT IN HELL
Are ma bracks the composers of mlomowuuu
Malawi malawi mmmmmmmmm no coment zip my mouth
Malawi24tu iwe usamale akukutumayo akupwetekesa.
akamangenso Dalitso pa nyimbo ya paul chaphuka ndichilitse.
Kusowa zomanga chani? Maunyolo achuluka kapena? Mmakanika kumanga an2 akupha ma alubino akuphedwa mkuona mkumat mmange an2 osalakwawa atani?oimba zauzimuwa amatengela an2 akujon kumatembenuza nyimbo zaweni wake osawakwizinga bwanj?
I suggest amange Kaye obena popanda chiloredzo onse
Chris martin:let her go,Busy signal:Gambler,one more night,personally,mwati mumulonde Nepia ndi Kaphuka komanso Burnett?agalu inu osapanga zanu bwa?Mwina ndinu nomwe munamupatsa Joseph Tembo minyama eiti?mxxxxxiiiiiewwww!
alani ngumuya naye ndiwakuba …if so…..example bizy signal nyimbo zija amakatenga permission kkkkkkk poor pple from warm hrt
kkkkk kayaa
No one will be jailed. Kanyimbo anyamatawa akatyakula bwino aka. (I also respect Matafale’s song)
Mmmmmmm guys kaduka lekani ,nyimbo iyi tayikonda anthu ambiri nchifukwa chake mukufuna kuti ayankhe mlandu.
mwadongosolo lake achina Son B akadayamba akumana ndi akubanja la Matafare atsanaimbe nyimboyo,,koma ngati sanatero ayenera kulandra chilango coz kumeneko nkuba sangapange ndalama pantchito yomwe idagwiridwa ndi wina….olo oimba akunja amene amaimba nyimbo zaena sikuti amangoimba ai,amakhala kut apasdwa chilolezo kuchoka kwa mwini kaya abale amwni nyimbozo…..copyright ndyolesedwa kulikonse
futso langa kwa inu amwene kod malinga anayimba ilov you ya nick komaxo busy amenyaxo john ya yemi kod athuwa anapepha chilorezo ngat sanapephe nde san b ndi azake siolakwa
Nyimbo ya munthu siingaimbidwe popanda chilolezo chamwini wake..kumeneko ndikuba ndip nzolesedwa nchifukwas chake kuli copyright society
Mpaka ku Banja nde inaimba ndi family choir2! Enawa nuisance chabe!
A moses chipote inu kodi a copyright anuwo azidikila nyimbo ikatchuka chomchi kapena akanailesa isanatulule bwa ..jealous yanu sikupindulilani enawaso angoyangana malemu awo abele kanyimbo kake kti atchuke
Mwini wake wanyimbo anafa musatipase busy
Moses Chipote inu ndi athu amodzi ajealous, kodi nyimbo inatuluka liti? Nanga akupanga clam anali kuti monsemuja? Vuto la amalawi mumakoka nkhani yopanda pake
But to say the fact here: The song was composed by someone( Evison Matafale)..these guys have just come up with the re-do …honestry San B had to take a step and consult The black missionaries band ( the band that was started by Matafale himself), and ask for a go-ahead. And am very sure these guys could not have said No! but the fact that they didn’t go for permission it like ” akuwadelera” anzaowa..which is very bad…..bolanso anayimba achina Anjiru eni ake ikanakhala nkhani ina…Komanso anthu ake ndi ife tomwe omwe tikanati tiziwanyoza anyamatawa kuti ” nyimbo zawathera, ayamba kumangobwereza zakale “….koma wina akaziyimba nyimbozi ndiye tiziti there is no problem?…No! ..there is a problem and that is ” Kusapempha chilolezoko “
acina busy signal,jah cure,romain uvirgo ndiena ku jamaica amaimba nymbo xaamxao kma samangdwa nde ixi nde xitixo d@s primitivnes
Zimatengela ndidongosolo lomwe latsatidwa kuti ayimbe nyimbozo
owo
Malawi wotembeleledwa nnyimbo ili bwno iyi kuposa mwini wake..
zamkutu!!!!
pasanapanu a police osakanga aja adaba ndalamawa bwanji
mukulephera kumanga ndikumalizisa milandu ya cashgate yoti inachitikadi & ziko lili mmadzi kaamba ka kubedwa kwa ndalamazi nde zoona mufuna mumange ma dolo woti angoimba? nde muyendenso mma church mukamatipeza tikuimba nyimbo za ena mutimange tonse!
Ndakunyadirani Man Mfundo Yabwino Amalawi Amadana Ndi Chilungamo
They ar fools y cant they produce their own songs
kkk malawi kuti buuu
Apa ndiye zafika pa boza komaso kaduka,, kodi nyimbo imeneyi yatuluka liti?? nthawi yoseyi analikuti?? ndindani samaziwa kuti nyimboyi ndi yamatafale,?? Matumbi, Ndirande Anglican, Loyd Phiri, Mau K, A Chirwa, Joseph Chadeleka, onse a HipPop bwanji sakuwamanga??? komaso inu olemba news inu bwanji samakumangani??? kodi zayamba liti zimenezi??
Mmmmm it is clearly that the song it’s not theirs and they don’t say it their song
Nosense!!!amalawi kwathu mkuponderezana..
Malawi
Oyamba kumangidwa akanakhala Michael Bolton yemwe anaimba nyimbo yot ‘Lean on me’ yomwe inaimbidwa poyamba ndi Bill Withers.sindkuona chifukwa chowamangira mamembawa,nsanje 2 much malawi eeesh
Alinayo andigaire pa WhatsApp. Nayonsotu ndi pirating. Bwino!
young kay u the only one umatha
Za zii inunso mmasowa nkhani eit simunawone even mayiko amzanthu ena nyimbo anayimba kale ena mkuyiyimbanso version ina za zii umbuli basi ndi umphawi zomwe mmantha
ha ha ha that y tili osauka ndipo ndizakhalebe osauka ngati moyo wake umeneu ungapitirire .
wat they dd is wat I called a cover no offence on that
Rumbidzai Manda
anyapala inu mwaonjeza san b pitiriza sanje bwanj?
Zaziiiiiii
Awa ndimadolo, kayaanabakayasanabe komanyimboyija yilibhoheavy
Dziko yolepheleka iyi aaaa
Zamkutu
I agree with this ,they stole that song ,same like dalisoul that song for chaphuka,come to sun B just accept that u that song was sang by matafale
Ine ndaikonda mene ayimbila kuposa eni akeo
Tigaireniko nyimboyo Big nafe tiinvere chonde Big
Whatsap #
kkkk ka remix kavuta
Zavuta amalawi chimidzi
Chimidzi malawi chimidzi palibe Vuto apa. Matafale he is no more or even anakakhalapo someone can redo
nanga ena anayimba nyimbo za allan namoko bwanji samangwida..ena anaimba zot “anapta ndinyanga zomwe kumanda, ena.. Achimwene muli bwanj.” bwanj sakumangidwa?? Zamkutu!
Honjo ndi reggae ndizosiyana nyimbozo zingofanana San B more fire kuti BUUuuuuuih
Ine nilibe polobulemu
za mkutu mxieeew
Ma brax nawonso amaba nymbo za culture amapanga blame ndndan?
Vuto ndi chan apa.malawi wachuluka mbuli zophunzira aaa…#wamphavu..now on repeat
Busy signal is international well known with music recycle and innovatives why not him and never been him???
nepman wangayo manyane samangidwa
I don’t see any problems of these guys Nepman & San B for there song…. problem is jerous Malawian people busy with other #Business wake up guyz and let others people’s do thy #Mission….Remember god separate us for reason
Ha ha ha ha Chilungamo Madolowaaa chinyimboochii anachiswaaaa and nyimboo zambili tikumavinazii nzobwerezabwereza. what mattters nkubvesesana basii nkhanii palibeee apaaaa
Mike Mugawa
As far as proper channels were followed , no case here because artists are supposed to get permission from someone. We have to know that composing a song is not a joke. This is talent and has to be respected and protected. Had it been that matafale is alive, this could have not happen or these two could have asked permission from the late great king of reggea music.
I love the song and I love Evison matafale and I don’t see anything wrong with San b, young k and nepman for redoing it, it’s a reminder that matafale was and is the best of all time so thanks to the three brothers that redid the song
Mmmmmm koma yaaaa, malawi wamoto
Ine ndipo ndikujambulaso nyimbo ya Lloyd Phiri muja adachitira ujayu. Lloyd mundimangisa?
All over the world they redeem songs if it is nice .And they can sing it even more than 6 musician .But my country Malawi, eeeh! is a crime . Remember there is too much churches but God is one and two much songs but one musician. Coz now people are just repeating what other musicians already sang about
Umeneu ndie ucitsiru wa waukulu agalu inu a News kaya 20_chani…. Bwanji mukuwayipitsa amzanu mbiri coz aliyenxe amadziwa kti chorux ija ndi ya #Matafale en da whole Malawian we owez respect him coz he oz a legend 4us plz plz plz thnkn twice b4 yo post yo sensles poxt lyk diz…. Mumafuna ayimbi nyimbo ya munthu wakunja kapena cani amphaka inu.. Nyimbo idatuluka last year en y y y y mukuyibwelesa nkhaniyi tym ino bwanji…?
Malawi malawi malawi kkkkk ayi ndinthu land of peace bt ful of jerous mwatopa ndikumunena bushili kuti ndiwasatanic you wll remain like that guyz work up open yo eyes and see
Malawi malawi malawi kkkkk ayi ndinthu land of peace bt ful of jerous mwatopa ndikumunena bushili kuti ndiwasatanic you wll remain like that guyz work up open yo eyes and see
Pautsilu panu
Mukumaleka kumanga oba ndalama zambirio bwa
pamalawi moyo wa nsanje suDzatha imeneyi ndi nkhani mpaka wina amangidwe eeee mwandiopsa
Amangidwe basi kuba nyimbo yamwini opanda chilolezo nkoletsedwa!
It happens siwoyamba
Nep man flng gudoo!!!!!…young k niceee!!!!!…san b flng bumbum!!!!
Busydii nde bwenzi atangolandira ‘life in jail’ basi coz of “Gambre” ya Kenny Rodgers, not 4getn the jst “sorry” by JB….kk! Nkhani ndkunvanaa btwn the one who is willing to re do the track ndmwini wake, but in ths matter a Nepman nd a San B amayenera ku chiller ndi achna Anjiru basi..(Matafale’s family)
Mmmmmmm Gambler paja anayimba ndi Don Williams eti??
They ask for permission to re do the song ngakhale a UB 40 akhala akuimba nyimbo za Eric Donaldson,if u remember very well Joseph Tembo anaimba nyimbo yaoimba waku Botswana and inailetse on the air waves
@TONY atsgo tiziti u dnt kno? Mumamukonda hvy Buisyman et. K! eeee adayimba ndi Mr Williams.
@BRIAN “They” u mean Nep and San? Mundiumboni wot they askd 4 permision man? Okie nde a UB40 nymbo zawo zmakomera muja amamenyanso ya redoing….aaaa zandkhudzaaa hvy! Hope nt o tracks?
Nde mwati ”The Gambler” ndi ya Don Williams Osat Kenny Rogers?? Kkk
Kkkkkkkkkkk Gambler twiiii twiiii twiiii twiiii evely man knows… kaya kwinako amati chani kaya kkkkkkkkkkkkkkk
Gambula ndi ya Kenny
Donn eti?? Ife tinamva mothamanga kt ndiya Kenny
Donn eti?? Ife tinamva mothamanga kt ndiya Kenny
Kkk! Sory guys, expecialy #TONY. Dat shud b Kenny not Don…..ha ha ha ha, “ndne munthu ndmalakwtsa” #singing_Saintsong
enawo azingoyimba nyimbo zam’gandazo aziti R musik…ngat mukulephera kuimba zolongosoka mungakwanitsa re-do zamatafale evison?…San B wakuposan zanu zomwe mwayamba nsanje…kkk
Kwathu kuno umbuli unatipweteka heavy! bt 2 say the truth sanaganize bwino amene awamangitsawo!
Chalakwika kweni-kweni n’chiyani? Ngati pena pake palakwika,chonde kambiranani mwaulemu ndi mwamtendere,musachotserane ulemu.Komanso dziwani kuti nyimboyi ndi yauzimu,yachilimbikitso ndipo yotikumbutsa a Malawi tonse za ntchito zake zabwino komanso za imfa yake yomvetsa chisoni ndi yosaiwalika.Mzimu wake uwutse mumtendere!
nde zwapweteka nd2
nyimbo madolowa atchuka nao
zdhlu zake ndzmenez.. Ena nsanje yawagwra nd2 Edward Kuntanga
come on Malawi! tili ndi anthu ambiri amaba luso anzawo ena amaiko akunja ena akwathu konkuno komaa bwanji samamangidwa, to be honesty mwina anyamatawa anapanga pofuna kuti tizimkumbukira Matafale, mukuganiza kuti Nepman sangathe kupanga produce nyimbo please Malawi wake up
Ine ndingoti “Mafiludefiya!”
Eminem did “What is love”
Brandy did the same with “Think twice” the Fuck are you going to arrest them for?
Kuzisatatu!!!!kkkkkkk
Haha eetu
Nvula ikagwa kuchuluka zolilalira but most high will protekt you guyz
kummanga San B walakwa chani osamakamanga a cashgate amene aba 577bn bwa?
Nep man motto kuti buuuuu mumathaaa zamubowa akasuke mkawa ndi poison
Mukadzaona oimba akuimba nyimbo za munthu wina just that,kupeka musik kukumuvuta.Other ways promoting Matafale’s legancy
Iiiiiiiiii zachikale,lean from jamaicanz this kind ov copy someone s song in different styles dey call t ridim.
Tink ov these songs dea in Jamaica
-brighter days ridim
-think twice ridim
-down by the river ridim
-sorry is a sorry word ridim
-night nurse ridim
-ragae music again ridim
-mama ridim
-cheaters prayer ridim
Just mention a few,nyimbo izi zinaimbidwa ndi oyimba asiyanasiyana ndipo ambiri koma sitinamvepo kuti wina wamangidwa kapena amangisana,ndipo nyimbozi zimachita kukoma ukamamvera.nde muli busy kumangisana nkhani yake iti? mmmm olo omangayo alibe manyazi ,I think nkhani ya njara yankhuzanso ku muzik industry .I .P MATAFALE nuf respect
If those cacoons does’nt know how to compose songs they shud contnu smokn chamba so that they remain ugly, if i respect Evi its bcoz of dat song, lamulo ligwile ntchito.
Amene ali ndi pulobulem, awamange. But 4me l lov th hit-song
Anthuwa yakula ndi jelasi basi sakufuna kuti tizikumbukila malemu aluso king of raggie Evison matafale kudzela mwa anthu omwe amkakonda ndipo akamakhala amatulusa misozi okha pokumbukila luso la oyimba wamkulu kamba ka ichi pofuna kupukuta misozi amangoyimba nyimbo zake kuti amweleko madzi. ndiye apapalibe chifukwa chomangilana mwatani kodi?bwanji simukulimbana ndiwokupha ma lubinowa?
Fire burn police
That’s Malawi I know
fire dem, dema wicked people kodi ngati zakuvutani osangopempha anthu asonkhese ndalama bwanji mwatani kodi amalawinu fo…….ool
Kwanthu kokuno ku Malawi komwe kunazaza ndi ku khomelerana.Munthu apange Radio station walakwitsa, Munthu apange ndenge ati ayi izipha wanthu Shit tizatukuka lit
That’s the word of God everybody can praise God using the same hym
these are issues to do with copyright zimene ku malawi kuno sitizitsata kwenikweni…redoing a song is not a problem but first permission from matafale’s family could have been sort…..people’s commets tend to take a blind eye on this no wonder grace chinga’s album was pirated….then mumva kuti wina wayimba ya grace album isanatuluke……..lets follow the rules and move on
Kamangeninso Gides Chalamanda anba nyimbo ya Bob Marley, Bufalo Soldier
easy ndi zokambilana izi ..remix /copying ndi zololedwa bola side inayo idyeko %
Busy signal bwanji amayimba nyimbo za anthu ena munamvapo kut wamangidwa?
Ine sindinavepo kuti BUSY SIGNAL kut wamangidwa? Kapena zayamba kumalawi kuno? Aaaaa amalawi tiyeni tikondane….
za ziii, osakawanjata lero bwanji?
amalawia mwasowa nkhani zokamba
Palibe zomangana apa waberedwa ndindani ?
San B uyimbenso ina ya nyeleke yokonda suga imangozungulira pa mlomo wakapu kenako kugwela mommooooooo ( watsetseleka) asakunyumwise
Aaaa why accused? its a gospel tune in both tracks of him n matafale komanso is a way of remembering him.Amalawi kodi mwatani?
Mmmmmmm ,,
Nanu musamakokomeze zilizonse nkhani ya nyimbo mpaka prison nde kwakhwekatu.wayimenyabe bwino ine pano ndikumvesela yomweyo
Tigaireni Big nyimboyo tinvere chonde
Nafe itipeze
osamanga obenawa bwanj? zachamba et
Nyimbo imeneyi anangotola ndiya masiye mwini wake anapita, ndiye akudandaula ndindaninso
zachamba bas
umphaw wafka pomatiganizitsa mombwambwana ndthu
Ndikuyambila iwe walembawe manyende ako ndipo mwini nkhani mavuzi ako olandila nkhani mbolo yako nawe ogemulawe pamtumbo pako {Nep man San B and Young K}kutimvetsa kukoma kuti wawawa nep man mafilu defiya (never arest you guys) kam’mangeni Dalisoul first zachamba etii
Amalaw mwanyanya kulndana,mind ur on busness &palibe cifukwa chowamangra, aymbaaymba bas asiyeni!!!
Ngati zili chomcho mangani mr malawi ,Aunt gettu ndi wina oyankhula ngati bakili uja koz awaso akudyela luso la ena….san b ndi no 1mo fire
that song rekindled my memory Evie.the burning sensation and realisation that Evie sung gospel well than these other crap calling themselves gospel artists
Kodi mumasowa zopanga post?prison iti?bwerani pa Firehouse muwapeza.
Nkhani zinazi kaya kkkkk
stealing from who? the late matafale? kulibe lamulo loti munthu akabera mtembo adzimangidwa
A china Daliso aja bwanj simunamange atayimba “mundichiritse?” zofaira zimenezo….i dont see any offence here……majelouse!!! Ndipasire machine gun! Bu!!!!!! Ndashuta!
Kkkl amalawi kaduka heavy. Even matafale nyimbo ya ndichilitse siyake. It was done by Phil Collins- heal me
Ndichilise anayamba kuiba lucius banda song originally done by alpha blondy(heal me) lucius copied it word by word but in chichewa
Yaaah!
Komaso machezo anaimba nyimbo ya Lucius mundikumbuke bwanji wosamumanga
wena osewo sadamangidwe pakuti padalibe odandaula
Amalawi tili ndi vuto lalikuru,kapena ndinene kuti tili ndi nthenda ya wumbuli,kubanyimbo kumakhala kuti mwini wake sanagulitsepo ikanali hot,koma munthu watenga nyimbo yoti inayimbidwa chaka cha 200
mkumati anaba??zichikhala choncho bwezi anthu monga celine dion,judy boucher,joan amartrading,whightney hoston,maria cary,sidy rank,lucky dube,lucian arlic kungotchura wochepa bwezi ali kundende wonsewa chifukwa anayimbapo zaenaso asaaa malawi wake up!!!
big up to dem,even matafale iz smiling wea eva he iz.chauta ngwa mphamvu pon ah replay KABOOM
Hahahahaha…moto kuti buuu…mumatha guys..ua so creative enough…big up…!
Sorry ya Justin Bieber aimba anthu ambiri ambiri, All of me Ya John Legend, Jah cure anaimbaso. Hello ya Adele, Alaine anaimbaso. Ndiye anthu akalephere kuimba nyimbo ya Matafale?
consent from a dead man
Achongolopiyo munthu kulemekeza matafale walakwanso koma ku malawi anzathu kunjaku angoyimba nyimbo za Bob mwale ali pheeee
Mwanena nokha kuti kunja nanga ku Malawi ndi kunja?
ife tili ku zambia tikamakhala timati kumalawi ndikunja
Kodi paja Malawi ndi kamudzi ka dziko liti?
Nepman alibe nyimbo yakeyake olo imodzi. Zose zakuba.i
Matafaleyonso nyimbo ya “timba” siyaketu anamatula
Ma brac ndio eni wache thefty of music
Palibe kuba….
Then MP Allan Ngumuya would also be arested for he has done the same track in his latest album
why arresting creativity?!
khani yake? zopuxa!
Nyimbo zinaimbidwa kale pano anthu angoimba zoimbidwaimbidwa
Kkkkkk atakasume ndi ndani?
Za ugalu basi
Sing your song of the late Evison because people like myself wants to remember him forever. And San B just did it. #EvisonMatafale the Legend.
And do it well not nyakanyaka zimene mmati mukuyimba reggae, koma zili mbola
zopusa basi kusowa zomangazotu apa
its jus jealous coz the song is hot
Mmmmmm..mesa ndi ma rexpect kd,,sausiru bax..nyimbo yaphedwa boh hvy
If you join Four corners Alliance Group and work very hard and the company does not pay you back, i promise to pay you tripple the amount you started with…….Join my team today!!!! Inbox
nsanje singamange mudzi ,
San B moto kuti buuuuu# Achina ‘ Ndili kuno konkuno’ awa akuti amandidziwa, awonso akuti amandiyaza kkkk ndili mmudzi momuno.Omukonda San B nayenso amakondedwa eyetu.
Awo akumaimba reggae ngati m’gandawo akhale# anakakhala madolo anakaimba iwowo.
Eishhh?
it was just as a riddim so they must not be imprisoned.Let us take example of Malinga ft sangie ,they did a song intitled i love u a song which was originaly done Mick minaj but they were not imprisoned . 4 me i dont c anything illegal on this scandle
Malawi 24? Which part of Malawi?
All musical protocolz must be observed otherwise nd izi
Hahahahahahah koma Malawian
omangao kusowa zochita basi nyimbo zake ziti ndipo kumeneko ndikuba ngati osamanga awa obenawa bwanji sopano kodi iye ndimaesa ngati ndichikumbutso kodi
Arrest busy signal 2
Hustle hard Ricas Snipson Chicas
hahaha ana ayamba kuba et?
Kkkkkk ndipo abrdz kusowa ma skill banx kut mwina mwake achuka
Hahahah ndikubasi zotchuka
Kkkkkkkkk eish abr
this thing use to happen and is not steaIing,Matse shouId v bein arrested Iong ago with mwapinduIanji,But jus because the song bIows every where its now a probIem ey
and billy kaunda sanayankhule kalikose
and awiri inuyo u dont even kn the relationship betwn martse and Billy,,,,mukudziwa bwanji pali ka relationship kena kake,,kutheka amacheza and mwina anapempha chiloleza,,how do u kn that ,? Chilungamo chiziyenda ngati madzi, even achina busy signal mutati mufufuze samangotenga nyimbo kwa anthu opanda chilolezo,, ya 1930 or 2015 amatenga consent,,ma rights kwa eni ake, kaya anamwalira kayaa anatani akuyenera kupeza achibale apemphe ,,agwirizane kuti zikhala bwanji whether pakhale ma payement or wat so ever,,,musayiwale matafale anasiya mtsikana ,,come rain come shine akuyenera kudyera thukuta la abambo ake kudzera mu mnyimbo za abambo ake ngati yomwe anatenga achina San B’yo,,!!.,,malamulo amachita kunena pa nkhani ngati zimenezi,,,its a pity anthu ozindikira ngati achina San B kumapanga izi yet akudziwa bwino zoyenera kuchitaa,,,,choncho now that the song is a hit fanz ikayankhula kumati ikupanga nawo jelous,,whch is nt the case.
How do you know that Son did not ask for permission
Kkkkk gud question, joseph
Iet us wait to hear from the other side,but it do seem as a big deaI akungofuna kudyapo,chipapapa anamenya achina Nep man,Tygrin wamenyanso nothing happen,Anie matumbi anamenya timakhaIa ku Bt from amakhaIa ku bt nothing big happened too,so I wonder y utake it so srs
Ingokambiranani,komanso ubwande umeneu udzakutherani omangopakula nyimbo zaweni popanda kuwadziwitsa eni?
Kumangomanga zlizonse
You didnt that?
Busy Signal Could Have Had Been Arrested Forever
Pokhapa nde wayankhula koz nyimbo zepeka yekha zambiri alibe koma zongo tenga za anthu ena
Amapempha chilolezo kaye kuti atero,,ndiponso amalipirana….
kodi simudziwa kuti amapempha permission nkulipira??? kuimba nyimbo ya nzako opanda permission ndi mulandu
inuyo mnazitenga kut zot busy amalipila busy amenyaxo ina ya john anayimba yemi wakunaiger bwanji xanamangidwe
l thot anagwiliza ndi akubanja kwa Evason Thafa
nde achedwatu!monsemuja kukamang’ala lero
I like the song anyway
Me too boy
Felix Chikhwaya imbatu ndimve kkkjj
Ndikuimbila mawa ndipemphe kwa San B kaye azangonama kuti ndamubela nyimbo kkkkk
aaaa ndekuxooowatu zomangirana apa!
aaaah I thought all of us knew that..and they were jus respecting the lengendary matafaleyo..
They must go prison that’s àñ offence of pirates
hustle hard!!!!!!
They must go prison that’s àñ offence of pirates
Kaya Anaba Kaya Sanabe, Nyimbo ija anamazaa,imabheba kuposa mwinawakeyo.