Ndirande boys Nepman and San B accused of stealing

Advertisement
San B, Nepman, Young K

The hit-song Chauta ndi wamphamvu that was originally performed by Evison Matafale but has gained prominence after a redo by San B who has involved Nepman and Young K will land the three in trouble.

San B, Nepman, Young K
Three thieves conniving

Media reports have quoted Matafale’s half-brother, Toza, as faulting the two for not having sought prior permission before redoing the song.

Malawi24 understands that Toza has since taken up the issue with the Copyright Society of Malawi (COSOMA) and Musicians Union of Malawi (MUM) to discipline the two.

San B has been known to redo songs of other people with Saleta Phiri and Paul Banda being some of the people he has used their music before.

Nepman was once accused of stealing a song he was featured in Chilawe changachi. The owner of the song complained that Nepman was performing the song in stage appearances as his own.

It is not yet known if the Matafale family is considering taking a legal action against the two.

Advertisement

365 Comments

 1. ifeso tikufila yomweyo pa theba pano mix manyawa mafilu okhaokha akuna nkinga dont arrest them ang’eke probrem malawi musamvele anthu achamba mwatani kodi amalawi nonse mukudya chamba kodi?

 2. its all about messege…..mesa chauta ndiwamphavu….. MATAFALE SANA IMBIRE AZIBALE AKE OKHA ….KOMANSO NTUNDU WA AMALAWI…..NDE AZIBALEO ATHA KUKHALASO KUTI SI MA RASTA NGATI EVISON…#Bless

 3. sindikuona chimene alakwitsa,km poti lidangozolowera kudana ndi anthu a luso,mwina akufuna awaphe ngati mmene adaphera Matafale,amuyaya mukhale inu, km ife nyimbozo adatiimbira bwino ndipo timazikonda.

 4. sindikuona chimene alakwitsa,km poti lidangozolowera kudana ndi anthu a luso,mwina akufuna awaphe ngati mmene adaphera Matafale,amuyaya mukhale inu, km ife nyimbozo adatiimbira bwino ndipo timazikonda.

 5. how many times were you listening to that matafale’s chauta ngwamphavu and how manytimes are you listening to the same track only that it was redone??? ngat chauta siwamphavu then San b ndi azakewa ndiolakwadi. otherwise nothing wrong here. majelous Basi kut thoo!! munakhala bwanji?????????

 6. Kubeledwa nkowawa guys mukongonena poti sanabere inu komaso mkuti anayiyimba bwino ashina Sun B anasithapo chani iwowo zachamba basi amangeni

 7. Hey my people please work up!! Its a matter of memory to the owner, thats all. Ndiye mupite ku Zambia mukamange Dalisoul first coz mayamba zachamba tsopano. Umbuli kapena Jerous??

 8. But y ma complants nkhani ya zii ngati imeneyi dont u kno theres so many musician amene amaimba nyimbo zoti zinaimbidwa kale without zinkhani koma inu mmmh; its fyn i kno de story jealous thoooo osanyadira kuti its rememberance

 9. uku nde timati kumpusa kusowa chochita okuba onsewa mmalo mowagwila mufuna kumanga mu2 ot akupanga zake kupusa open up your eyes maso pasogolo #san_b_nep_man_young_k like david say #OSAOPA

 10. Dziko Lamalawi guys ndilolephera limalimbana ndi zinthu za simple akulimbana ndi anthu oti angoimba sanatukwane koma kulimbana nawo ayiwala kut dziko la2li iri pa moto wazaoneni ndikuvutika ndiumphawi kamba ka ndalama zomwe zidabedwa ku capitalo zija sono mmalo mosova mavuto amenewo mukulimbanana ndi zinthu zoti sizingapindulire ziko why my country malawi bd wise pochita zinthu taonan amalawi tili pa moto wazaneni kamba kandalama zomwe zidabedwa zomwe zikadathandiza malawi kukhala pa map koma kuli zii anthu olemera kale ndi amene akusangalala choncho musathamangire zasopanozi kamba koti ndi zophhweka ai muthane kae ndi cashgate then go through with oyimbawa. tipange malawi wabwino wolemera ngati maiko anzathu osati kulimbana ndi zinthu zomwe sizingakweze malawi

 11. mbuli mukukomenta zanzi pano kusumilana kumatengelano amene akuva kupwetekayo ndiye ngati Toza Matafale akuona kuti ndichosakhala bwino wina kuimbaso nyimbo iliyose yam’bale wake akuyeneladi kupita pakhoti matafale ndani sadziwa kuti adafa ngati nkhuku? ndipo kuonjeza apa iye mwini adaimba kale ma albam awiri yomwe adatulutsindwa ndikugulitsindwa ndiye ndichanzeru chanji kuti mbuli ina ikatenge nyimbo yamatafale ndikumaimbaso? nyimbo zamatafale zilipobe ndipo akuzigulitsabe m’ma shop ambiri kulibwanji kugula nyimboyo yake matafale ndikumaivela sitingamukumbukile pamenepo komaso timakhala ndi 28 Nov nditsikuso lomwe timamukumbukilaso ndipo sindikuonapo chifukwa choti adaimba nyimboyi ndicholinga chokumbukila matafale no! San B ndichizolowezi chobweleza kuimba nyimbo zayeni:

  .Moda
  .Anjiru
  .Toza
  .Chizondi
  .Hazwel
  .Yanjanan
  .Chokani’s Family
  Musamutaye Toza pangani chimodzi mpaka aone polekela pajasa mukuti san b adabona kagulu kamene kamakana kuyenda ndi mablacks ati amasuta chamba ndiye mukuimba nyimbo zawo?

 12. guyz muimbenso poison so sweet mwamva????? mukutha mukutha kuimba ndipo ngati apite ku Court musakalipire ….ku malawi music inalowa pansi kwachuluka ku burner

 13. If you sing a spiritual song. You are preaching the Word of God, The song belongs to God and you spread it to many souls, so if people sing the same song it means they have received your preaching, that’s your goal of singing. If Matafale sang this song to win souls and praise God, then he is happy people singing these songs, unlike you focussing on money as your god. Well done Son B and Fellows. Behold the Temple curtain was torn during the death of Jesus on the Cross. Just see the hidden now. Who triggers your speech in your heart?

 14. if u eva imprizoned mo than 5 pple due de issue lyk dis,u can do accordngly 2 thse dear brthers BUT!,if not i should not hear dat u h’ve jailed thse men,,,,but if u delay i wll narrat 2 mr Shphrd Bushri 2 do smethng upon them to aim at rescuing thm and cursing u!!!! i min those who r follwng ths stry 4 these nicknamed guyz Sun B, Young K & Nepman, MafewDefiah!!! az Shadrk, Misheck and Abrnegoh respectvly, Keep It Up Guyz Never Gve Up!!,, Those Frogs shd not bother u az wel az me,,,,,,o de best u tri-guz

 15. iiiiiii amalawi tatopa kumunena prophet pano mwaganiza kuyatsamula miromo yanu kwaoyimba? hahahahaha matafale RIP koma mkazisatira kwambiri nyimbo zomwe amaimba ma missionaries wo nawoso ndiakuba amaba ma meto a malemu joseph hill zonse nyimbo zawo kwamene amasatira nyimbo za raggea plz ingowatayani akuba azanuwo?

 16. Kodi mukamat amalawi amalawi chimakhala chili chan ?? Mukuganiza kuti mitu ya tonsefe imapeleka nawo mfundo zokhuza zimene mumawelengaz ?? Mumawaziwa amene amapanga post zoterowo so why nat pointing ya fingure straight to them ?? Mumaopa eti ?? Ndie mumaona kut its beter to put the blame on Malawians ?? If you blaming Malawians then then who you ?? Instead of commenting accusative comments here be the first commenting on how to change.. pointing anyone will never change anything … Everyone has his own opinion and to them its facts … So respect every opinion and overcome it by telling wise nat dissin …. Gud day

 17. nyimboyi ndinaiwala koma mmene yayimbibwamuso shaaaaa ine kunva kukoma kundikumbusa zana,koma guys mumatha tayimbaninso ina.

 18. Malawi don’t judge these three brothers bcz i don’t want you Malawi to regret after judging these three brothers, San B is a well known artist since long time ago and he had been sharing the stage with Matafale before San B became a born again, and now San B is showing up a good memorial to the late artist Matafale, so i don’t see any reason to send them in prison. Hi San B and ur brothers imani njiiii pachoonadichi Mulungu akumenyelani nkhondoyi, and i wanna give you new names for it and these are Daniel, Misheck and Abilinego, opikisana nanu he/she will get what he/she deserves. Thanks.

 19. that is a remix, amalawi kupusa palibe mulandu apa.Look at American music industry alot of remixes, they do remix the song which is a hit and still fresh on the market, nde nyimbo mukunenanoyo ndiyakalekale and they just trying to revive it,we already know that it was done by Matafale.

 20. mmmmm guies..sometyms musamangolemba ma dry copies munakavaya kwafanzyo mkukafunsa bhobho…ur story is lacking relevance, truthfulness, balance and fairness…. plz consider ourselves guies

 21. Kutha kwa nzeru zopekera nyimbo za newone ndizimene zavuta

 22. koma mwafatsa just jealous y uleave bushiri and arrest innocent pipo goverment of Malawi ur out of mind nonsense serous asiyen kod njala ? zaziiii asiyen athu

 23. aToza aona kut zalephera afuna amudyere San B,, heeeee “Omukonda San B amamukonda mbali ya kwanu ndili kuno konkuno ine aaaaa ndili kuno kunokooooo”

 24. enawo azingoyimba nyimbo zam’gandazo aziti R musik…ngat mukulephera kuimba zolongosoka mungakwanitsa re-do zamatafale evison?…San B wakuposan zanu zomwe mwayamba nsanje..kkk

 25. Musicians plz learn to respect your friend’s talent I never say it is wrong to redo your friend’s songs but first of all follow right procedure before you come upwith the track , if you do so I think both parties will enjoy your talent

 26. Kaya man……koma adayiimba booo2 madolo atatuwa

 27. Tupt zanu amalawi ndife otani what kid of pple we walawians ee bas mumangofuna munthu avutike mukatero muzimuseka fulshe!! Majeras bas akamakhala amakonda majerous sianzathu awa maheters ndipa machine thothothoo akudana weee mbuu!! ndashuta;):p;( 😎

 28. Hahahaha! They Have reminded me someone who said,” if that one did it,those ones did it why can’t we did it?” Awowo awo maluzi awapweteka ndiye akufuna achina SAN B mungo wachula kenakake.

 29. Mukuyankhula zambiri chifukwa San B wayimba bwino?let’s talk developmental issues koma izi sizitithandiza ayi!Ask God to give you a talent like that of San B,San B salimbana ndi munthu ayi zipatseni ulemu

 30. Malawi sazathekanso basi. Achina Toza zangowavuta basi asowa yajada km sapanga choncho ndife amodzi. Nanu a COSOMA ndi a MUM timadziwa kale kt ndnu wadyera teleku pamenepa mwapeza cocita. Inu mene nyimbo #wamphamvu remix inatulukira bwino zakunyasadi ine ndkuziwa kt or mwina wa Evison mzimu wake wanasangalala kwambiri. Malawi sitingapite paxogolo khalidwe lomweli.

 31. Sivuto mpaka kuwamanga but akanapempha permission kwa matafale family that so .achita bwino tisamayiwale matafale in other style

 32. Amalawi munatan kaduka malo momanga obena mikumanga oimba malo momanga bushiri kut ndalama wazitanga kut malo mumuotan joice azayankhe milandu amasulen anthu osalakwa

 33. Kapena amafuna aziyimba munthu yekha nyimbo yikakhala ya mtundu wakwawo okha ngati mene anachitila. Song Title Bwenzi Langa late Robert Fumulani anayimba kenaka late Gift Fumulani kuyimbanso ndizimene mukufuna zimenezi

 34. Bwelan muone KU botswana ambili anaimba za eni ake koma no vuto NDE madolo aimba bwino mubwela kumati aba za ziii pezani zina zonena kip it up SAN B,NEPMAN+YOUNGK

 35. Patha nthawi yaitalibwanji kut azindikire zaozo? Sbwnoyi nthawi yonseyi sankazimva nyimbozo? Aaa! No! Samamuona mzao waku jamaica Busy signal? Popeza nayenso amaimba zamzake koma alibe nthawi yomusaka chifukwa amakhalazoti akukwezanso lusolija.chifukwa tikati tione nyimbo yaatatuwotu mwiniwache anaidyelelakale.

 36. Kkkkkkkkkkkkkk ha ha ha ha ha ha ha ha ha ha eheeeeeeee mwasowa chochita eti???? Mvetselani tsono, mukamangenso a boma for implementing one village one product (OVOP) chifukwa it was not their idea. It was Brown Mpinganjira’s idea but the govnt store and implemented it. Yet when Mpinganjira complained munamuyankha kuti IDEAS HAVE NO COPYRIGHT OWNERSHIP. Mxiiiiiiiiiiiiiw mwangofuna kuwabera anthuwo mwina mukuonangati alindindalama. Mumaleka kungowapempha mwachilungamo bwanji????? Foolish.

 37. Lack Of Apreciation Wen One Has Done A Gd Ting Honestly To Say It The Track Is Dope,,,# Hahahahahahahahaha Amalawi# Palibe Pulobulemu Apa*** Am Lovin Tha Song,..

 38. ayambekaya amanga chimwemwe muhango ndi nyimboza Rabecca malope ngati wankulu akuba nanga anafe inenso ndiimba zopusa

 39. MY NYASALAND MALAWI:Munthu akalemela ndi wa satanic, akasauka ndi wa ulesi,akakhala osakwatira ndi hule,akakhala lova ndi wakuba, akakhonza mayeso amawonera, Chipani chikawina chabela, Ugule chigayo wakhwima SAN B. DIS Z NYASALAND MALAWI,,ZOVU ZEDI ODALA KUZIVETSAA!!!

 40. waiyambisa nkhaniwe ukufuna kutukwanidwa?peza nkhan yolemba cz nyimboy ndye yaphikika than mwini wake ma3lu defiyaaaah!!!!

 41. Gyz tien a Malawi tikondane, Ndiangat aimba nyimbo zobwereza kumalawi? Ndipo ndindan anaimbidwapo mlandu? Nyimbo bax pot anthu atchuka nayo wina apezelepo kanganyasee mpakana! Well done San B, Nepman and Young k mumatiimilira inuyo 2019 wina aimire pampando wa president,wina MP, wina khansala 2019 BOMA!!

 42. Matse Anaymba Ya Billy Kaunda_mwapindulanj Nanga Munawona Billy Kaunda Akudandaula? Ths Is What We Call Remix, Mumafuna Nepman, San B Nd Young K Aymbe Ya Gwalad Tumbocid Ndy Smukanawamanga??

 43. Palibepo za prison apa. Bwanji Kodi? Aaaaaaaa! Kharani ngati anthu ozindikira.

 44. Kungoti tinene zoona anyamatawa chinyimbochi achikwapula mpakedi anthu kuchita majerous koma cmungapundule kanthu iotu alibe probulemu koma inu ma3lu nepiyaaaa

 45. That song z jxt amazing n most of us we lyk t. They z no any prob on wat sun b dd lets us jxt enjoy the products of late evason matafale.

 46. Nw I bliv in young kay (CMPHANVU ZANGA NDICHISOMO CHAKE,NDIOPASO CHAN WAIKAPO NKONO WAKE,DZIKO LITIWELUZA TKAMENYA NKHONDO YAKE) Here its in ua accusin them jct cox thy av spread the gospel news MAY U ALL LOT IN HELL

 47. Kusowa zomanga chani? Maunyolo achuluka kapena? Mmakanika kumanga an2 akupha ma alubino akuphedwa mkuona mkumat mmange an2 osalakwawa atani?oimba zauzimuwa amatengela an2 akujon kumatembenuza nyimbo zaweni wake osawakwizinga bwanj?

 48. Chris martin:let her go,Busy signal:Gambler,one more night,personally,mwati mumulonde Nepia ndi Kaphuka komanso Burnett?agalu inu osapanga zanu bwa?Mwina ndinu nomwe munamupatsa Joseph Tembo minyama eiti?mxxxxxiiiiiewwww!

 49. alani ngumuya naye ndiwakuba …if so…..example bizy signal nyimbo zija amakatenga permission kkkkkkk poor pple from warm hrt

 50. mwadongosolo lake achina Son B akadayamba akumana ndi akubanja la Matafare atsanaimbe nyimboyo,,koma ngati sanatero ayenera kulandra chilango coz kumeneko nkuba sangapange ndalama pantchito yomwe idagwiridwa ndi wina….olo oimba akunja amene amaimba nyimbo zaena sikuti amangoimba ai,amakhala kut apasdwa chilolezo kuchoka kwa mwini kaya abale amwni nyimbozo…..copyright ndyolesedwa kulikonse

  1. futso langa kwa inu amwene kod malinga anayimba ilov you ya nick komaxo busy amenyaxo john ya yemi kod athuwa anapepha chilorezo ngat sanapephe nde san b ndi azake siolakwa

  2. Nyimbo ya munthu siingaimbidwe popanda chilolezo chamwini wake..kumeneko ndikuba ndip nzolesedwa nchifukwas chake kuli copyright society

  3. A moses chipote inu kodi a copyright anuwo azidikila nyimbo ikatchuka chomchi kapena akanailesa isanatulule bwa ..jealous yanu sikupindulilani enawaso angoyangana malemu awo abele kanyimbo kake kti atchuke

  4. Moses Chipote inu ndi athu amodzi ajealous, kodi nyimbo inatuluka liti? Nanga akupanga clam anali kuti monsemuja? Vuto la amalawi mumakoka nkhani yopanda pake

  5. But to say the fact here: The song was composed by someone( Evison Matafale)..these guys have just come up with the re-do …honestry San B had to take a step and consult The black missionaries band ( the band that was started by Matafale himself), and ask for a go-ahead. And am very sure these guys could not have said No! but the fact that they didn’t go for permission it like ” akuwadelera” anzaowa..which is very bad…..bolanso anayimba achina Anjiru eni ake ikanakhala nkhani ina…Komanso anthu ake ndi ife tomwe omwe tikanati tiziwanyoza anyamatawa kuti ” nyimbo zawathera, ayamba kumangobwereza zakale “….koma wina akaziyimba nyimbozi ndiye tiziti there is no problem?…No! ..there is a problem and that is ” Kusapempha chilolezoko “

 51. acina busy signal,jah cure,romain uvirgo ndiena ku jamaica amaimba nymbo xaamxao kma samangdwa nde ixi nde xitixo d@s primitivnes

 52. mukulephera kumanga ndikumalizisa milandu ya cashgate yoti inachitikadi & ziko lili mmadzi kaamba ka kubedwa kwa ndalamazi nde zoona mufuna mumange ma dolo woti angoimba? nde muyendenso mma church mukamatipeza tikuimba nyimbo za ena mutimange tonse!

 53. Apa ndiye zafika pa boza komaso kaduka,, kodi nyimbo imeneyi yatuluka liti?? nthawi yoseyi analikuti?? ndindani samaziwa kuti nyimboyi ndi yamatafale,?? Matumbi, Ndirande Anglican, Loyd Phiri, Mau K, A Chirwa, Joseph Chadeleka, onse a HipPop bwanji sakuwamanga??? komaso inu olemba news inu bwanji samakumangani??? kodi zayamba liti zimenezi??

 54. Oyamba kumangidwa akanakhala Michael Bolton yemwe anaimba nyimbo yot ‘Lean on me’ yomwe inaimbidwa poyamba ndi Bill Withers.sindkuona chifukwa chowamangira mamembawa,nsanje 2 much malawi eeesh

 55. Za zii inunso mmasowa nkhani eit simunawone even mayiko amzanthu ena nyimbo anayimba kale ena mkuyiyimbanso version ina za zii umbuli basi ndi umphawi zomwe mmantha

 56. I agree with this ,they stole that song ,same like dalisoul that song for chaphuka,come to sun B just accept that u that song was sang by matafale

 57. nanga ena anayimba nyimbo za allan namoko bwanji samangwida..ena anaimba zot “anapta ndinyanga zomwe kumanda, ena.. Achimwene muli bwanj.” bwanj sakumangidwa?? Zamkutu!

 58. I don’t see any problems of these guys Nepman & San B for there song…. problem is jerous Malawian people busy with other #Business wake up guyz and let others people’s do thy #Mission….Remember god separate us for reason

 59. Ha ha ha ha Chilungamo Madolowaaa chinyimboochii anachiswaaaa and nyimboo zambili tikumavinazii nzobwerezabwereza. what mattters nkubvesesana basii nkhanii palibeee apaaaa

 60. As far as proper channels were followed , no case here because artists are supposed to get permission from someone. We have to know that composing a song is not a joke. This is talent and has to be respected and protected. Had it been that matafale is alive, this could have not happen or these two could have asked permission from the late great king of reggea music.

 61. I love the song and I love Evison matafale and I don’t see anything wrong with San b, young k and nepman for redoing it, it’s a reminder that matafale was and is the best of all time so thanks to the three brothers that redid the song

 62. All over the world they redeem songs if it is nice .And they can sing it even more than 6 musician .But my country Malawi, eeeh! is a crime . Remember there is too much churches but God is one and two much songs but one musician. Coz now people are just repeating what other musicians already sang about

 63. Umeneu ndie ucitsiru wa waukulu agalu inu a News kaya 20_chani…. Bwanji mukuwayipitsa amzanu mbiri coz aliyenxe amadziwa kti chorux ija ndi ya #Matafale en da whole Malawian we owez respect him coz he oz a legend 4us plz plz plz thnkn twice b4 yo post yo sensles poxt lyk diz…. Mumafuna ayimbi nyimbo ya munthu wakunja kapena cani amphaka inu.. Nyimbo idatuluka last year en y y y y mukuyibwelesa nkhaniyi tym ino bwanji…?

 64. Malawi malawi malawi kkkkk ayi ndinthu land of peace bt ful of jerous mwatopa ndikumunena bushili kuti ndiwasatanic you wll remain like that guyz work up open yo eyes and see

 65. Malawi malawi malawi kkkkk ayi ndinthu land of peace bt ful of jerous mwatopa ndikumunena bushili kuti ndiwasatanic you wll remain like that guyz work up open yo eyes and see

 66. Busydii nde bwenzi atangolandira ‘life in jail’ basi coz of “Gambre” ya Kenny Rodgers, not 4getn the jst “sorry” by JB….kk! Nkhani ndkunvanaa btwn the one who is willing to re do the track ndmwini wake, but in ths matter a Nepman nd a San B amayenera ku chiller ndi achna Anjiru basi..(Matafale’s family)

  1. They ask for permission to re do the song ngakhale a UB 40 akhala akuimba nyimbo za Eric Donaldson,if u remember very well Joseph Tembo anaimba nyimbo yaoimba waku Botswana and inailetse on the air waves

  2. @BRIAN “They” u mean Nep and San? Mundiumboni wot they askd 4 permision man? Okie nde a UB40 nymbo zawo zmakomera muja amamenyanso ya redoing….aaaa zandkhudzaaa hvy! Hope nt o tracks?

  3. enawo azingoyimba nyimbo zam’gandazo aziti R musik…ngat mukulephera kuimba zolongosoka mungakwanitsa re-do zamatafale evison?…San B wakuposan zanu zomwe mwayamba nsanje…kkk

 67. Chalakwika kweni-kweni n’chiyani? Ngati pena pake palakwika,chonde kambiranani mwaulemu ndi mwamtendere,musachotserane ulemu.Komanso dziwani kuti nyimboyi ndi yauzimu,yachilimbikitso ndipo yotikumbutsa a Malawi tonse za ntchito zake zabwino komanso za imfa yake yomvetsa chisoni ndi yosaiwalika.Mzimu wake uwutse mumtendere!

 68. come on Malawi! tili ndi anthu ambiri amaba luso anzawo ena amaiko akunja ena akwathu konkuno komaa bwanji samamangidwa, to be honesty mwina anyamatawa anapanga pofuna kuti tizimkumbukira Matafale, mukuganiza kuti Nepman sangathe kupanga produce nyimbo please Malawi wake up

 69. Eminem did “What is love”
  Brandy did the same with “Think twice” the Fuck are you going to arrest them for?

 70. Mukadzaona oimba akuimba nyimbo za munthu wina just that,kupeka musik kukumuvuta.Other ways promoting Matafale’s legancy

 71. Iiiiiiiiii zachikale,lean from jamaicanz this kind ov copy someone s song in different styles dey call t ridim.
  Tink ov these songs dea in Jamaica
  -brighter days ridim
  -think twice ridim
  -down by the river ridim
  -sorry is a sorry word ridim
  -night nurse ridim
  -ragae music again ridim
  -mama ridim
  -cheaters prayer ridim
  Just mention a few,nyimbo izi zinaimbidwa ndi oyimba asiyanasiyana ndipo ambiri koma sitinamvepo kuti wina wamangidwa kapena amangisana,ndipo nyimbozi zimachita kukoma ukamamvera.nde muli busy kumangisana nkhani yake iti? mmmm olo omangayo alibe manyazi ,I think nkhani ya njara yankhuzanso ku muzik industry .I .P MATAFALE nuf respect

 72. If those cacoons does’nt know how to compose songs they shud contnu smokn chamba so that they remain ugly, if i respect Evi its bcoz of dat song, lamulo ligwile ntchito.

 73. Anthuwa yakula ndi jelasi basi sakufuna kuti tizikumbukila malemu aluso king of raggie Evison matafale kudzela mwa anthu omwe amkakonda ndipo akamakhala amatulusa misozi okha pokumbukila luso la oyimba wamkulu kamba ka ichi pofuna kupukuta misozi amangoyimba nyimbo zake kuti amweleko madzi. ndiye apapalibe chifukwa chomangilana mwatani kodi?bwanji simukulimbana ndiwokupha ma lubinowa?

 74. these are issues to do with copyright zimene ku malawi kuno sitizitsata kwenikweni…redoing a song is not a problem but first permission from matafale’s family could have been sort…..people’s commets tend to take a blind eye on this no wonder grace chinga’s album was pirated….then mumva kuti wina wayimba ya grace album isanatuluke……..lets follow the rules and move on

 75. Aaaa why accused? its a gospel tune in both tracks of him n matafale komanso is a way of remembering him.Amalawi kodi mwatani?

 76. Nanu musamakokomeze zilizonse nkhani ya nyimbo mpaka prison nde kwakhwekatu.wayimenyabe bwino ine pano ndikumvesela yomweyo

 77. Ndikuyambila iwe walembawe manyende ako ndipo mwini nkhani mavuzi ako olandila nkhani mbolo yako nawe ogemulawe pamtumbo pako {Nep man San B and Young K}kutimvetsa kukoma kuti wawawa nep man mafilu defiya (never arest you guys) kam’mangeni Dalisoul first zachamba etii

 78. Ngati zili chomcho mangani mr malawi ,Aunt gettu ndi wina oyankhula ngati bakili uja koz awaso akudyela luso la ena….san b ndi no 1mo fire

 79. that song rekindled my memory Evie.the burning sensation and realisation that Evie sung gospel well than these other crap calling themselves gospel artists

  1. Ndichilise anayamba kuiba lucius banda song originally done by alpha blondy(heal me) lucius copied it word by word but in chichewa

 80. Amalawi tili ndi vuto lalikuru,kapena ndinene kuti tili ndi nthenda ya wumbuli,kubanyimbo kumakhala kuti mwini wake sanagulitsepo ikanali hot,koma munthu watenga nyimbo yoti inayimbidwa chaka cha 200
  mkumati anaba??zichikhala choncho bwezi anthu monga celine dion,judy boucher,joan amartrading,whightney hoston,maria cary,sidy rank,lucky dube,lucian arlic kungotchura wochepa bwezi ali kundende wonsewa chifukwa anayimbapo zaenaso asaaa malawi wake up!!!

 81. Sorry ya Justin Bieber aimba anthu ambiri ambiri, All of me Ya John Legend, Jah cure anaimbaso. Hello ya Adele, Alaine anaimbaso. Ndiye anthu akalephere kuimba nyimbo ya Matafale?

 82. Achongolopiyo munthu kulemekeza matafale walakwanso koma ku malawi anzathu kunjaku angoyimba nyimbo za Bob mwale ali pheeee

 83. Sing your song of the late Evison because people like myself wants to remember him forever. And San B just did it. #EvisonMatafale the Legend.

 84. If you join Four corners Alliance Group and work very hard and the company does not pay you back, i promise to pay you tripple the amount you started with…….Join my team today!!!! Inbox

 85. San B moto kuti buuuuu# Achina ‘ Ndili kuno konkuno’ awa akuti amandidziwa, awonso akuti amandiyaza kkkk ndili mmudzi momuno.Omukonda San B nayenso amakondedwa eyetu.
  Awo akumaimba reggae ngati m’gandawo akhale# anakakhala madolo anakaimba iwowo.

 86. it was just as a riddim so they must not be imprisoned.Let us take example of Malinga ft sangie ,they did a song intitled i love u a song which was originaly done Mick minaj but they were not imprisoned . 4 me i dont c anything illegal on this scandle

 87. omangao kusowa zochita basi nyimbo zake ziti ndipo kumeneko ndikuba ngati osamanga awa obenawa bwanji sopano kodi iye ndimaesa ngati ndichikumbutso kodi

 88. this thing use to happen and is not steaIing,Matse shouId v bein arrested Iong ago with mwapinduIanji,But jus because the song bIows every where its now a probIem ey

  1. and awiri inuyo u dont even kn the relationship betwn martse and Billy,,,,mukudziwa bwanji pali ka relationship kena kake,,kutheka amacheza and mwina anapempha chiloleza,,how do u kn that ,? Chilungamo chiziyenda ngati madzi, even achina busy signal mutati mufufuze samangotenga nyimbo kwa anthu opanda chilolezo,, ya 1930 or 2015 amatenga consent,,ma rights kwa eni ake, kaya anamwalira kayaa anatani akuyenera kupeza achibale apemphe ,,agwirizane kuti zikhala bwanji whether pakhale ma payement or wat so ever,,,musayiwale matafale anasiya mtsikana ,,come rain come shine akuyenera kudyera thukuta la abambo ake kudzera mu mnyimbo za abambo ake ngati yomwe anatenga achina San B’yo,,!!.,,malamulo amachita kunena pa nkhani ngati zimenezi,,,its a pity anthu ozindikira ngati achina San B kumapanga izi yet akudziwa bwino zoyenera kuchitaa,,,,choncho now that the song is a hit fanz ikayankhula kumati ikupanga nawo jelous,,whch is nt the case.

  2. Iet us wait to hear from the other side,but it do seem as a big deaI akungofuna kudyapo,chipapapa anamenya achina Nep man,Tygrin wamenyanso nothing happen,Anie matumbi anamenya timakhaIa ku Bt from amakhaIa ku bt nothing big happened too,so I wonder y utake it so srs

Comments are closed.