The Ntchisi First Grade Magistrate Court has sentenced a 21 year-old man to five years imprisonment with hard labour for breaking into a shop and stealing items.
According to police prosecutor for Ntchisi Fred Luhanga, the convict, Joseph James, stole 24 tablets of Azam soap and 5 packets of Soya pieces all valued at K2, 600 from a shop belonging to Maliseni Simoni.
The convict pleaded guilty to the charge of breaking into a building and committing a felony therein which is contrary to section 311 of the penal code.
Passing her judgement, First Grade Magistrate Dorothy Kalua said the offence is serious, hence the offender deserve a stiff sentence to send a warning to who would be offenders.
James hails from Mguza village in the area of Traditional Authority Nthondo in Ntchisi District.
In a similar case, the court in Ntchisi has sentenced Thomas Banda, 23, to four years imprisonment with hard labour for stealing a bicycle.
koma opezeka nd mafupa a albino 15 months ! fuck the judges.
anthuni ndimati ndifuseko kodi zaka 5 apasidwa okubayo zipundulira ndani,obeledwayo kapena boma,majaji athu muzikhala ndi masomphenya achikondi poweluza,wakubayo ndi wobeledwayo onse ndi ana a amalawi azanu.
kodi akumagamula atamwa kachaso eti?
Madam magistrare, did i hear you well saying this offence is a serious one? and you mean it? do you remember that gentleman amene anagwirilira mwana wake ku Balaka, was that not a serious offence? how many year did you guys slapped with him? Mudzalangidwatu anthu amalamulonu
Amphawi tili mmadzi ndalama il pasogolo chilungamo chinatha
Mai Senzani anaba millions kuwapatsa 3 yrs kodi zija za community service 4 milandu ing’ono ing’ono osapangako adopt bwanj our prisons are orede crowded

sha! koma magistrate uyu ndiye akugawa zaka…
Why opezeka ndi Albino bones 15 months in prison?
Soya pieces ndi ziwalo zamunthu. Mlandu oopsa ndi uti?
Kodi ma secton amilanduwa akukhala bwanji?
Mukugamulira kukhumbana bwanji?
5yrs for soya pieces
And…
9 months for attempting sell a human being
kkkkkkkk Malawi why!!¡?
what?
koma zoona…katundu osakwana 20 thousand mpaka 5 years…. #injustice at ts best….just not fair
Ma #Judge aku malawi amapeleka chigamulo mwa opposite. Ndamva kuti wina wake amafuna kugulitsa munthu pa mtengo wa #mk5_kwacha amulamula kukakhala ku ndende miyezi 9. Where by this little man waba #Soya basi zaka 5? Pliz! Dnt smoke #Chamba mukamapita ku #court.
iiiiii koma osaukafe tilibe ma loya ndithu
cashgate 1 Year. Soya Pieces 5 Years????? mmmm amphawi tunalakwanji?
Lets make a deal with a khoti. Inuyo mudzigamula milandu ingono ingono ngati imeneyi ifeyo tidzisova monga yogwiririra, kupha ndi ina yotere monga anachitira kuNsanje coz you have just demonstrated your stupidity on the way you are passing judgements. LOL
chonde amene mukumudziwa amene anaweluzayo mukangomuonetsako macomments 15 okha basi akaganizenso kawiri komaso ngati amapemphera asankhe 1 thing.
woba soya pieces 5 years,wogwiririra 5 years ,woba ndalama za boma ku capital Hill 0 years(walking away freely),,,,,,what kind of justice is this????
The paupers will ,at all times, be on the wrong side of a coin…..thats malawi i grow up with.
Munthu or atasowesa track yonse ndie kukampasa 5yrs in jail koma ma judge aku malawi kaya mukumapita ku ntchito mutamwa manip muzaona pole, busa wina anasowesa msikana uja ku mpasa zaka 2 wasoya peaces 5yrs zamisala basi.

Komatu majaji mwaonjeza kupondereza osauka. Simumva chisoni ai? Niwachingati ameneyu inu nokha? Aja mudawaweruzira mowapulumutsa atakufumbatitsani akwana angati? Inu ameneyo. Tilibe chonena dzilo lidakukomerani anzathu.
Mwaonjeza . Mupatseni munda alime soya beans basi .
Soya piece 5 years cashgaters 2years mxiiii
Munthu wofuna kugulitsa munthu kumupatsa miyezi yisanu, fun of sentences pa Malawi
SOYA pieces wake nde wa Golide eish nanga ndiyemweyu ????
Be Fair Enough Judges
Zachamba Nonse Aza Malamulo
Dziko ndilokondera kwambiri, milandu yaing’ono imakokedwa kwambiri while those who r involved cashgate scandle ali pheee kumadya pizza ndi bugger zoti anaba ndalama sizikusonyeza, chilungamu chagonekedwa tulo
judge idiot…mwini shop idiot.. apolice ma idiot.. nonse amene nkhani iyi ikukukhuzan ma idiot nokha nokha.. chimene ndanenela izi mukuziwa

Soya pieces,,5yrs,,,,cashgate oba ma million 6months with house arrest,,,,koma eeeeee.

akuti 5yrs with hard labour, soya pieces yemweyo zachamba eeetii ,osangompatsa community service bwanji…..kumphunzira kugamura mulandu!!!!!!!!
Kma2 majajinu mukalandila chilango kumwamba
opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

Injustice
Injustice
Achair, JB akuba mamillion awo akuyenda mwaufulu, wa soya pieces mpaka 5yrs

kkkkkkk koma amphawife tili pamavuto eti,mpaka 5 yrs? pamene wina anaba ma million kungompatsa 3 yrs?

kkkkkkk koma amphawife tili pamavuto
kkkkkkk koma amphawife tili pamavuto
But man suspected to have killed Njauju has been given bail. Thats malawi for u

Wakuba ndi wakuba
Wakuba ndi wakuba
Kuba phone or kuba chimanga ndi opusayi wa soya yi, these people azikhala 15yrs olo 20 anthu awa akuononga budget yadziko tikusungila un productive citizens. Akafele kundende koma wa cashgate azikhala 6mths kuti ndalamayo izizungulila

Okupha munthu 5yrs ,okuba mbuzi 5yrs , okuba 90 billion 10 yrs koma zoona zimenezi , all the judjes god must 4 give u

Albino abductors six months. Manyi anu ndithu

not fair at all
Masiku ano dziko likukomela olemela coz wina wapha alubino akuti akakhale miyezi 15 pamene wakuba soya pecies zaka 5 kodi moyo ndi soya chilichotsogola m’chani abale? koma tiyeni timusiyile yehova ndi amene adziwa kuweluza kwachulungamo.
Koma Malawi why kkkkkk
Soya pieces anali ochuluka bwanji. Truck yathunthu kapena bwanji. Koma wina wopezeka ndi mafupa a albino miyezi 15 yokha . Wasoya pieces five yrs koma zoseketsa ndithu. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kaya ma khoti amalawi sizizayenda mpaka kalekale
Tiwona kut Acashgate aja muzawapasa zaka zngat ndiposo izatha lit ?Anthu oyipa Inu!!!!!!
Charles msaku woimba,wanzeru kumalawi mlandu woba mamilion kumangopondeleza koma oba nkhuku womweu mpaka 5 years ,moti mukuona kuti apa pali chilungamo Osward lutepo mabilion osewa 11 years koma soya pieces ndi soap zokwana 2600 mpaka zaka zonsezo,pepani majudge zinazi osamangoti ena atengelepo mphunzilo mukulakwa.
Sizinandisangalase ameneyu amafunika anyongedwe bas
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.
MALAWI walero
MCP will pardon all these
Thats too much
Jailhouse iz full ov innocent & poor people,
Shame on u
Iknw ndende munapangra amphawi
fodya ameneo
Zopusa mutuluseni ndizalipila zomwe waba
Fuck magistrate court,people are stealing billions but u put them into bail,why giving this man five years for the money less than k3,000,please release him and just teach him
wasoya pieces 5 yrs,wopha alubino 3 yrs,,eishh
Osauka alibe mawu. zomvetsa chisoni kwambiri
malawi 4sale!!
This country is belong to rich people crc
Y tayamban #JoyceBanda dzakadzake den enawa kumawapatsa bwino dat unfair judgement…5yrs sukudziwa kt kuli njala iwe opusa kwambili ndikukamba ndi judgewe
Judge amene wagamula mlandu umenewo ndi kape wa cashgate 3yrs wokuba soya pieces 5yrs shame
becareful for ur judgement. also uwill be judged according to what urdoing
Olo ukanamupatsa 20years usawone ngat akupatsa VX
Mwana wa anzanu 5years ;(;(;( uzimu mulibe mwa iwe oweluza

Nkhan yopepela ngat iyi mpaka 5years while cashgate mpaka lero mwangoti ziiiiiiiii

aixe Kelly mwanayu ndi kape malo moti aziba zeni zeni busy kuba soya pieces…Hahahaha
Eish!Lamulo ndi lautsiru bwanji!
Eish!Lamulo ndi lautsiru bwanji!
ummmm
ummmm
He deserve that punishment its house breaking

Koma ma judge enawa aonjeza mudzikhala serious mukamapeleka chigamulo uchitsilu wachitika apawu
Thats why prisons are over crowded! Yea to the magistrate can say this was a warning to would be offenders but he was supposed to send him to community work!

The chances u take n the mistakes u make my God is writing on the wall••Ndangodusa ine

Ndiye kuti munthu wosauka padziko, ndiyemwe azipita kundende.

kkkkk yaaaa
kkkkk yaaaa
Nanga cash gate mwawachaja zingati?
Nanga cash gate mwawachaja zingati?
kkkkķkkkķ
kkkkķkkkķ
Ur saying breaking. Henious offence is breaking not stealing saya pieces. He deserve the penalty.

Mmmmmmm
Mmmmmmm
awa a cashgate akuwapasa ma 2 years bwanji,,,,,bwelani muzatenge mk200

Wa cashgate 3 yrs komanso 1 wk watuluka… Ayi chabwino

ndiye kenako okuba singano kwa neighbour muziwalamula 2 yaars. Malawitu ulendo uwu.

yet one associated with bones of people with albinism sentenced to only 5months in central region. .

Someone stole 11 bagala.bars and sentenced to 12 months in prison so u fair

Anthu ena angokhala anjilu,nanga mulandu wa soya pieces mpaka ku court,,,,,,,not nice

5yrs for stealing soya pieces 15 months for being found with human bones is that fair?????

Ukaba zopoila umamangidwa zaka zambiri koma ukaba mamillion ndichaka chimodzi kuti ukagwilitse ntchito ndalamazo.

Ndichifukwa enafe sitikonda kukhala ziko lathu zibwana ngati izi ndibwela ndi mfuti ndizabe mamillion tione

Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkk kkkkkkkkkk kkkkkkkkk kkkkkkkk kkkkkkk kkkkkk kkkkk kkkk kkk kk k

Uyu waba Soya pieces mwamupatsa sentence ya 5 years pamene a cashgate mukulephera kuwapatsa chilango choyenera. Malawi sazatheka ndithu, osauka ife tikatheradi ku ndende.

koma zinazi mukukweza kamba muntengo palichochokhalora kundende paka zaka 5 koma mukawerengeso Buku lamalamulo kawiri mungotengeta malamulo a Nyumba mwanu.

AAA soya pieces yemweyu amapangila tija amadula ku mdulidwe wa azibamboyu…mpaka zaka 5….???si boh

kkkkkk aka 5
kkkkkk aka 5
Komatu Tsiku Lake Ndi Limodzi Limene Mudzadziwe Kuti Amalawi Siopusa.Kamuzu Is A Good Example.Sanakhulupilile Kuti Ndi Amalwi Omwe Aja Opusawa.Tifika Pa Boilling Point Ndipamene Mudzaone Kuti Anthu Amakwiya.Anthu Akupha Anzao Koma Kumawapatsa Zaka Zochepa Oba Soya P Zaka 5.

Mukulephera kumanga kasambala kapena kuwasaka mai aja anaba ndi kugulitsa ndege yadziko ndalama zake osaoneka aja umphawi sizithu eti

zautsiru bas! zaka zosezo chfukwa chasoya yo? nanga amene adaba ndalama zaboma aja bwanj akumango wang’ana?. zaziii

Zaka 21 kutchola shop, pofika zaka 30 bwezi atayamba kuba ndi mfuti… Very fair mwina tsogolo lake laumbava lingaonongeke afta long term imprisonment
apolice ndi majudge bzitsiru poti simudyako bzomwe wababzo.

zopusa basi just becoz he is poor cashget people 2yrs in prizon malawians why we do lyk ths

stealing soya pieces 5 years. Found with albinos spare parts 1 and half years

Aaaaaah zausilu! people are stealing millions of money out ther in the government and they are free citizens now you telling that one got arrested 5 years jail time for stealing soya pieces haaaa.. police ikulephera ntchito yawo. that’s simply to say jail is for us the poor et. they should come in open and declare that!
Ndalama Zimatseka Pakamwa Bro. Ukuwona Opezeka Ndiziwalo Za Alubino Ena Akuwatchaja Zaka4.
Addng to ur point amene anamudula mzake private parts ku BT in 2014 angomupatsa 6yrs, nt life imprisonment,nt fair at o
mxxiiiew it seems these people praise money kwambiri not the law.. samachita manyazi koma akamalengeza zopusa ngat zimenezi
Oooh! Ok , for sure the best judge is God who is never corrupt.
yes you are right brah..
Amphawife Tidzivutika. Km Mkulaka Azipeleka Zilango Zofanana Tose Ndife Anthu.
tingoti phee tiwone ngat kumwamba ndalama zawozo zikawayankhulira…

Koma Ogamula Siwapolice Ndi Ku Court
kuyambila a policewo ndiwa court yemweyo onse ndopepela zitsilu za anthu, ngat malamulo awo ali amphamvu akamange akuba ndalama za boma aja!
Dziko lamalawi ndilopusa kwa mbiri munthu kuba soka pieces zaka 5 Koma wa cashgate mwezi iwiri . Chambatu ichi

koma woba ma million 2 years very unfair
Wooo 5yrs n jail coz of 2.6????? That’s unfair