Man sentenced to 5 years for stealing soya pieces

Advertisement
Machinga

CourtThe Ntchisi First Grade Magistrate Court has sentenced a 21 year-old man to   five years imprisonment with hard labour for breaking into a shop and stealing items.    

According to police prosecutor for Ntchisi Fred Luhanga, the convict, Joseph James, stole 24 tablets of Azam soap and 5 packets of Soya pieces all valued at K2, 600 from a shop belonging to Maliseni Simoni.

The convict pleaded guilty to the charge of breaking into a building and committing a felony therein which is contrary to section 311 of the penal code.

Passing her judgement, First Grade Magistrate Dorothy Kalua said the offence is serious, hence the offender deserve a stiff sentence to     send a warning to who would be offenders.

James hails from Mguza village in the area of Traditional Authority Nthondo in Ntchisi District.

In a similar case, the court in Ntchisi has sentenced Thomas Banda, 23, to four years imprisonment with hard labour for stealing a bicycle.

Advertisement

185 Comments

 1. anthuni ndimati ndifuseko kodi zaka 5 apasidwa okubayo zipundulira ndani,obeledwayo kapena boma,majaji athu muzikhala ndi masomphenya achikondi poweluza,wakubayo ndi wobeledwayo onse ndi ana a amalawi azanu.

 2. Madam magistrare, did i hear you well saying this offence is a serious one? and you mean it? do you remember that gentleman amene anagwirilira mwana wake ku Balaka, was that not a serious offence? how many year did you guys slapped with him? Mudzalangidwatu anthu amalamulonu

 3. Ma #Judge aku malawi amapeleka chigamulo mwa opposite. Ndamva kuti wina wake amafuna kugulitsa munthu pa mtengo wa #mk5_kwacha amulamula kukakhala ku ndende miyezi 9. Where by this little man waba #Soya basi zaka 5? Pliz! Dnt smoke #Chamba mukamapita ku #court.

 4. Lets make a deal with a khoti. Inuyo mudzigamula milandu ingono ingono ngati imeneyi ifeyo tidzisova monga yogwiririra, kupha ndi ina yotere monga anachitira kuNsanje coz you have just demonstrated your stupidity on the way you are passing judgements. LOL

 5. chonde amene mukumudziwa amene anaweluzayo mukangomuonetsako macomments 15 okha basi akaganizenso kawiri komaso ngati amapemphera asankhe 1 thing.

 6. woba soya pieces 5 years,wogwiririra 5 years ,woba ndalama za boma ku capital Hill 0 years(walking away freely),,,,,,what kind of justice is this????
  The paupers will ,at all times, be on the wrong side of a coin…..thats malawi i grow up with.

 7. Munthu or atasowesa track yonse ndie kukampasa 5yrs in jail koma ma judge aku malawi kaya mukumapita ku ntchito mutamwa manip muzaona pole, busa wina anasowesa msikana uja ku mpasa zaka 2 wasoya peaces 5yrs zamisala basi.

 8. Munthu or atasowesa track yonse ndie kukampasa 5yrs in jail koma ma judge aku malawi kaya mukumapita ku ntchito mutamwa manip muzaona pole, busa wina anasowesa msikana uja ku mpasa zaka 2 wasoya peaces 5yrs zamisala basi.

 9. Komatu majaji mwaonjeza kupondereza osauka. Simumva chisoni ai? Niwachingati ameneyu inu nokha? Aja mudawaweruzira mowapulumutsa atakufumbatitsani akwana angati? Inu ameneyo. Tilibe chonena dzilo lidakukomerani anzathu.

 10. Dziko ndilokondera kwambiri, milandu yaing’ono imakokedwa kwambiri while those who r involved cashgate scandle ali pheee kumadya pizza ndi bugger zoti anaba ndalama sizikusonyeza, chilungamu chagonekedwa tulo

 11. judge idiot…mwini shop idiot.. apolice ma idiot.. nonse amene nkhani iyi ikukukhuzan ma idiot nokha nokha.. chimene ndanenela izi mukuziwa

 12. judge idiot…mwini shop idiot.. apolice ma idiot.. nonse amene nkhani iyi ikukukhuzan ma idiot nokha nokha.. chimene ndanenela izi mukuziwa

 13. akuti 5yrs with hard labour, soya pieces yemweyo zachamba eeetii ,osangompatsa community service bwanji…..kumphunzira kugamura mulandu!!!!!!!!

 14. opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

 15. opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

 16. opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

 17. opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

 18. opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

 19. opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

 20. opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

 21. opezeka ndi mafupa a wanthu mukuwapatsa 15 months koma wa soya pieces ndiye zaka 5 koma yaaaa chilungamo chikuvuta dziko lapansi.

 22. Kuba phone or kuba chimanga ndi opusayi wa soya yi, these people azikhala 15yrs olo 20 anthu awa akuononga budget yadziko tikusungila un productive citizens. Akafele kundende koma wa cashgate azikhala 6mths kuti ndalamayo izizungulila

 23. Kuba phone or kuba chimanga ndi opusayi wa soya yi, these people azikhala 15yrs olo 20 anthu awa akuononga budget yadziko tikusungila un productive citizens. Akafele kundende koma wa cashgate azikhala 6mths kuti ndalamayo izizungulila

 24. Masiku ano dziko likukomela olemela coz wina wapha alubino akuti akakhale miyezi 15 pamene wakuba soya pecies zaka 5 kodi moyo ndi soya chilichotsogola m’chani abale? koma tiyeni timusiyile yehova ndi amene adziwa kuweluza kwachulungamo.

 25. Soya pieces anali ochuluka bwanji. Truck yathunthu kapena bwanji. Koma wina wopezeka ndi mafupa a albino miyezi 15 yokha . Wasoya pieces five yrs koma zoseketsa ndithu. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kaya ma khoti amalawi sizizayenda mpaka kalekale

 26. Charles msaku woimba,wanzeru kumalawi mlandu woba mamilion kumangopondeleza koma oba nkhuku womweu mpaka 5 years ,moti mukuona kuti apa pali chilungamo Osward lutepo mabilion osewa 11 years koma soya pieces ndi soap zokwana 2600 mpaka zaka zonsezo,pepani majudge zinazi osamangoti ena atengelepo mphunzilo mukulakwa.

 27. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

 28. Fuck magistrate court,people are stealing billions but u put them into bail,why giving this man five years for the money less than k3,000,please release him and just teach him

 29. Koma ma judge enawa aonjeza mudzikhala serious mukamapeleka chigamulo uchitsilu wachitika apawu

 30. Thats why prisons are over crowded! Yea to the magistrate can say this was a warning to would be offenders but he was supposed to send him to community work!

 31. Thats why prisons are over crowded! Yea to the magistrate can say this was a warning to would be offenders but he was supposed to send him to community work!

 32. Thats why prisons are over crowded! Yea to the magistrate can say this was a warning to would be offenders but he was supposed to send him to community work!

 33. Thats why prisons are over crowded! Yea to the magistrate can say this was a warning to would be offenders but he was supposed to send him to community work!

 34. Thats why prisons are over crowded! Yea to the magistrate can say this was a warning to would be offenders but he was supposed to send him to community work!

 35. Thats why prisons are over crowded! Yea to the magistrate can say this was a warning to would be offenders but he was supposed to send him to community work!

 36. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkk kkkkkkkkkk kkkkkkkkk kkkkkkkk kkkkkkk kkkkkk kkkkk kkkk kkk kk k

 37. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkk kkkkkkkkkk kkkkkkkkk kkkkkkkk kkkkkkk kkkkkk kkkkk kkkk kkk kk k

 38. Uyu waba Soya pieces mwamupatsa sentence ya 5 years pamene a cashgate mukulephera kuwapatsa chilango choyenera. Malawi sazatheka ndithu, osauka ife tikatheradi ku ndende.

 39. Uyu waba Soya pieces mwamupatsa sentence ya 5 years pamene a cashgate mukulephera kuwapatsa chilango choyenera. Malawi sazatheka ndithu, osauka ife tikatheradi ku ndende.

 40. koma zinazi mukukweza kamba muntengo palichochokhalora kundende paka zaka 5 koma mukawerengeso Buku lamalamulo kawiri mungotengeta malamulo a Nyumba mwanu.

 41. koma zinazi mukukweza kamba muntengo palichochokhalora kundende paka zaka 5 koma mukawerengeso Buku lamalamulo kawiri mungotengeta malamulo a Nyumba mwanu.

 42. Komatu Tsiku Lake Ndi Limodzi Limene Mudzadziwe Kuti Amalawi Siopusa.Kamuzu Is A Good Example.Sanakhulupilile Kuti Ndi Amalwi Omwe Aja Opusawa.Tifika Pa Boilling Point Ndipamene Mudzaone Kuti Anthu Amakwiya.Anthu Akupha Anzao Koma Kumawapatsa Zaka Zochepa Oba Soya P Zaka 5.

 43. Komatu Tsiku Lake Ndi Limodzi Limene Mudzadziwe Kuti Amalawi Siopusa.Kamuzu Is A Good Example.Sanakhulupilile Kuti Ndi Amalwi Omwe Aja Opusawa.Tifika Pa Boilling Point Ndipamene Mudzaone Kuti Anthu Amakwiya.Anthu Akupha Anzao Koma Kumawapatsa Zaka Zochepa Oba Soya P Zaka 5.

 44. Mukulephera kumanga kasambala kapena kuwasaka mai aja anaba ndi kugulitsa ndege yadziko ndalama zake osaoneka aja umphawi sizithu eti

 45. Mukulephera kumanga kasambala kapena kuwasaka mai aja anaba ndi kugulitsa ndege yadziko ndalama zake osaoneka aja umphawi sizithu eti

 46. Zaka 21 kutchola shop, pofika zaka 30 bwezi atayamba kuba ndi mfuti… Very fair mwina tsogolo lake laumbava lingaonongeke afta long term imprisonment

 47. Aaaaaah zausilu! people are stealing millions of money out ther in the government and they are free citizens now you telling that one got arrested 5 years jail time for stealing soya pieces haaaa.. police ikulephera ntchito yawo. that’s simply to say jail is for us the poor et. they should come in open and declare that!

 48. Aaaaaah zausilu! people are stealing millions of money out ther in the government and they are free citizens now you telling that one got arrested 5 years jail time for stealing soya pieces haaaa.. police ikulephera ntchito yawo. that’s simply to say jail is for us the poor et. they should come in open and declare that!

Comments are closed.