The opposition People’s Party (PP) has called on government to stop charging duty on imported maize as one way of ensuring that people have maize.
The remarks follow reports that most Agricultural Development and Marketing Corporation (Admarc) depots have run out of maize to sell to hunger victims in the country.
PP acting president Uladi Mussa has argued that many companies have maize outside the country but they are failing to import because of the high duty that is charged on the staple food.
“With the hunger crisis, government could have stopped charging duty on maize for some months until people have some food from the harvest they are to have at the end of this agricultural season,” said Mussa.
Mussa further blamed government for delaying to transport maize to regional Admarc warehouses, arguing that the delay means hunger victims will not have access to maize on time.
While the lack of maize has been blamed on vendors for buying maize from Admarc depots, reports reveal that some Admarc selling points have not been supplied with maize since the crisis began.
Meanwhile, government has disclosed that it will need over K3.5 billion to procure more maize from outside the country.
for sure
Mmmm kaya amene mnavotela bwampini kma 2019 safika galu ameneyu wakwana asa
@p chikweza,plz osamangoyamikira zilizonse,inu mukuonapo chazeru mchani kumbali ya PP?kodi mmesa njalayi vuto ndiomwewo anagulisa chimanga chonse kulephelanso kubwezelamo,vuto laife anthu,timangoyamikira mzopusa zomwe,Malawi sangatukuke ndi nzelu #zombwambwanazo ata
zoona change golo!
Onse ndiamodzi palibe wabwino akanakhala kuti amatikonda bwezi dziko lino lili lotukuka kwambiri koma popeza kwawo ndikuononga ndichifukwa chaka aini dziko tikuvutika pamene obwera akusangalala. Dziwani kuti Nyani ndi nyani ngakhale atamuchotsa m’phiri la Mulanje kukamuika m’phiri la Zomba sangasinthe akhalabe Nyani. Chachikulu tiziyamika kwa Namalenga pa chikondi komanso chisamaliro chomwe amatipatsa pa moyo wathu wa tsiku ndi tsiku
Maliro akatuluka m’nyumba sabwelera Mcp,UDF komanso Peter for president (PP) zidapita kale silibwelera moving forword don’t insulting ur leader (chitsime chimaoneka chakuya pamene chapwera).
vuto lako ndi chani?
komanso muzingolemba chichewa
Munalitaila ku phompho Malawi mungatiuze chani inu?
Gud Idea!
Gud Idea!
hahahahahamanpepan….oredy mention by other interlligent goverment officialz….nice try….lol
zazaziii basiii mavto onsewa ndi pp ndege ili kuti zisiru zokuba basiiiii mukagwere simuzalamula inu mungo zivta
Alamulile ndi abambo ako
amene ukut zaziiii ndiwe mbuzi
yanyamka pp ndakuona ulad tili pambuyo panu
panja amati mumangotsutsa mwapatsa nzeru koma sangapange ati kuopa kutchipa anthu akumvutika aaa bwampini tikumudziwa
Mmesa a pp anagulitsa chimanga kumanama kut chavunda achibuku products anapempha kuti akachione kut akachione amayi aja anachinakaniza amaopa chani ndiye pano mukuda DPP osamaganiza mwanzeru bwanji
Bolani On dat tym, lyf imkafewa,
Bolani On dat tym, lyf imkafewa,
Sure Paja Pp Inaotcha Mankhwala Komanso Chimanga!
Iiih komaso kkkk
….and even all agricultural inputs like tractors, …etc…
thats great Hon Mussa. not only maize even maize flour
the voice for the voice less .muli boo pitilizani
Mr president please listen to this constructive advice
Amene anayamba Dpp ndi amenewo panopa ali ku pp zabwino koma mulimba
Amene anayamba Dpp ndi amenewo panopa ali ku pp zabwino koma mulimba
Amene anayamba Dpp ndi amenewo panopa ali ku pp zabwino koma mulimba
True pitala ndimbuzi
True pitala ndimbuzi
True pitala ndimbuzi
Thats politics i know,not debating 4 u own benefits.majority first political wlils bhind.
Thats politics i know,not debating 4 u own benefits.majority first political wlils bhind.
Thats politics i know,not debating 4 u own benefits.majority first political wlils bhind.
kumeneko ndiye kuganiza mwakuya bravo sir
kumeneko ndiye kuganiza mwakuya bravo sir
kumeneko ndiye kuganiza mwakuya bravo sir
Mmm pajatu boma ili duty chinachilichonse, even ndi ma kondomu omwe, they charge duty. Iiiiiih
Mmm pajatu boma ili duty chinachilichonse, even ndi ma kondomu omwe, they charge duty. Iiiiiih
Mmm pajatu boma ili duty chinachilichonse, even ndi ma kondomu omwe, they charge duty. Iiiiiih
Duty on imported maize ? Be serious guys.This can’t happen.. Chimene tikudziwa ife ndi Ufa basi osati duty pa chimanga..

Mlimi Wa Fodya ngati iwe ungayendese dziko.Change goal ngopusisa sachedwa kusintha mawanga
Zoona Ufa Wa Kuzambia Timapulumulira Uja Awuletsanso Chonsecho Chimanga Akugulitsana Pa Mtundu Wawo.Bravo Change Goal.
Abaiba ndiye mkumakamba ngati amzelu zauchitsilu basi.
Guys timayiwala nsanga bwanji, Bakili Muluzi pa ulamuliro wake anthu anafa ndi njala chaka china chake kumbuyoko , na Admarc munlibe chimanga , koma lero pa ulamuliro wa Peter Muthalika bola chimanga chikupezekako, pa msika chikuonekako
Zavuta Peter
mbola mavendor nonse!!!!!!!
True
Good move
Tell them what is right and ignore what others might say,gud move mussa
Bravo! opposition isamangokhala koma kudzudzula ndikupereka maganizo. MCP ndiye ili pa holiday very quiet as if doesnt exist.
That’s what we need the opposition leaders to do for us, may be the vendors will sell it at the reasonable price.
The president is busy dining and wining at the State House , he has no time to look into people’s problem . Malawians were forced to have this abnormal man to be the president.
vuto amalawi tinavotela chitsilu
Bravo, Hon.Mussa, Sir. This is the type of opposition we need for people’s lives to improve. People first politics. Thanks SIR.
Zamkutuuu!
kupusa , iwe ambwiyako akugona ndinjala ku thyolo uko
Good idea, thats awesome
Nkhan zopusa ngat izi pano ayi PP inatha kale, Chipani chokuba ichi.
Inu apposition kwanu ndikutsusa basi mwapanga chani paulamuliro wanu?simavuto onsewa mkamba a inu
A Galu a PP mavuto onsewa anabwera kamba ka inu ndiye mukuti chiyani apa??
That’s the best solution in older 4 the poor to have cheap maize sturf!
zaziiii
thats the best for our pipo so that the price is affordable to an ordinary person
Mu ulamulo wanu ujamum’kaba ndalamauja, mumalekelanji kupanga zimenezi. musandichimwise, inendiwachalichi mwam’va.
Cos That Tym Kunalibe Njala-simple.Leave Politics Aside This Is A National Tragedy.Govnt Has To Do That!
Man if u dislike the party then just support the point someone raised rather than just be against anything. All politicians are thieves.
But is this guy really using his head?
Mwabadwalitinu? njalayakeiti? taafuseni achambuyanu ngati asanafe akuwuzeni njala imene inaliko 1949. palichaniapa? njala, njala mukumagula galanimilo ndikumadya zifumbaa! ana ausiluinueti?
Iwe makani bwanji,anayamba kuba ndi ambuyanu che Bingu mpaka kuma kasablanka wake kundata kuja.Awa ngakhale anaba koma kunkhani yachakudya sizinafike apa.kuma Admarc chimanga chimapezeka ndipo mavenda sanakweze mitengo ngati pano.ikondeni Dpp yo koma osamangolesa zilizonse,good leader ndiyemwe amamvakonso maganizo awena ndikuwagwirisa ntchito,osangokula mutu wekhawekha ayi

Aamosi, olomukulem’tima ndim’fumu yadziko basi ikulamula. manuyo akungopanga uhule kunjapano, inu ndiulesiwanuwo mukuchedwa m’kunyoza boma, kanda patuwe ngatiwe, osowa om’nenela kapanda mboni wachabechabe ngatiwe oloutayankhula bwanji sikuti olomauakowo orokuboma angafike ata! limbika ntchito usazichedwese m’zanga.

Auze isay!Kkkk
Chiboda nzelu ulibe tapita mmakomo aanthu ukaone mmene anthu akuvutikila ndinjala osati uzikamba zamanyi zakozo
Atripple T, ndimakuonanitu ngati ndinu ozindikila, komano mmm any-way popanda zisilu, am’zelu sangaziwike. vuto kusaenda munakati muzienda, bwezi mutasukikako pang’ono coz olomutapita kwamerica mukapezako ovutika sizingatheke kutitonse tikhale olemela. mwina kuti um’vesebwino ndikuwuze chom’chi, iweyo ulichivutikile chom’cho uyang’ane dela lakwanu lomwelo upeza am’zakoena kwanukom’ko ozilimbikila akumanga manyumba, ena akugula magalimoto komatu njalai ilichomchibe. so zingokuchedwesa ukamalimbana ndi boma am’zako ozindikila akuthamangathamanga.
mavuto sazatha pa dziko lapansi chifukwa cha chinyengo admarc ya pa nchalo apolice amene ndiye akupanga za chinyengo nyamata wina podzudzula anamanga usadzudzule ndi ufulu umeneu wa police kumapeleka matikiti achimanga window yakutseri