Man arrested for being found with Rands worth K4 million

Advertisement
South African Rand

Malawi Police at Kamuzu International Airport (KIA) in Lilongwe have arrested a man for trying to leave the country with forex that had no supporting documents.

Lufeyo Chitukukula was arrested on 18th January around 12:30pm for attempting to externalise forex.

South African RandMalawi24 understands that the suspect was about to board SAA 171 plane to South Africa when he found himself in hands of the law enforcers.

Reports indicate that he was searched by police officer upon arrival at the departures lounge. It was in his luggage where the police found South African Rands worth about K4 million.

However, Chitukula failed to produce supporting documents forcing the police to arrest him. He is currently in police custody while the money has been seized.

Chitukula will therefore appear before court soon to answer two accounts: attempt to externalise foreign currency and illegal possession of foreign currency without ministry of finance approval.

Attempting to transfer currency is contrary to section 11 of Exchange Control Act of the Reserve Bank of Malawi (RBM), whereas illegal possession of foreign currency is contrary to section 25 of Exchange Control Act.

The suspect hails from Tsanulani Village, TA Njolomole in Ntcheu and he is 35 years-old.

Advertisement

186 Comments

  1. Atulutsdwe ndalamazo nd zake sangapte kujon kokaoda nd makwacha ay ayenera tenge ma rand mwamulakwra nd mway wake wamarand inunso mul nd wan wa mak10 mkumat salary .

  2. yankho kawale wale kuzindikila kwako kulipati ulindichiyani pa dziko pano nanga sukulu yako unalekeza pati?vuto la ana amphawi inu mnsanje basi mumalimbana ndi omwe chauta anawadalitsa usafa ulichocho ndi litima lakolo

  3. Umoyo walitima amalawi mukananenakutiwapezekandimakwacha komansopakanakhalapomvekakumumangangatitamvakutipenapake pathyoledwa koma maRand akwazumaeeeeeeee

  4. Ngati ndi umphawi ndi wanu mzibera boma osati anthu wamba ndalama zinabedwa zankhani nkhani nthawi ya Joyce Banda munapangapo chani koma mkumanga munthu wavutika yekha ,. bwenzi mkuti watchola shop kapena ku bank , ngati mkufuna wudindo mwaulephera bwenzani ndalama kwamwini wake ya, Boma lanji limeneli?

  5. Give his own money god will punish u if you want to take that money, A police inu penapake simupangabo ndalama ndi zake bwenzani anavutika yekha kugwira ntchito mkumulanda bwanji, mlungu sangakudaliseni ayi m’makonda kubela anthu basi msiyeni munthu ndi waku Malawi koko koma mkumvutisa , a mwenye amatenga ndalama zambiri kupita nazo kwao simuwagwira why? Amene angadye ndalama yimeneyo Mlungu amlenge ndiziko alisadzike Amen!

  6. kkkkk malawi zawonjeza wina adza ndifuse zopusa ndidzadula masende akewo awone kunotimangwila tchito tokha ndiyewina aziti wazipezakuti koma guys zavuta kumalawi osangolimbana ndi peter muthalika bwanji kuti atsiytse fetereza kumalawiko kapena akuwonjezeleni timalipilo tanuto oopaja simunalandile mpaka pano apolice amalwi eti ndakuwonani zitsilu nzaathu inu

  7. His own money arrested? Thatz bullshit! If tha Police knows somewhere there is bank robbery or 1 is crying 4 his missing money. It will be same the man don’t have document shows all the money belong to him, like wise there will be no evidence bank robb or anything. Then money is for this man, and police must pay arrest innocent person,

  8. Mukumamupemba mulungu kuti akululukire dziko la malawi,angakululuke bwanji mukumachita jeratsi kwa azidzanu, nanga inu chikukunkudzani pamenepo dza chamba basi

  9. Kodi tiphuziseni guys Malamulo a malawi ukamalowa mdzikoli umapanga declare kuti walowa ndi ndalama zingati zakunja?, popeza munthuyu anabweletsa ndalamazi all the way from RSA ndicholinga chodzapanga business, koma chifukwa choti chuma chakumalawi sichlibwino anaganiza zobwelera ndi ndalalama zake zomwe zinali in South African Rands, nanga Malawi imapanga ma Rands?

  10. I think that is the problem of employing someone who has a very small of thinking capacity,lack of education or ignorance.The guy has got rand.not kwacha.why bothering him? Come-on guys!! Shame on u.

  11. Zopusa,amubwezera ndalama zamwiniwake,ndiwabusiness ameneyo,cash gate pandalama zamwini wake ayi mupeleke,business mmene yavutilamu ,zopusa!!

  12. mukanakhala kuti ntchito yanuyo ndiyadongosolo mukanaliuza zoona fuko la Malawi kuti nkhani ya chasowa kapena matafale kuti zinathera pati,mumutuluse mwachangu chifukwa inuyo sidziko la SA ayi

  13. i think de malawi police now dey r going crazy akungopanga zinthu zosanveka mchere akanakhala ena akanangomutulusa kut apitilize ulendo wake ameneo

  14. i think de malawi police now dey r going crazy akungopanga zinthu zosanveka mchere akanakhala ena akanangomutulusa kut apitilize ulendo wake ameneo

  15. guys be serious its obvious that guy has changed the kwacha to Rands….n frm ur own info where do think he is going with the money n wat was he doing in Malawi to find all that kind of money???osamangokamba zinazi think b4 kuti dziko lililonse has got rules n regulations.

  16. Munthuyo mwina anasintha ndalamazo pa black market ku bank kulibe forex ndiye ma receits akanawapeza kuti? Munthu asapange biziness azikdiira forex ikazapezeka ku bank mwina izapezeka 2019 nthawi yoseyi azingokhala?

  17. Koma ma comments anawa akugowonetseratu kuti a Malawi ife ndife mbulu heavy….this guy he had money not supported in his travel documents. …and that means he had money illegally and he deserve to be behind bars…Police job well done

    1. kkkkkk ndakumva m’bale anthu enawa kumvesa kumavuta , ma Admin athuwa mwina akanati azingolemba chichewa chokhachokha bwezi mwina kumvesa kukukhalapo. chimene chimachitika Nachi!! Tikama choka Dziko lina kupita Dziko lina ngati tilindi Ndalama zochuluka chochi ,timayenela kuka Dindisa Envlop ku Bank imeneyi ndi imodzi ya documents ikunenedwayo.osati kuti akuti ndalamazi ndi za fegi Ayii!!.

  18. kkkkkk wat is happening in malawi mukugwira muthu ali ndi ma Rands mwati skutuluka ndi ma Rands kani tayamba kugwiritsa ntchito ma rands instead of kwacha?mumutuluse ngati ali kupolice akanakhala kuti akutuluka ndi makwacha bola.mwalephera kugwira anthu a ndalama za cash gate lero mukulimbana ndizopusa umbuli basi.taoneni khakhi osachapayo

  19. Ine ndikubwera ku malawi ndi ma Rand anga ndagwira ntchito yawukali ndekha kuno,wina wake wa boma la malawi andilande???? Kikkkkkkkkkk zimenezo nde zikwanje ndithu aaaaaaa osamusiya bwanji? Ndizanu ndalamazo???? Kapena alembapo kuti ndizakuba?,? Zopusa basi,ndichifukwa chake malawi tikungosawukabe basi,aaaaaa

  20. umbuli uzatha liti ku Malawi ma comments oukila police kusaziwa malamulo kapena umphawi.Enanu muli kunja kwa malawi chifukwa chani mumakadindisa ma passport ku bank I thought we all understastands the development but it seems civic education on our laws is needed.he must face the laws no possesion of foreign currents without proper documents

  21. Ndalamazo anazipeza via black market bcoz he had no supporting documents. If u do business u need to have a foreign currency account with the reserve bank nde ukamatuluka amakuikila mu passport mwako. Failing which then its a serious offence and I ask MRA kut ifufuze business yamkuluyu i hope he even invades tax akuoneka ndiwachidule kwambiri

  22. Guys Rand ikuvuta kupanga kuno please musiireni here R100,000 sindalama ai musone kuchuluka after exchange Please Please nzotheka

  23. inu ndinu dzitsilu ee kodi anthu asamakhale ndi ndalama akamachoka kunja kuba kwanuko mudzafa osauka kupusa kungonvano kurti kuli njala

  24. Ahaha but guys i think education is very important looking at these comments its sad. Nobody is allowed to leave malawi with more than 5000$ and especially if he does not have a currency control stump in his wallet there is no country in the word tgat would let any one carry that much money out of the country thus is a crime because cash is un traceable when didnt he send the money through the bank all would have been ok but that money is too much it needs to be investigated the police did a very good job in uprehending him

  25. Zausilu nsanje basi a police akumalawi umboniumboni wachani mwamva kuti kumalawiko kubank kwabedwa ma rands mpaseni ndiwabizines amaneyo kuteloko mwamuonongola nthawi ndegiso yamuthawa. Basi mukufuna ndalama zamunthu muyendesele zikolanulo ministry of health mukagulire mapanodo eti

  26. Kdi kweni-kweni chimakhala chani inu apolisinu umphawi kapena nkhanza chabe give him his money akaodere mwina tngapezeko tmaphone tolimba ta johns kma tocheapa 4ro him.

  27. Looking at the comments, one can learn a lot. Everywhere in the world there are policies that regulate foreign currency and there are limits. Don’t just look at the Rand value, consider the Kwacha value of the said amount as well. How did he manage to change all that and what is it going to be used for. Abale tiyeni tilikonde dzikoli; ndi lathu. Sanatisungitse anthu ena.

  28. U must leave that person alone with his cash, everywhere on earth every person has the right to move with foreign currency. Dont restrict pple in that way, tym is money he has alot of things to encounter.

  29. Thats simple is low. And if he has asl if he has withdrow up to the amount, If he done then give him his money. Its low.

  30. Zausiru basi musiyeni ndizake ndalamazo akakhala maluzi ndi anu musalimbane naye inu osapeza zanu bwanji. Nde mumutsegulira mlandu okuti chani? Ngati alimaluzi osangompempha akutchuleni inayake bwanji? Mukuona ngati angalandidwe ndalama zokhala zake? Inuyo ma 3kwacha anu mumalandilawo vuto ndiyeyo ? Ana anjoka

  31. umphawi apolice aku malawi njiru basi amwenye amatulutsa ndalama kumeneko ma china almost every fright nde muzikalimbana ndimunthu mukufuna mutani nazo ndalamazo musiyeni ndithukuta lake nanunso sakani zanu siza jelasizoyi futsek.

  32. thus y malawian u will end up poor , is that a case found with money?

  33. Malamulo Anji Yongwila Ntchoto Pa Anthu Wosauka! Koma Akadakhala Waboma Mkadasiya. Musiyeni Ndalama Ndizake Komanso Anthu Abizinezi Akutukuka Wosafanizila Maripilo Anu.

  34. No wonder chi dziko chi chikungosauka y limiting amount of forex for people did they found out kuti anaba?ish koma kuno dis realy Hell kunena kwa matumbi kuti tizichita kuopa kulemera!

  35. Ngati sanabe awonetse ma risiti a ku bank komwe wasinthira ndalamazo, chifukwa chimene ndikudziwa ine ndichakuti malawi simagwiritsila ntchito ma RANDS. or fullstop

  36. Za ziiiiiiii! Zopanda ndi nchere omwe. Ndalamazo zawo kapena zake? Anamva kuti watchola shop kapena bank pena pake? Koma akanakhala mkulu wa boma mukanangomuyang’a akupita nazo koma osalankhula kanthu.
    Musiyeni naye ndi mwayi wake kupezeka ndi ma Rand.

    1. Mmmm Do u know what our laws says on foreign currency? Even Malawi kwacha ili ndi limit yoti munthu utha kupezeka nao. Zikapitilira limit even zili zanu u can b arrested. Its better to kip it in a bank. To allow de money 2 b flowing.

    2. Kkkkkkkkkk! Kuti nawo a Bank azikazitapa pang’ono pang’ono mpaka zidzathe? Malamulo ndiri kuwadziwa komatu anapanga ndi anthu ndi cholinga kuti awo ndi awa ziwakomere. Pakali pano kuno ku Malawi zinthu siziri bwino ayi. Malamulo akudana ndi a Mpandadzina (anthu osadziwika) koma iwo odziwika malamulo sagwira ntchito pa iwo.

    3. I agree with you ngwazi..ngat a2 akuluaklu nawo akulephela kutsata malamulo nda afuna enafe titani…bas za illegal zomwezo ifeso tipanga asaa

  37. I think there’s a certain amount of money you can carry . Otherwise you have to have the documents from bank that tells where the money is going or from.It does make sense to me{my personal view}

  38. amufufudze kaye monga apolice pantchito yawo kutiamapanga chani? Amapita nazo kuti?amakaguliranazo chani? Wadzipedzera bank yake iti nanga amagula mabwanji? Osati kumangonyodza apolice apa boma likuyetsetsa kufunafuna forex ndie wina azingonyamula mwa any how?ife kuno tikuyetsetsa kutumidza forex kuti mwina dziko lathu likhale nawo forex ndie wina azingoti nazo savusavu tamufufuzeni ameneyo apo bii mungomutcherera bomba coz umeneu ndi mlandu waukulu.

  39. Ngati a police mumafuna ya Fanta muzinena anthu mumavana? Umphawi basi a Police wakukulilani ukateroso wagwirawe ukapeza a kazako ataphika therere shame

  40. Koma ngati amakagula katundu kunja mafuna adzagure ndi ma luvera? Wakwera ndege kusonyeza kuti zake zimamuendera kodi kandalama kalikonse basi adzikhala ndi lisiti kuti mususepo mudzimolonda mpaka muchotse moyo wake, its his privacy athutu ali ndi ndalama ma Euro komko koma samanena uphawiwuso ndi uchimo eti.

  41. okuba inu ziko waliononga ili,ndye mufuna muzilanda athu ndalama zawo kut muzithandizila zikoli ndicholinga tiziti zili bwino mmmmmmmm ……….. shame

  42. Did he stole the rands?? If you want to hav money these days you to have cash sale or receipt bola osamutsa makobili ake pajatu ndikhalidwe

  43. ..with forex that had no supporting documents oh my foot ! when are we going to wake up ? bwerani ku Mangochi ma forex ali mkhonde every currency is available pa mtengo othandiza mphawi ; forex documents ? who provide them ? how long it takes to get ? ma rand wo nga Fake kapena bwanji ; mukatero mumutsekera ; mum’bere ma Rand wo ; akamadzatuluka adzauzidwe kuti Boma linatenga ; pa Malawi

  44. Was he found with Malawian kwacha or rand?? So why arresting him a foreign currency??? Umbuzi wa a Police Aku Malawi akuti kufuna potchukilapo,,Amwenye amatulutsa kwacha kumapita nazo kwawo mumawagwira?? Ngati uli umphawi osangomupempha bwanji??

    1. Ndalamazo ndi zake and si za Malawi. Oyenera kumumanga ndi boma la RSA chifukwa ndiwo eni ake a Rand. Mkulu uyu sanapezeke ali ndi ka Kwacha kanu ayi.

    2. Enanu kaya ndinu a Police kaya mumadya nawo a Police’wo izo ndi zanu. Ndalama zapezeka ndi mkulu omangidwayo ndi zake sanatenge mthumba la boma kapena Kampani yakuno ku Nyasaland. Dziko likanadandaula likanakhala la RSA.
      Ndiye mukuti akanatsata ndondomeko yake yotani? M’mene anapezera ndalamayo bwanji simunkamuwuza kuti atsate ndondomeko yomwe inu ozindikiranu mukuyidziwa? Kkkkkkkkk! Kumvetsa chisoni ma Nyasa. Bwanji simukulimbana ndi ma Burundi/Rwanda amene akumakuberani ka Kwacha kanu kopanda ntchitoka? Kuzolowera kupangirana kaduka basi.
      Amasulidwe ameneyo basi

    3. Aaah u people need to learn the laws of malawi nobody is allowed to leave the country with more that 5000 $ its a crime thats why they have arrested him for externalising forex

    4. pipo r stil in dark the laws everywhere speaks loud n clear abt forex nde enanu mukuti apolice ndi olakwa for wat??? shame kusadziwa ndikufa komwe open yo eyes nd see guys dnt rush to judgement bfo yu kno

  45. Koma malamulo enawa? Was the money fake? What if he worked hard to make that money? Ife ndife anthu akuntcheu tikulodzani muona kkkk

Comments are closed.