Malawi Blantyre based super league side Mighty Wanderers Coach Eliah Kananji has blamed his players for not showing commitment to the game following their 3-0 loss to Mzuzu University FC on Saturday.
The former Bullets coach wondered why the players show much effort during training sessions but choose to not show up during games.
”If they have problem with me they could have said, rather than to frustrate me with their type of play, it’s not football,” said Kananji.
Kananji also noted that the nomads usually have golden opportunities to score in every game they play in the league but they fail to utilize them.
Last weekend, Victor Gondwe who scored twice and Wacheta Mwenifumbo, who netted once for Mzuni, shined on top of Lali Lubani stars Muhamad Sulumba, Luka Bruno Milanzi, Jabulani Linje and Victor Nyirenda who failed to punish the rookies.
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk koma mzuni!!
I love NOMA 4 LIFE;kochi alibe vuto koma ma player makamaka striking force yathu yilibe ochinya zigoli.tingawine bwanji ngati sitikuchinya?next season try to find good strikers.Nawe wa bullets nde usayelekeze kutokota TNM inde mwatenga koma sikukwanilaso kubweza ngongole yanu ya 90 MILLION
Ngati maplayer akukana kugwila tchito awathamangise ndizitsilu
Team manager Chembekezo Zidana achoke munthu wa usiru. amenewa ndi ena amene akupangisa kuti team iziluza stupid manager. Zimatiwawatu.
Noma Ndimaikonda Zedi Koma Panopa Ikuchititsa Manyazi Ngati Sitimu Yayikulu Wake Up KANANJI timu idzichinya vuto ndi chiyanni mapuleya osachinya
Zinachita kuoneseratu kt kinnah ndiakatundu coach wa national team ya Malawi osati zinazi ai………………!!!!!!!!!!!
Vuto nd squad nd yaikulu!35 players;#trim_it.You cant please evry1 otherwise consistency z lost.Ndye2 ndzmenez!
koma nyerere julius ng’ombe zamkaka zinatha?
Shame sure ngati wantchembele mbaya!
msachukise kinnah inali nthawi basi mavuto ndi athu tikoza zonsezi zizatha tiyakhurana timu ichita bwino
Coach aliso ndi chivuto not maplayer okha timpatsa ma game. 2 apo biiiiii achoke
Neba zangomuvuta basi mwina mawa zidzayenda
Yasala fisd Wizard izakung’mbeninso inu a Noma!
Ndinanena ine kuti kumeneko kuli Kinnah Phiri akakuyikani ku dzino. Si izi!
Eliya Kananji ndi kochi wabwino koma vuto ndi loti samapatsidwa ufulu ogwira ntchito payekha. Every substitution amayenera kulamulidwa ndi Yassin Osman kapena Eddington Ng’onamo. Technical Panel ikukokerana mphamvu ndi kochi m’malo mompatsa mpata kuti agwire ntchito yake momasuka ngati kochi.
vuto losaina ma striker amiyendo yonse ya left ndilimenelo
Koma “kananji” ndye wagaya english yabwinotu.kkkkkkk! Interpleter wake ndani ameneyo????
Achoke wausilu ameneyu
A BB NTHAWI ZINA SAMALIPIDWA NTHAWI ZINA AMANYANYALA TRAINING KOMA SANAGONJEPO NGATI CHONCHI AYI.ZAMANYAZI.STUPID MIGHTYBFORWARD PLAYERS.
MAPLAYERS TIMU YA BFORWARD AKUIYALUSA NGATI ASAFUNA KUSEWERA MU WANDERERS AKANGOCHOKA MWAULEMU.
kambiranani muzuni ndi ife anganyu osatopa tikuvua kukoma ukutikumwa wakhati khati bwana wabwino mzuni
To Join the Illuminati family originally called the ILLUMINATE ORDER; explore the ends of riches…..I extend an open invitation to all those who agree with the concept of individual rights to apply to join the Illuminati Order. The more members it has, the greater its influence will be. Join the world of the happiest and most influenced people in the world and be the first to join in your community and spread the word of the famous SASHA FIERCE. Call +2347033672143 Join the great Illuminate.Email:[email protected]
ku bullets kuwina zikho ndi chikhalidwe, dzina lokhalo longoti bullets player amadziwa kuti si team yamasewera nde sapanga chibwana. kananji uxamafanizire bullets ndi noma ndi tsoka
players are not yet payed up to this date salary ya october, how can they work hard?
Katha ka team kameneko ma spornser aku siyaso akuti ndalama zango pita padela mungo joina bb
Nkhan zinaz musamaziike apa zikutithera nthaw waluza, waluza basi. Osangoyang’ana chitsogolo bwanj. Mumainena #bullets kt siichita bwno ths round lero ikulepherayo nd bullets? Tidzingokuyang’anani kt mutani. Tiye nazoni!
khani yamanoma imandigonetsa
Kaya zanuizo
Muthamangiseni ameneyo walephera ntchito. Mpaka 3-O
Iwe ndie coach ngat noma siyako tisiyire ife eni tikoze mavuto athu basi koma kulozana zala no solution at all
sakukufuna kananj
tikumane Ku Bb vs tiga kuti kananji aphunzireko tima technics.
usakalowa bwanji zachamba,mbolatu izi
Akananji akape
Hahahahahahahha just dissolve the whole team including Mr Kananji
Noma iri ndi ma player ambiri abwino koma kananji amakondera maplayer ena samawapatsa mpata thats why angochinyidwa 4sure magame onse amene noma yawina czon ino ref amawathandiza komanso team ija iri ndi striker mmodzi yekha wophonyanso
Kkkkkkkkk ine ndiwanoma koma sunayankhule bwino kkk mpaka wophonyanso kkkk thats bad to my team
Ine ndiwa Bullets! Kananje should polish up striking force! Ife a Bullets tikakhala pa top, timafuna inu muzibwela second! Pazikhala real competition.
Ine ndiye zikundikonda kwa mbiri cz inu anyelero mumayankhula kunya kwambiri!!
Chenjerani a bwana Kananji ndi anthu monga achina Yassin Osman.
ana aakazi akachuluka pakhomo amasowa wotsuka mbale coz amati atsuka mnzangayu chimodzimodzi inu abfwad munagundika kugula maplayer ambilimbili lelo akukanika kupasilana mpira wabwino ndiye mukonzele kusewera musenjele komwe kuli size yanu.
Kananji akugwira ntchito mopanikizika ,exective iwunikepo
ask bb! Nyerere manyi a team!
just waint and see, we wiil come back soon reminds’ Ants is Ants.
Vuto ndilokuti team yachuluka asilamu iyi. Alipotu 10. Nanga mmesa Iwo amakhala ndi Njala akamapanga namazani
Knanji amamenya mpila mbuli za ma player get out
mzuzi univesite job weldone u make it congrats ndaona ena ake akhala chete,,,!
kkkkkkkkkl mudabwa simunat
Koma matama baxi
Ine zanga zikuyenda.
uchimina kananji kayaaaaa dikiranso 3….0 4rm Bankers
Mwina kuzikonda ndikomwe kwakula maplayer, ndipofunika kumapungula enawo
Mukulumana choncho koma ndi students, big 3-0 noma,
I ll be back wit a comment
kananji samatha
Chekananjiwa zikuwavuta2 apa penapake masubstitution omwe akumachitika akumadabwitsa.2 aKananji asiyanitse BB ndi noma BB ili ndi maplayerz olimbikila till 90 mn pamene kunoma akangocinyidwa difficult kut abweze sono akamatengela kut ku BB ndinatele kunonso ndichoco zikuimbilan nyimbo nyelele “NDITHU”
Kananji alibe 1st eleven
Mr moyo mwalankhula kwambiri
yapangisa zonse ndi mzuni kuti manoma afike pamenepa
Kodi Noma ndika Nyama kanji Ku Malawi ko
No idea
Ayamba ndiwowo uluza…..zaziiiii
Zikayambika mumvera ku noma
Kananji wants to blame players than take the blame for irresponsible fielding and sub’s. We must commend mzuni for blowing them apart. No offside goal, no referee errors, clean goals.
Where in a must win game can you start malumbo and kaliat at central midfield leaving khobenjan,a holding midly pa bench? Where in the world can you take out kabango and put victor Nyirenda soon after bringing in fat Mlimbika for the injured suman? Milanzi was drunk,literally, but you gave him a game,then pulling him out for an out of sorts sulumba
Your goalkeeper couldn’t command his defence for all the 3 goals( Enerst was right)
On Sunday Cobenjan and kaziputa started, Vic,fm7,kaliat,milanzi ,sparo were dropped and you got a point.
Stupid coach
This was the worst technical goof
our team z lacking an assistant coach dats y there are poor sibstitutions.A team lyk noma needs assitant coach
U r the best soccer analist
Magame atsalawa chonde muyesese a Kananji mmmm sizikuyenda
Nthawi ya Bingu no donors, nthawi ya JB we had donors, nthawi ya Piter no donors. WHY?
I tnk bcoz they r against the gay issue wch the donors want
abad carpenter always blames his tools!akananji ndiolephera,thats why bb had to bring in ramadhan.