The Blantyre City Council (BCC) has expressed concerns over the increase of unpermitted fixing of posters in Malawi’s commercial city by some residents.
According to a BCC press statement released signed by Alfred Chanza, Acting Chief Executive Officer for the council, some residents in the city are fixing posters to walls, trees, streetlight poles, barricades and other structures using glue and others strong adhesives without first seeking permission from the council as required under Section 44 of the Town and Country Planning Act.
The statement explains that most of the posters and other types of unpermitted advertisements are cluttered and when removed, they leave hardened adhesives that are difficult to remove and the clutter caused by these unpermitted advertisements diminishes the beauty of the city.
“The Council, in line with Section 45 of the Town and Country Planning Act, hereby gives a 30 day notice to all residents of the City to remove all unpermitted advertisements from walls, trees, streetlight poles and any other structure”, says the statement.
The Council has also advised all Blantyre residents to first seek from BCC permission and guidance on how to display advertisements before putting up any.
BCC emphasises that any new advertisement displayed in contravention of Section 44 of the Town and Country Act after issuance of this notice shall be immediately removed without further notice.
nanga a lenhad bonke akuchita ku nyasa blantyre yonse aja bwanj? osangonena kuti akufuna chenje chathuchi bwanj?
Good Idea amalawi tiyeni tizilikonda dziko lathu,kwina kayamkusayenda?ku Ruanda kunali nkhondo koma tapitani mukaone ukhondo wake from mtawuni main city Kigali mpaka ku border ndimaiko ena kuyenda osaona kapepala or botolo lotaidwa very clean.Nanga ife chimatilaka ndichiyani?
Apangisa zimenezi ndi aja anamata za bonke aja aaaah
Malawian Heroes #Pika_Manondo and #Oswarld_Lutepo
M’mene watinyansila Bonke mtownimu, mxiiiiii pano town yonse zigamba za Bonke.
Akufuna anthu azilipira, cholinga azipeza cholowa
bravo Blantyre city council! we need our city to be clean osati mati mati ma poster pena paliponse. there should b designated places where posters should be pasted. i second the idea.
malawi wil die poor bcoz is stil sleeping why fighting against our rights??
Guys umbuli uzatithela. ? ? this nat xumthn political iiiiii iyayi!it’s our city, it’s our responsibility to keep it clean.where you there nthawi ya KB (kamuzu Banda? nayeso amabitsa zama gay? ? ? let’s be reasonable xumtymz before wi gudge
Kumalawi kuli Town yot mpaka kulesa zimenezi?? Kkkkkk
ZOSAMVEKA KONSE. BWANJI OSACHOTSA ZOIPA NDI ZONUNKHA ZA MMUDI RIVER.
AKU CITY NONSE KANYAKANU NDITHU.
The devil is aliar , why now? bcoz bonke is coming ?
what are u saying?
koma kusampunzila kuzatipwerekesa amalawi how does it make u feel the way aome of these poaters are being placed?
whether zamulungu or not order in the way these things are posted in our city has to be noted and guided.
look at these posters of this so called prophet coming they are all over. Zikunyasa kaya penapaluponse its nasty and amnoying.I agree with BCC
Mupengatu ndizazii apa
kkkkkkkk
i support for that idea, koma mukuyenera kuika some like ma notice boards m’malo omwe amakhara busy like ma ptc, post office, shopping malls, markets entry’s, schools & hospitals
mmalo molimbana ndi mbava ziri mu blantyre mwaganiza zolimbana ndi ma poster?? Ndevu phwii ndi pa nkolokolo pomwe kumalimbana ndi poster? Shame
Very good,please include those who urinate paliponse…
so wat about banners did they ban banners also?
Malawi dziko langa mukusiya kulimbana ndi mbava za cashgate nkhani imodzi mpaka zaka zitatu lero mukulimbana ndiwokhoma maposter apatsenitu chochita poti nawo akagwira ntchitoyi amapeza kanganyanse
Zofunika. Mzinda umanyasa. Tiziika pa fb
Chonde Yanga musachose nda khoma lero m’mawa
City iziwonekako bwino abale, ndife osawuka koma tizionekako smart. Osati zikuchitikazi, thats a good move
Taudze anadzolowela kukhal pa malo pa umve, mbudz za anthu
Alese,kumata-mapositawo.Koma,asafulumile-kumanga,anthu.Chofunika,kunchenjeza-anthu,kaye-mwina-kwa,two,weeks
and the right to information?
Amangidwe basi
Poster yaulendo Wa Bushili ,ikadali mtown mu mzuzu. Yina youdza azibamba kukadulitsa (yamu march) Ku Moyale clinic ili kumabank Ku. Ya gara ya pa mzuni(0ne n half months) ili pa round about. Amangen azilipila
Ndiye tizikakhoma kuti
Palibe alese ndiufulu wanu a MALAWI ngati zakunyasani. Paliponse pali office yaboma Poster.
Ayike Zima Plasma Zambiri Ntaunimu Anthu Aziona Pamenepo,osati Reinhard Bonke Pali Ponse Ndi Pachayamba Pomwe
Aziba zimenezi. Amalawi ndi anthu isatheka
panopa ndikukhoma yanga yausing’anga ija,mukut bwanj a BCC
Mverani okoma maposter.komani m.mene mungakomere ndipo muzigwitsa ntchito super gruu kuti asachoke maposterwo ndikulamula ndiyine kapoto osati peter ..peter ndiye ndani kod ndikanyamakanji?
Mwina City Izioneka Bwino, Osat Ma Poster Phwi
kdi inu mukuti maposter achokenu mulimbali iti yanyanio kapena yaife anthu abwinobwino sonondiye muzingo bwebweta
inzitsilu bas iwemphawi wachabechabe ndikumaikila anyani amenewa kumbuyo kd iwe akhukuziwa or ndipang’onopomwe nzandikwiyitsa kwambili abwaphini inu macape inu anthu onyela majumbo mapwalanu kapena pachiolopao
Brilliant!!
Nanga ochepekedwafe mutitani?
Reinhard Bonnke
kkkk! koma amwene nde wakwana paliponsetu mtaunimu
Kungoimika Galimoto Yako Wa Mushop Pobwera Upeza Aimatamata
kkkkkkk anamata pashop ina yake pomatula ndi paint yemwe out
akuzembelera ndani?
Ma radio station achulukilenji good move
akuwopa apanga deliver za zokwatirana amuna okhaokha ndi akazi okha-okha
kodi Noel Chalamanda wa ku Lilongwe ndi ndani?
Heeede heeede town kkkkkk nyumba za dothi mwati town mulibe manyazi eti,akunamatu uyu A MALAWI muziyenda ,let me tell you ndi mbadwa ya BLANTYRE kuyambira pa CLOCK TOWER BP pa kondodo cornershop zonse za dothi apart from MRA building ,escom house up to ma robots zomse za dothi anangopanga face lifting and from Raj ‘Kuj to NICO pakati paja atolamkhani takaonani eeee inu,LIMBE NDIYE. Eeeeee. From standard bank to kapenga all are face lifted kkkkk town
No town without posters.
osakazikiza lamulo lanuro nthawi ya kampeni bwanji? musinje wa mudi ukuwonongeka mukungoyang’ana poster ya mpawi yalakwanji poti sitingakwanise mu-ma radio kapena mu news mukufuna tife ndinjala kodi akubanu?
You read a news paper government is encouraging the youth to contribute to our country’s income mostly by engaging in different businesses hw do pipo do that if our ideas or businesses r not advertised. Oooh maybe on radio or TV, where do thy get that money from? the option ws those walls and trees.
Shyne Young-luv Chikapa
haha yandiwaza imenei lol
Paja you spoke about this hahahahaha
Zikunyazisa tauni zimenezi, zilesedwe!
M.palibe Nkanthu tiziona sitinati
nda agalu ake amenewa
zaziiiiii zenizeni izi
m’mayesa malonda ndikutsatsa,iyi ndi njira imodzi yotchipa chifukwa si onse angakwanitse kulengezetsa malonda awo pa Radio.muganizepo bwino pamenepo.
m’malo mwake nde tidzikhoma chani??
Misomali
kkk mwatelo akulu…
Nde akhome maposter odziwitsa anthu za zimenezitu….
Yes, the city doesn’t look clean with those posters; It is even worse during the campaign period. Let them come up with new ideas and stop the use of posters.
Akunena za Bonke,
zaononga town, ama user bostic ndiye sakuchokanso. Ndiye zikulirenji zima poster zakezo
Tsono mmalo mwake mwati adzikhoma kuti ma poster woo??
mmalo mothana ndi umphawi kulimbana ndi za ziiiiiiiiiiiiii
Nanga asing’anga owonetsa njoka mtawunimu muwatani?
i think mwasotchito eti
Aaa tinganene kuti palizelu apa ma rubish
that is agood idea
rubish ndiyiweyo chifukwa ulibe nzelu
That’s good move
Then ‘ey should Provide Poster’s Walls In Some Places In the City
komadi za bonkie zinanyanya, limbe yonse. Abale tisamale mzinda wathu