Five prisoners have escaped in Mulanje district after they were left at the hospital to receive medication, Malawi police say.
Mulanje police spokesperson, James Kadadzera, refused to name the prisoners but he said there were six inmates at the hospital and one inmate refused the idea of escaping.
Kadadzera said the prisoner who stayed behind has two weeks remaining on his jail sentence and that could be the reason he did not escape.
The six prisoners were to stay at the hospital for two weeks to receive TB treatment.
Ameneo nde Madolo atii!!”’
kkkkkkk Koma Zina ukamvaaaaaaaaaaa ! Iaiaiaiaiaiaiaiaaia
koma out patient amakhala anthu aphamvu, wodwala mpaka liwilo la mtondo odowoka, pasya tonola mkayidi
kkkkkkkkk
what a marathon run! amanamizira kudwala amenewo
Achita bwino, nawoso azikaba ma pipe ku stadium ku lilongwe.
If they were left alone without a prison warder, wat else can they do? Run away soldier basi. Komadi pachithunzipa akupitilira 5
Kuthawa athawa koma chomwe chimavuta ndichinthu chimodzi usawone wa boma akungoziyendera uwona monga afuna iwe, so chenjerani muka saver x2 akakugwirani.
kkkk munkhanimu mwati athawa 5 koma pa chithunzipa ndie gulu,ndie kuti amawapelekedza 5wo? Inutu mumanama mwamva ngati mulibe chithunzi cha nkhani yanu kulibwino kungolemba nkhani osaika chithuzi
Malume nthumba la achimangalo munalakwitsa polingulitsa kwa nokha pamenepo munaba. Ndiyewo pokukalipirani amakukalipirani zoona
Alibho amenewo
no comment….malo aja!!!satana chabe..
Enao anawamanga zoti sanalakwe nde achita bho. If there was an ounce of justice left in this world then JB would be in prison by now
Sangathawe wamba kalipo kalipo. Apolice athu ndima ziwa. Adyapo basi.
muli boh koma mudzingopita ku moshiko mukapume kufikila pamene angazansiye udindo …
..ambuyangawa …….mulimbikile kutawako muwoloke chifukwa mw ndiochepatu atakhukugwila kawili
Hahahaha
Chinachitika ndichiyani kuti abanduke anthu amenewa,mwina anachita kugulisidwa target yothawila
So What?Zikusiyana Pati Kundende Ndikunja Kuno!
???????
Koma ndiyekuti kumeneko kunali kuthamangatu amwene, nanga sii by yoti live buleti ingandipeze ndisanakhote paja! Ayi choncho mwathawa ndithu bola asakupezeni, koma mkangochita zibwana akugwireni eeeeish mngawone mbwaza bwanji!
Ngati chakudya chikuvuta ku chipatala mpaka odwala nkumathawa nde kaye under arrest eeeh ! Mpata ukapezeka fuuumbula !
Mwai satola mjoka mwaonesa udolo nde ukhale kwanu komweko akutolaso
Asiyeni akafele kwawo.
This is not on the warders must explain what happened and what they did with the prisoners
Thanx alot prison escapers 4 the job wel done,u hv succesfully escaped..now u r about to participate round #2 which is #ManHunt
Opusa ndi apolisi powasiya okha iwo nkukagona
Kkkkkkkk, atitengatu akazuka
bb pa top
zonama
Apolisi akugwire iweyo amene unajambula chithuzichi.. Coz sungamangowonelera akuthawa then iwe busy basi kumawajambula
Inenso ndimadabwatu pamenepa kuti ajambula bwanji maguys akudya liwiro.kkkk
Kkkkkkk eti aixeeee kkkkkkk ameneyunso ali ndi mlandu
Mlandu wake ungakhale wanji? Gross negligence kapena breach of peace or wa idle uja? paja a khoba akakwiya amangogawatu milandu.kkkk
Hahaha wa idle wo kkkkk
Coñgrats for escaping, komà mukagwidwa ndi zañu
apolice anali kut?
Chess 3 Man you 0
Indeka ndiyo yakeyo
Prison/hospital break season 7
Akapume
Akati mwayi sindiye kuti waponda wire nkukubaya,,,koma kuti waponda ndalama nkutola…Mwayiwawo athawawo,akukanika kumalizitsa kumanga a cash-gate ndiye kulibwanji oba mbuzi.
pakaphweka timaika phazi kumene hahahahah!
who luvs prison?..
zachamba basi!!!!!!!…
anapusa bwanji apolisiwo? iwo anali kuti nthawo yomwe amathawa akaidi?
aaaaaaaaaaaa
zausilu
..