
Akaidi a mndende 62 alemba nawo mayeso a MANEB a PSLCE
Nthambi ya ndende ya Malawi Prison Service yati ophunzira okwana 62 a mndende ndi omwe alemba nawo mayeso a Malawi National Examination Board (MANEB) a standard 8 chaka chino. Mneneli wa nthambi ya Ndende a… ...