Malawi Police in Nkhotakota district yesterday arrested a 35 year old man for allegedly being found in possession of 65Kgs of Indian hemp.
According to Nkhotakota police spokesperson Williams Kaponda, the suspect, John Gunde was nabbed last night at Kaombe road block after police searched the bus he was travelling in.
“The illicit drug was found concealed in a woven basket commonly used to carry tomatoes and in a green sack bag covered in a black jumbo.
“The vigilant officers upon thoroughly searching discovered the hemp and let the passengers come aboard. Professionally, we identified the suspect through the bus conductor,” Kaponda said.
He said the suspect was travelling to Blantyre from Dwangwa.
Nkhotakota is one of the districts in the country where Indian hemp is highly cultivated.
Gunde hails from Chimbeya village, Traditional Authority Mpando in Ntcheu and is expected to appear before court soon.
akangomva dada Positive~Yute zanu a police nonse,akupherani riddim ndy paja mukumuxiwansotu
Shitiii!zinapezeka pa manda a solomon kma hemp gyz
fuck police!!!! dziko lilibe dollar ili mukuti anthu azitani?? let him to go,, akakumasula ukangolima chako munda onse,,
Just legalize it
kodi mwati ndi Indian hemp Aaaaaa fwetseki ndimaona ngati malawian hemp,,,,
Mumalimbana ndi ife anthu achamba kma zimbalangondo zili ponse ponse mu ndirande……..mumatikhomelera ufulu wathu wachipembezo ife ma RASTAFARIAN tisiyen tibande mwa ufulu!! Fire bon vatican
Mutayeni ameneyo nanga zingafanane ndi oba ma billion omwe ali phe kudya ma pizza ndi ma burger, zopusa!!!
free him pliz, ngati mumachifuna mukadangopempha rather than accusing him of the matter or bringing the guy before the court. Mabi ndithu!!!!
Apolice aku malawi muzachangamuka lit basi bizy kulimbana nd chamba chfukwa chake malawi sakutukuka.maiko anzathu pano akutukuka nd chambacho inu muzingokhala choncho kuvala mapoto mmutumo ati chpewa za zii
i heard that you are legalizing it now why are you criticisizin it, ini will advertise it. tsono mmene mwamsungamo mutakhala kut mwapanga legalize iye ali komweko pomutulutsa mudzamulipira? am totally comfused
Ntchimo siliphuka nthaka koma munthu ndiye abadwa ndi sautso yobu6v5 amalemekeza malamuio aboma kusiya amulungu zitsamba mulungu analenga kut tichite nazo fire burn coolcrax cran akapokola amenewa afe ndithu mmudzina la yesu
you r da great thinka Rastaman I gab dam salute almighty most I jah………..
paja chambagate
Mmalo momagwira mbava za cash gate kapena akuba atii mbwee ntaunimuwa kalimbana ndiwachamba sindiye chambacho chimenecho, mtayeni ameneyo sanaphe munthu 65 kgs kusowa zogwira ku kk ko?
something is happening right now in Mzuzu. plize details.
Apeza podyela amenewo
Inu mufuna mutani nacho
Ok kma wakapokola wakumalawi esh
will vote when weed will be legalised
How much is a 65kg of chamba? fore sure it’s less than K100,000.00, the government is felling to arrest people who are concerned with cash gate scandals. why keeping in custody an innocent person? yet leaving criminals.
Zomanga achamba zidakalipo koma musekedwa nd obama.iye ananenelatu kut chamba chili bwino than beer.
65Kgs yokha basi?
Apolisi akabandike ndi Nazi tsopano nde sidzinena kut chamba tinalanda chija tachitaya pakuti bwanji
Mukamange wachamba kusiya wa cashgate
Kody bwanji osamanga southern bottolers si marujuana akuphika ija ? Ngozi zambili zikuchitika chifukwa cha carsberg bawa
mumango limbana ndiogulitsa koma osutawa simumawa gwira bwanji?mumatha kuma kumananao akuoneka kuti uyu ndiyewa chisuta koma ay osamungwira muza elekeze anyani inu kuzalanda chaine muzaona zoti ambuyanu sanaonepo
business yanga ndiyomweyo,bt wapolisi kubwera kuden kwanga,,ndingamutunge ndi mpeni2
MZANDIMANGESO INE NDILINACHO CHAMBACHO CHAMBILI.
Mukulephera kugwira anthu akupha mukulimbana ndi osuta chamba let him go en just legalise it
DON STANLY KAMWATHENDO AKUGWIRA NTCHITO KU BEYOND FM(92.1 MHz)
Koma inu zoona osangomulanda bwanji?
regalise it..dont criticise it
Just free him
zausilu basi mmalo moti mngomusiya meneyo
Nanga 65kgs ya marijuana apita kukayitaya ku lake malawi kapena apolice ayitha ndikuisuta
Kumupeza akutani nacho?was he smokn th 65kgs mwina wamagulisa?beta zan kubela amalawi osauka misonkho yawo.am sur naye biznes yake ndiyomweyo thou ndiyolesedwa ndi boma wamalelela ana ake.
A polisi awa a ku Khotakota ngatulo man. Amzawo akulipililidwa ma rent plus ma xool fees ukagwirizana nawo bwino anthu amenewa, sikulakwa koma ma British anatitseka mmaso tulo mpaka pano, mbuzi za wanthu.
hahaha
Palibe chomwe walakwa
Cash crisis
Chamba tilima
ndalama nayo yavuta udyo abale
mmesa paja amati boma laloledza kulima ndi kusuta?
He must not be punished bcz is a way of earning money here in MW bcz marijuana is a profitable bzns
anthu inu kumanga munthu ogulitsa fodya,koma akakhala wa cashgeat ndiye kufunsa titaninaye .kumeneko ndikupusa.
anthu inu kumanga munthu ogulitsa fodya,koma akakhala wa cashgeat ndiye kufunsa titaninaye .kumeneko ndikupusa.
anthu inu kumanga munthu ogulitsa fodya,koma akakhala wa cashgeat ndiye kufunsa titaninaye .kumeneko ndikupusa.
eee zachamba basi
Mungolimbana ndi achamba koma cashget mwayilephela
zachamba
Mwawina lero mawa mzachita kukubweletserani nkukuuzani kuti ndimangeni kkk tizaone aliii
usiyeni agulise apeze kwacha inu ngati simumbanda ndizanu.
free him!””
Mumusiye ameneyo
Okuba achulukilenji koma kumanga achamba
if possible share me some police men
Zokhomelera baxi