
Khansala Willy M’manga aikidwa m’manda
Kunali khamu la anthu ndi nkhope zakugwa komanso zodzala ndi chisoni dzulo pomwe amapelekeza kukayika m'manda thupi la Willy M'manga yemwe anali khansala wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) wa dera la Naming'azi mu dera… ...