Bullets yagonjetsa Wanderers
Zatha pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre, oyimbira ndiye waweluza kuti FCB Nyasa Big Bullets ndiyo mfumu ya Blantyre pakadali pano kutsatira chipambano chomwe apeza pa adani awo a Mighty Mukuru Wanderers mu… ...