
Mighty Wanderers yasefa ndikutsala ndi osewela 30 omaliza
Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Mighty Wanderers, Bob Mpinganjira watulutsa m'ndandanda otsiliza wa osewela a timuyi okwana 30 omwe wati ndi amene akufuna kutengetsa nawo chikho cha 2025 TNM Super League chaka chino, monga limakhalira… ...