
Zotukwanizana sizabwino – Atcheya
Ati ndale kumapanga koma mwaulemu. Osati mukafika pa nsanja koma ndiye kutukwana. Atcheya Bakili Muluzi ati zimenezo ayi. Mtsogoleri opuma a Bakili Muluzi adzudzulidwa ndi kuyamikilidwa pa nthawi imodzi kamba kodzudzula atsogoleri a ndale chifukwa… ...