![High Court in Mzuzu](https://i0.wp.com/malawi24.com/wp-content/uploads/2024/06/Tadikila-Mafubza-jpg.webp?resize=235%2C176&ssl=1)
Tadikira tsopano ndi mfulu
Bwalo lalikulu lozenga milandu ku Mzuzu lathetsa mlandu omwe limamuzenga Tadikira Mafubza Mutharika komanso anthu ena asanu ndi awiri. Tadikira yemwe ndi mwana wa a Gertrude Mutharika anamangidwa pamodzi ndi anthu asanu ndi awiriwa powaganizira… ...