Awunikirenso ngati ofesi ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino ndiyofunika, watero Namiwa
Malingana mkuona kwa a Sylvester Namiwa yemwe ndi mkulu wa bungwe la CDEDI, ati ofesiyi ya mtsogoleri wachiwiri mdziko muno siikuwoneka ntchito yeni yeni yomwe ikugwira kotero iwo ati mpofunika kuti dziko lino liwunikenso ngati… ...