
Bambo wadzipha atatopa ndikudwazika mkazi wake
Zina ukamva kamba anga mwala, bambo wina wazaka 81 ku Kasungu waphwanya lonjezo la paukwati lokhala limodzi ndi mkazi wake pamavuto ndi pa mtendere pomwe. Malingana ndi malipoti a apolisi, bamboyu yemwe dzina lake ndi… ...