Man kills cheating wife, kid before committing suicide

Advertisement
Zingwangwa Killings
Zingwangwa Killings
Dead bodies lie in pool of blood in a police vehicle.

There is commotion at Zingwagwa Township where an angry man has shot his wife after he caught her in sexual action with another man.

The husband also shot his kid to death before shooting himself.

Currently, all three bodies have been taken to Queen Elizabeth Hospital mortuary.

According to Blantyre Police Spokesperson Elizabeth Divala, the husband, Charles Chipanda, 52, killed his wife Grace, 44, and stepson aged 13 before killing himself.

She says a pistol and a suspected suicide note signed both by the man and the woman was found near the bodies.

She says the police believe the woman was forced to sign the note, alleging that she was cheating on her husband.

Advertisement

325 Comments

 1. so many comments but chilungamo chomwe mamunayo waphera mkazi ndi step son komanso kudzipha yekha akuchidziwa bwino yekha ndi mulungu wake lets leave it in the hand of God dont judge others

 2. Ine ndamva zot bamboyu amasakidwa nd apolice ,kamba kot anapha munthu.nde atafika panyumba mkazi wake anakwiya naye ndpo anamuopsyeza kut akamuulula kupolice.Nde mwamunayo anakwiya after ziliope.nde anapanga izi kut asaziwike mkuzipha kut asayankhe mulandu.Ndmmene ndamve makonsana.

 3. Cheating is really bad and it is against God’s will .. in another way…it is a sin. but God does nt give us a mandate to kill whosoever cheats .Let God alone b a judge..No wonder that many pipo r supporting this evil act…wat about an innocent kid is he also concerned with dat ??? Repent pipo this is one of the sign that the kingdom of God is near!!

 4. chomwe mwaphera mwana ndi mai ndichani A bale,bwanji osangomusiya nkazi yo bwanji,akazi onsewa pa dziko pano,uwuse mumtendere mwana iwe! .

 5. Oooooh Bad News Is That The Man And The Woman Were Unbelievers Thats Why They All Comited That See And My Bible Tells Me That The Wage Of Sin Is Death See?So You Who Are Reading This News Is Your Life Worthy For The Word Of God?Today We Are Talking Abt These Too And Tomorrow We Shal Talk About You So Bevery Careful Gud Day

 6. THIS IS A PUBLIC SERVICE ANNOUCEMENT!!! AUCTION! AUCTION!! AUCTION!!! THIS IS TO INFORM ALL THE CITIZENS OF NIGERIA THAT THE NIGERIA CUSTOM SERVICE ARE AUCTIONING OUT CLEAN TOKUMBO CARS AT CHEAPER RATE, BAGS OF RICE, ELECTRICAL APPLIANCIES, COMPUTERS AND LAPTOPS, REFRIGERATORS, BAILS OF TOKUMBO USED CLOTHES, JEWELRIES. INTERESTED PERSON SHOULD CALL OUR SALES CONSULTANT CUSTOM IBRAHIM LARRY ON 08130061095. THESE ARE SOME CARS AND THEIR PRICES. TOYOTA HIGHLANDER #650,000 TOYOTA CAMRY #450,000 TOYOTA VENZA #600,000 TOYOTA SIENNA #500,000 TOYOTA MATRIX #450,000 TOYOTA ALVENSIS #550,000 TOYOTA HILUX #650,000 TOYOTA SPIDER #600,000 TOYOTA RAV 4 #500,000 TOYOTA PRADO #650,000 HONDA EOD #500,000, HONDA CIVIC #500,000 HONDA ACCORD #450,000 RANGE ROVER #950,000 GOLF 4 #350,000 PIGEOUT 504 #400,000 PEGUOT 505 #450,000 PEGOUT 507 #500,000 LEXUS #500,000 AND MANY MORE THOSE CARS ARE VEHICLES SIEZED BY US FROM ILLEGAL IMPORTER. INTERESTED PERSON SHOULD CALL OUR SALES DEPARTMENT ON 08130061095 WARNING! ONLY TO NIGERIA CITIZEN! YOU CAN ALSO GET NEWS UPDATE FROM FANPAGE CLINK ON THIS LINK AND LIKE OUR PAGE FOR MORE UPDATE https://m.facebook.com/Custom-Update-1574775269434475/

 7. if the cheater was the man would it had been justifiable for the woman to kill him?? men cheat alot we women forgive u over n over does that mean we r stupid if women kill cheating men how many men would have been dead?? this man had a taste of his own medicine and it was too bitter to swallow ..shamee

 8. Phwala la munthu chitini chapenti. nkazi samangoyamba kuchindisa, tinene chatsitsa zaye kuti njobvu itchoke nyanga. 1-Mfuti? amatani nayo? anaipeza bwanji, oho ndiyake? ndiwapolisi iyeyo? olo wapolisi messa mfuti imakhala ku besi? anaiba? Hule nchi gawenga banja la nyatwa.

 9. Osangosiyana wina wamoyo bwanji,mfuti anaitenga kuti!?Akutiso mwanayo anali steo son kuphera nkhaza basi mwina nayeso anali ndi vuto osachisiya chilungamo chioneke bwanji?Kupha mwana osalakwa zoona shit

 10. Osangosiyana wina wamoyo bwanji,mfuti anaitenga kuti!?Akutiso mwanayo anali steo son kuphera nkhaza basi mwina nayeso anali ndi vuto osachisiya chilungamo chioneke bwanji?Kupha mwana osalakwa zoona shit

 11. Zimakomera amuna ,akanakhala iyeyu man bwezi Ali limodzi ndikaz wake ,koma poti wapanga ndi mkaz eeee mfutiiii, amuna muziganiza pena lake & have 4giving spirit

 12. Zimakomera amuna ,akanakhala iyeyu man bwezi Ali limodzi ndikaz wake ,koma poti wapanga ndi mkaz eeee mfutiiii, amuna muziganiza pena lake & have 4giving spirit

 13. And mwanayo mkukhala oti siwake may his soul rest in hell,Zandiwawa kwabasi anaganiza bwanji kuti aphenso stepson waķe 13 yrs he was just a little boy,May there soul rest in peace

 14. And mwanayo mkukhala oti siwake may his soul rest in hell,Zandiwawa kwabasi anaganiza bwanji kuti aphenso stepson waķe 13 yrs he was just a little boy,May there soul rest in peace

 15. Zinazi tizinbvetsetsa coz munthu akukhalila yokathyola ma nyumba a anthu usiku nthawi yomwe banja limafunika ndipo amakhalila kubisala kuwopa apolisi nthawi yomwe nkazi ndi mwana akufuna chikondi chake,ndizotopetsa izi munthu ungathe kuchimwa kumene coz munthuy samapezeka pakhomo

  1. Life is not all about killing… Why did he do that??? Akanangomusiya mkaz kupeza wina not that,,,,, mfuti anakatenga kut tioneposo pamenepa

 16. Correction; the woman was never caught doint sexual act as put in your news, but rather, the man found information that his wife was cheating. He killed the wife, kid and himself atlast out of jelous if we are to go by the two letters signed by the late man n wife.

 17. Jst imagine ulingat iweo ungatani deaz no nid of killin dat bitch de best way mkungomuthotha akaptlize ku3litsana katunduo.Men plz plz wek up diz’re ada yrz dont kill tkapsele zina coz i dislyk men to go to hell kunayanjana ndi akaz omwewa

 18. Ndamuthokoza kwambiri mkulu ameneyi ndipo wapanga ndendende ndizimene ndimaganiza ineyo.azibambo amzanga mukangopeza mkazi wanu akupanga mchitidwe umenewu tiyeni tiziwapha azimayi oterewa.ndikuti tiyeni tiziwapha azimayiwa.chonde azibambo amzanga mzathuyi watipasa chitsanzo uyu ndipo ndikudziwa kuti azibambo ambiri asangalala ndi nkhaniyi ngati mene ndasangalalira ineyo

 19. Iiiiiii koma kt tionetsetse yakula a bamboo ndi msanje chifukwa zikatele timamule basi apitili u hule wakeo.koma mpaka kupha nde akazi athatu. osewa!!

 20. How did you know that it is a man who killed the other two since the man was also found dead? Did you find a suicide note with information that the wife was cheating?

 21. It iz writen in the holy bible “we shall all die” its cause being sin. But police officers, medical doctors , etc ignore this,

 22. Mwayitha man; n mkadakonda zoterezi zitamachitikachitika tsiku ndi tsiku.Akuzolowera kobasi azimai aku Malawi uhule;mwano+nkhanza kwa azimuna awo.Ngati uku werenga text yangayi #ULEMUWAKO kuyambira lero ndiwe nzanga undipeze pa #MALAWI SUN HOTEL udzadye mgonero nane;kenako tikudya ma pulani obola ntambo kuwayenda njomba yovuta okulondola asochere.Mbuzi zina zili kuno ku #RSA za akazi apusa ukawatengera kuno akajaira mkupeza zochota amayamba njomba;mwano kenako mkukusasa mwamwano tiyambanso kumawadulako makosi kuno #MUSAMALE

 23. Mwayitha man; n mkadakonda zoterezi zitamachitikachitika tsiku ndi tsiku.Akuzolowera kobasi azimai aku Malawi uhule;mwano+nkhanza kwa azimuna awo.Ngati uku werenga text yangayi #ULEMUWAKO kuyambira lero ndiwe nzanga undipeze pa #MALAWI SUN HOTEL udzadye mgonero nane;kenako tikudya ma pulani obola ntambo kuwayenda njomba yovuta okulondola asochere.Mbuzi zina zili kuno ku #RSA za akazi apusa ukawatengera kuno akajaira mkupeza zochota amayamba njomba;mwano kenako mkukusasa mwamwano tiyambanso kumawadulako makosi kuno #MUSAMALE

 24. life is so precious.. killing yourself is a weakness.. people are struggling for life in hospitals. why not leaving the wife and move on. there is much more to the story that we don’t know.. am not convinced with the reasons.

 25. life is so precious.. killing yourself is a weakness.. people are struggling for life in hospitals. why not leaving the wife and move on. there is much more to the story that we don’t know.. am not convinced with the reasons.

 26. Eeeeish malawi watanganidwa. Yap Sharia law will help maybe awa osanduka njoka masanawa, ogwirira ndi ozembera *achikondi* awo atasogozedwa mmanda so that mbewu imeneyi isasalenso mmalawi muno.

 27. Eeeeish malawi watanganidwa. Yap Sharia law will help maybe awa osanduka njoka masanawa, ogwirira ndi ozembera *achikondi* awo atasogozedwa mmanda so that mbewu imeneyi isasalenso mmalawi muno.

 28. Mkazi mwakumana naye mutakula kale why having all trust in her? One to trust is Jesus because he never disappoints anyone. Believe and trust in him. If you trust a human being , one day you shall regret. We are human beings and everybody has weaknesses. So dont waste your time to trust anyone. We are all sinners. May the spirit of the child Rest In Peace

 29. kaya zawo izoo mahule always kuwakwatira amavetsa munthu kuwawa,timanena kuti mkazi ukamuona kuti Ali ndizibwenzi zambiri kuli bwino kumusiya,akazi ndi ambiri pa malawi pano

 30. kaya zawo izoo mahule always kuwakwatira amavetsa munthu kuwawa,timanena kuti mkazi ukamuona kuti Ali ndizibwenzi zambiri kuli bwino kumusiya,akazi ndi ambiri pa malawi pano

 31. Mkazi wina aliyense ndi hule,tiyeni tikhale ochenjera kwambili amunafe.Atha kukuvundula nthawi iliyonse usakuyembekezera iwe kubalalika kenaka kuchimwa nazo.Eva(mkazi wa Adam) ndamene anayambisa uhule namubalalisa Adamuyo uchimo ndikulowa padziko.Tawerengani za Samson muBible kuti mphamvu zake zinchokere si mkazi(hule)kodi?Nanga mfumu Ahab amamulakwisa ndindani pobwelesa milungu ina pakati pa ana a Israeli simkazi kodi(hule)?Mukakhulupilira Kwambili muzakhumudwa ndipo azakuchimwisani,Satana amawagwilisa ntchito kwambili chifukwa anaonesa kusavuta kwao mu Eden muja ndiye akaterono amakhala nyambo yotikolera ife amuna nkutichimwisanso.Mkazi,eeeeeeeee…chenjerani nayeni,ndigwero latchimo!

 32. Mkazi wina aliyense ndi hule,tiyeni tikhale ochenjera kwambili amunafe.Atha kukuvundula nthawi iliyonse usakuyembekezera iwe kubalalika kenaka kuchimwa nazo.Eva(mkazi wa Adam) ndamene anayambisa uhule namubalalisa Adamuyo uchimo ndikulowa padziko.Tawerengani za Samson muBible kuti mphamvu zake zinchokere si mkazi(hule)kodi?Nanga mfumu Ahab amamulakwisa ndindani pobwelesa milungu ina pakati pa ana a Israeli simkazi kodi(hule)?Mukakhulupilira Kwambili muzakhumudwa ndipo azakuchimwisani,Satana amawagwilisa ntchito kwambili chifukwa anaonesa kusavuta kwao mu Eden muja ndiye akaterono amakhala nyambo yotikolera ife amuna nkutichimwisanso.Mkazi,eeeeeeeee…chenjerani nayeni,ndigwero latchimo!

  1. yoo point taken n ukangofika pokut wamugwila nde kut anayambira kalekale mulungu amakhala kut atopanaye n mapeto atchimo ndi imfa bax

 33. Another version to the Zingwangwa tragedy: It is alleged that the man was an armed robber and was wanted by the police. He therefore went into hiding. Last night he came and he started quarreling with the wife and the boy who was his step son was on his mother’s side. The wife then threatened to tell the police that “the criminal” z home or reveal his hideout to the police. Bang! The bastard sprayed bullets on the wife and the boy before turning the gun on himself…. Pheee! Waiting to hear the version from police. Koma life version yomwe tikudziwa ndiyoti anampeza mkazi wake akuchitidwa phwando…

 34. Munthuyu sanalakwitse ngatidi amamubela nthawi ndawonako galu akuluma galu mzake kuteteza kuti asasuse koma sikuti amabweletsa chakudya kuti adye galu wa mkaziyo olo chitenje samugulira ndiye ngati amapanga nsanje galu ndiye munthu akanatani a

 35. Good idea except killing the child and leaving that guy whom he caught with bwenzi ndikut zilibwino afera #chigololo. Akanayamba mamunayo kenaka nkazi then mwini wake.

 36. that’s cool Nigga, killing foolish lady then chikd juti asavutike, kenako iwe mwini esih RIP

 37. Ndimwamuna wakeyo akamumphatikiza kumuthila ma chaka. Mwina kuti ena atengele mphunzilo. Wamkanzi kumugwilila ntchito kuti mwina azipeza chakudya ndi ana! Ukuso mkumadyesatso katundu, mwamuna wanuyo atani?

 38. Tisanyozanepo tokhatokha apa kozi wi all dont know what evil sprirt comes to the lady to do that kind of thing ,while she knows she iz married on the other hand we also dont know what comes to that to jurge like that ,let it b like that,satan on duty.

 39. Nop dts a lie da lady wsnt cheating she’s a friend of myn koma amunawo NDA ma ARV nde amazunguza ubongo ngati misala olo pena amatha kudzicheka okha ndi mpeni osazindikila kuti akudzipweteka ndipo ngati musakuwadziwa dzina lawo ndi MR MKWAYILA

  1. George ndilibe nawo ntchito onuozawo bola ndawawuza chilungamo ngati asakukhulupirira ndauza poti apite akamve bwinobwino adzauze anzawo akukomenta za bodzawo vuto lake anthu ena NDA thomasi didimo

  2. Guys a person is telling u de truth walakwitsanso mpakana kumnena kut ndi hule come on if u dont have a comment seat and relax ok.

  3. dis s not only a page which has published dis, r u telling me dat all the pages hadnt investigate b4 posting? iyi si nkhan yot utchukile

  4. Mpaka ku anglican voices zomwezi? Aliyese kumpingo amakhulupilika even u, sikut ungapange nyasi ku church, mayi uyu adali hule ndipo mamunai sadalakwe i rest my case sure

  5. Hahahahaha a duwa ndaona zotchukila ine nat izi koma poti ndinu a thomasi didimo ndakuizani kuti pitani ku Anglican yaku chitawira olo mutakapeza abusa awo nde midzandiuze kuti ndikukuuzani bodza ma page enawo Ali ngati yomweyi yosafufuxa yomanena khani zabodza osamangokhulupirira zilizoxe zolembedwa ma page mu end a duwa ine xindinati muhulupirire zili ndinu

  6. I Personally Agree With #Nambe, She’s Telling You Guys The Truth And I Happen To Know This Guy Bigtime..
   Osamangotukwana Munthu Yemwe Ndi Source Without A Valid Reason OF Disapprove.

   Search: #ZINGWANGWA_LA_FAMILIA

  7. I Personally Agree With #Nambe, She’s Telling You Guys The Truth And I Happen To Know This Guy Bigtime..
   Osamangotukwana Munthu Yemwe Ndi Source Without A Valid Reason OF Disapprove.

   Search: #ZINGWANGWA_LA_FAMILIA

 40. akazi anchitidwe umenewu achulukitsa mnthuyu ndamuyamika kwambili akazi ena atengelepo phuzilo,evn me i can do this iyeyo wapanga mwachisoni kupha nkaziyekha akanaphaso ndimwamunayemwe zikakhala zamimbayo sitchimolake

 41. Nzimene amachita Satana2,amakunyengelera wezi wezi ukamadzatutumuka,bullet in ur head…pofikira mkazi kuitana chibwenxi n ur own house zimakhala kuti spiritualy u r down n zero

  1. iwe mfuti ndi chida chozitetedzera from any attack chabe kuti iwe siungakwanitse kuyipeza kma ndiyofunika ya licence kukhala nayo ine choncho ndili bize kufunafuna kma yanga ndiyothudzulira magay

 42. anthu enanu ndekut Satana mmamulolad kukulamulani zopusa eit. mpaka apa? Yekha akudziwa kut mulungu anati usaphe bt mkumachitilabe…mpaka kupha mwana osalakwa? enaso alipompa apa a commentaso moti azazichita ndithu

 43. Mulungu apa aweluze mzimu wa bambo ameneyu masiku anowa palibe chifukwa chomaphana chifukwa cha banja ndibwino kusiyana mwamtendele ife otsalafe chifukwa uyu wapita ndibwino kupewa nchitidwe ngati uwu

 44. I always tell my niggas never to trust a bitch…see now? Tf is this? Killing an innocent child? You will burn in hell bra….RIP duh

 45. Its very unfair kuti wapha ndi mwana Yemwe akanangopha mkazi atleast things could have bin fair,Cheating is not good ngati sukumukonda Masulanani basi aliyense ayendele yake

 46. Zimapweteka indeee koma the guy akanaugwilako mtima,wat if wanagwidwayo ndi iyeyo???Badness is that zimakomela amunafe…nway,may thy rest in peace thou apha baby wosalakwa.

 47. Eish so sad but the fact isman amamukonda kwambili mkaziyoo so that z why he decided to kill her and to committ suicide

 48. We hate cheaters in Malawi… A man short a bitch b4 he commiting suicide. May his soul rest in peace n’ her bitch will suffer to hell for ever fuck mxxxiee. Malawi is doomed adultery, rape, homosexual, cashgate, mhhh stinking habits we want sharia law here….

  1. Usakhare mbuli m’bale wanga “Usaphe” mau awawaMose anawadziwa bwino lomwe zomwe amkatanthaudza ,amkatanthaudza usaphe munthu osarakwa not nyama yodyedwa ndi munthu orakwa you will find King David killed Goliath,Joshua was a commander ambilimbili azitumiki amapha anthu orakwira malamulo monga ra “Usachite chigololo” munthawi ya mose amamugenda miyara opezeka akuchita za chigololo mpaka amwalire… Not only this people even adani achipembezo amaphedwa, do you know Samson?? Don’t misuse bible words God will punish you!…

  2. Pa mwana po sitikudziwa couse yake mwina mayi ake amalalata mpaka kufika ponena kuti mwanayunso siwakoR.I.P(only God knows) Koma munthu ukakwera BP chinachilichonse chimachitika wrongly. Azimayi azaka zathu zino mhh kaya mmalo officemu zikuchitika zonyasa ndithu.

  3. killing innocent person ndi tchimo kupha chigawenga chikufuna kukupha isnt tchimo becoz usanaphe umayamba kupempha mphamvu from God zot ulimbane ndichigewangacho ndikuzipulumutsa

  4. Hahahahahaha kma amuna ena ngofoilad mkaziyo anali okongola motan?akanakhala maliya magadalena bola kma akaz a2wa ndia contract ukakhalapo ndwako ukapta ku vep or kwina ndwaena kkkk kumalimbla2 mtma ukamafuna kukwatla masku ano ndgame xikwanje

  5. Hahahahahaha kma amuna ena ngofoilad mkaziyo anali okongola motan?akanakhala maliya magadalena bola kma akaz a2wa ndia contract ukakhalapo ndwako ukapta ku vep or kwina ndwaena kkkk kumalimbla2 mtma ukamafuna kukwatla masku ano ndgame xikwanje

  6. Sitikuyenera kupha olo munthu atalakwa motan kuweruza sikwathu ndikwaiye mwini wake Mulungu.zinangovuta kut opulumutsa panalibe kma tikuyenera kupulumutsa kut wina asaphedwe uno ndi m’bado wina

  7. Sitikuyenera kupha olo munthu atalakwa motan kuweruza sikwathu ndikwaiye mwini wake Mulungu.zinangovuta kut opulumutsa panalibe kma tikuyenera kupulumutsa kut wina asaphedwe uno ndi m’bado wina

  8. Tchimo lamzimay nde mumaliona loophya azibambo amasiku anonu nde ndinu otani mumakhala ndi akaz 10 munthu mmodz nde musazitenge ngat ndinu angelo kulibe wabwino pano

  9. @Tuma wt do you mean “uno ndi m’bado wina” pls tell me.
   .
   Kill all the mosquitoes to end malaria, mchitidwe wachisembwere sungathe ngati dziko likuyang’anira mkuma sekerera we need to take action. Mamuna wa mbali inayo akanakhara mamuna wako I believe ukanakanika kudya pa tsiku la reloli… Not couz you head dat some1 iz dead nah couz he is de cheater and this man needs to be stoned to death mxiee busy busy kugawa matenda ali ndi p***y kunyumba koma kumavulanso azimayi ena mesa mumalonjezana mpaka mmanda? I hate this shit…

  10. Lets Not Use The Scriptures For Our Own Lasts When You Talk Of Those Old Garantee Soldies Of That Was A Time Of Law And Now We Are In Grace Period And You Who Said Abt Sheria Law Do You Tel Me That You Dont Sin Its Only That Your Sins Are Not Being Exposed See Lets Not Judge People By Our Thinking Lets Use The Word And The Word Says All Have Come Short Of The Glory Of God See?Jesus Said Live Them And Its Shal Be Seen At The Last Day.The Bible Says Cursed Is He That Comite Sucide

  11. Barnabas “We are in grace period” do you mean that Jesus diead on the cross for someone to cheat his/her partner no!!! People u r using words wrongly that’s why tili ndi mipingo yambilimbili kmagwiritsa nchito buku limodzi koma kukanika kufanana muka khulupililidwe ohh lemme get out ov dis story…

  1. Leave the wife, & shoot to kill the man, nkazi timateteza ngati mmene timapangila ndi nkhuku pomupha bvumbwe akamagwira nkhuku mmakola athu full stop

Comments are closed.