Zibwana zofinyana pakhosi: nthabwala za Ichocho zikhumudwitsa a Malawi
…apolisi awayendere — katswiri wa chitetezo Ena akukanika kuyankhula momasuka chifukwa akuopa kukupidwa makofi. Ena ndiye angomasula. Koma a Malawi ochuluka aoneka odabwa ndi vidiyo imene watulutsa phona wa mu mzinda wa Blantyre, Ichocho, yolengeza… ...