
Boma lati lagula mathalakitala 8 oti athandize ulimi wa m’ma Mega Farm
Boma lati lagula mathalakitala asanu ndi atatu omwe agawidwe mzigawo za chitutuko cha ulimi mdziko muno (ma ADD) ndi cholinga cholimbikitsa ulimi wa ma Mega Farm. Nduna ya zamalimidwe a Sam Kawale atsimikiza izi pa… ...