Kalindo wamangidwanso
Dzulo apolisi amanga mtsogoleri wagulu lomenyelera ufulu wa anthu la Malawi First a Bon Kalindo pa Kamuzu Road m'boma la Salima. Malipoti akusonyeza kuti a Kalindo awamanga pa mlandu okhudza kufalitsa uthenga osayenera pamasamba a… ...