BWB

Madzi akwera mtengo

Kuyambira pa September 1 2024, ogula m'dziko muno akulipira pafupifupi 10 peresenti yowonjezera pa mtengo wa madzi omwe akugwiritsa ntchito pambuyo poti unduna wa zamadzi ndi ukhondo wavomereza kusintha kwa mitengoyi. Malingana ndi chidziwitso chomwe… ...