Alimi adandaula ndikupselera kwa mbewu kamba ka dzuwa
Ngakhale kuti mvula yayamba bwino m'madera ambiri m'dziko muno, alimi ochuluka akuti ali ndi nkhawa kuti sakolora zokolora zochuluka mchaka chikubwerachi kamba kakupselera kwa mbewu zawo zomwe anabzala ndi mvula yomwe ankayiganizila kuti itha kukulitsa… ...