
Khirisimisi isakuloweni mnthumba – atero Papa
Mtsogoleri wa mpingo wa akatolika pa dziko lonse lapansi Papa Francis walangiza akhristu kuti asaononge makobiri mu nyengo yokumbukira kubadwa kwa Ambuye Yesu. Papa walankhula izi ku likulu la mpingo wa katolika ku Vatican. Ndipo… ...