![Malawi Nyama ya Galu](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/12/Nkhani-ya-nyama-ya-galu-ku-Angola-276x176.webp)
Mabodza: Nkhani ya nyama ya galu siyinachitike ku Malawi
Malawi24 yapeza kuti nkhani yomwe ikuyenda m’masamba a mchezo yoti anthu amagulitsa nyama ya galu ku Dowa siyinachitike ku Malawi. Pa masamba a mchezo a pa Fesibuku kuyambila dzulo madzulo pabuka nkhani yokuti anthu atatu… ...