Chiyanjano Mbeza akanizidwa kutuluka pa belo
Bwalo la milandu munzinda wa Lilongwe lakana pempho la belo la mkozi wa nyimbo Chiyanjano Mbeza yemwe anamangidwa poganizilidwa kuti wakhala akutulutsa ndi kufalitsa mauthenga onyoza mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera. Malingana ndi oweruza… ...