MACRA yadzudzura kutumizirana zithuzi za ngozi ya ndege
Bungwe lowunika mauthenga la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) ladzudzura mchitidwe otumizirana zithunzi zowopsa za ngozi ya ndege yomwe yachitika Lolemba m’dziko. Malingana ndi kalata yomwe wasayinira ndi mkulu wa bungwe la MACRA a Daud… ...