
Ulendo uno mukabera zisankho ndidzathana nanu – Mutharika
Mtsogoleri wakale wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP), Peter Mutharika wanenetsa kuti masankho amene akubwera pa 16 September ngati patadzachitike m'chitidwe obera, iwo ndi chipani chawo sadzalora… ...