Nthambi ya Immigration yatsutsa kuti maina a anthu omwe ali ndi ziphaso zoyendera asowa
Nthambi yoona zolowa ndi kutuluka mdziko muno ya DICS yati mphekesera zomwe zimkuveka kuti nthambiyi ilibe dzina ngakhale limodzi la anthu omwe ali ndi ziphaso zoyendera mdziko muno, ndizabodza. Nkhaniyi ikubwera pomwe nthambi ya DICS… ...