Boma likufuna limange bwalo la masewero kwa Nsundwe
Pomwe bwalo ya Kamuzu ili chikalambire ku Blantyre, dera lomwe linatchuka kwambiri nthawi ya ziwonetsero m’chaka cha 2019, Nsundwe, lalandira mphoto ya bwalo lochitilapo masewero lomwe boma lalengeza kuti likufuna kumanga kudelali. Nkhaniyi yadziwika pomwe… ...