A Malawi adzalipira pobwezeretsa chiphaso cha nzika – NRB
Nzika za dziko la Malawi zomwe zikhale ndi ziphaso za unzika zimene zili mkati mogawidwa mmadera ena zikuyenera kukonzeka mokwanira bwino pofuna kubwezeretsa ziphaso zawo zikazasiya kugwira ntchito kapena zikazasowa. Malingana ndi mneneri wa bungwe… ...