NRB yati ikupitiliza kalembera wa nzika mu gawo lachinayi
Bungwe loyendetsa ntchito ya kalambera m'dziko muno la National Registration Bureau (NRB) lati likupitiriza gawo lachinayi la ntchito yolemba nzika zonse zomwe zilibe ziphaso za unzika komanso zomwe zimakhala kutali ndi ma ofesi a NRB,… ...