
Abambo achikulire omwe akuganiziridwa milandu yakupha apatsidwa belo
Abambo asanu achikulire omwe amaganizilidwa milandu yakupha ndipo milandu yawo sidayambe kumvedwa patantha nthawi yaitali, alamulidwa ndi bwalo lalikulu ku Zomba kuti atuluke ndikukadikila za milandu yawo kunyumba. Abambowa akhala akusungidwa ku ndende yaikulu ya… ...