Anjatidwa kamba kopha aMalume ake
A Polisi m'boma la Dedza amanga mnyamata wa zaka 20, Joseph Sankhani pomuganizira kuti wapha a malume ake. Malinga ndi m'neneri wa Polisi ya Dedza, a Beatrice Jefita ati mnyamatayu yemwe amachokera m'mudzi mwa Kawaliza,… ...