
Zayang’ana kungolo: khothi lati Kalumo sioyenera kutsogolera nthambi ya Immigration
Ogwira ntchito ku nthambi yowona zolowa ndikutuluka m’dziko muno ya DICS akuyenera kukhala osangalala pomwe bwalo la milandu munzinda wa Blantyre lalamula kuti Brigadier General Charles Kalumo asiye ntchito ku nthambiyi kamba koti anasankhidwa mosatsata… ...