Vutoli silitha pano, naye Kachaje alibe chiyembekezo, watelo Namiwa
Pakutha pankumano omwe anayitanidwa ndi mkulu wa bungwe la MERA Henry Kachaje, mkulu wa bungwe la CDEDI, Sylvester Namiwa wati zikuoneka kuti vuto la kusowa kwa mafuta a galimoto lipitilirabe ponena kuti naye Kachaje alibe… ...